Okha okha ku MCP akuumba mkota ndi imfa ya Chilima patsogolo la MCP panopa😂😂😂

Ойын-сауық

Пікірлер: 84

  • @NEBERTMVULA
    @NEBERTMVULA15 күн бұрын

    CHAKWERA, MKAKA. KUNKUYU. CHIMWENDO BANDA, ZIKHALE NG'OMA, CATHERINE HARA be careful Malawians are watching your footsteps!!! MCP IS ENDED. IT SHALL NEVER EVER BE AGAIN!!!

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v14 күн бұрын

    Palibenso chipani chilichonse mMalawi Muno chingazaphatikizane ndi MCP palibe ndipo uku ndikutha Kwa mcp

  • @elishakalungwe6899
    @elishakalungwe689914 күн бұрын

    Eeeee how did you record this guys, respect to you

  • @user-iu6mr5xu6r
    @user-iu6mr5xu6r15 күн бұрын

    Pepani a MCP, mwaononga kopanda manyazi. Dziko la makolo Anga lanunkha kwambiri. Mtendere uja watha, yatsala ndi nkhondo yopha anthu oyankhula za nzeru.

  • @RalphB265
    @RalphB26514 күн бұрын

    😂😂😂😂uyuy ndiwabodza

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience228314 күн бұрын

    Ngati Chakwera sanamange Mkaka, Kunkuyu, ndi Zikhale ndiye kuti anali limodzi popanga chiwembu chopha Chilima.

  • @InnocentMlowoka-ew4lo
    @InnocentMlowoka-ew4lo14 күн бұрын

    Muthu uyu amalakhula ndi friend wake, akuchenjezana kuti azake😂😂😂😂

  • @DJ-APPETIZER-MW-265
    @DJ-APPETIZER-MW-26514 күн бұрын

    Akuveka ngati alikumunda komankhaniyo ndiyowona koma uyuyu ndi garden boy😂😂😂

  • @WalkerElick
    @WalkerElick7 күн бұрын

    Mzimu wa munthu ndi ovuta ndipo awululana okha okha

  • @AmandaConstance-fx8cr
    @AmandaConstance-fx8cr15 күн бұрын

    😂😂😂😂😂😂😂😂 No secret under the sun that is it

  • @KHAHMWAMAD
    @KHAHMWAMAD15 күн бұрын

    Chaka Chinoo muphana ndithu mmmmm nginii ndiyomweyoo

  • @mphatsosadiki4983
    @mphatsosadiki498315 күн бұрын

    Mwabudula mpunga wa Gulu 😂😂

  • @BwanaGD
    @BwanaGD14 күн бұрын

    Ukatamba kuamawona kumawa kumakuchera ngati zililimu

  • @user-zx3pz2wy1j
    @user-zx3pz2wy1j9 күн бұрын

    Wenanu mumangotsutsa bwanji munthuyu akunena zowona.

  • @user-ge5su6ex8k
    @user-ge5su6ex8k14 күн бұрын

    😂😂😂😂😂😂 akuti ma hule awawa tu kkkkkkkk

  • @user-oh8nj8yx6d
    @user-oh8nj8yx6d15 күн бұрын

    I'm on yo side kma iwe ndimbuli😂😂😂😂

  • @Luxemaven8686
    @Luxemaven868614 күн бұрын

    The pressure is getting worser!!!!!!

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa14 күн бұрын

    Mpaka kusakaniza ndi kachizungu

  • @VasasaMoyo
    @VasasaMoyo15 күн бұрын

    Unaboza iwe galu ulindi udindo wanji iweyo

  • @user-ge5su6ex8k

    @user-ge5su6ex8k

    14 күн бұрын

    😂😂😂😂😂 km ndaseka

  • @actuarialscience2283

    @actuarialscience2283

    14 күн бұрын

    Mukuganiza mungabise ufiti wanu in a MCP. Zomwe mumkafuna zatheka ndipo Chakwera wanuyo adzapezeka pa ballot koma ifeyo voti sitidzamupatsa. Kale lija tinavotera mfiti yanuyo kamba ka Chilima osati iyeyo

  • @MaryBanda-ts3vp
    @MaryBanda-ts3vp15 күн бұрын

    Mmmmm zaboza ngat

  • @GiftManuel-er7yh
    @GiftManuel-er7yh14 күн бұрын

    Chokamoni bro mufera dzaweni

  • @Wonder-boyNtago
    @Wonder-boyNtago14 күн бұрын

    Kma chaka chino zilipo ndipo muziona nonse a MCP coz achinyamata Ife tinali pambuyo panu coz chachilima anja ndie apa bas

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg15 күн бұрын

    Chakwera mlomo ngati mphaka😂😂

  • @NditajiMaxwell-cz8ir
    @NditajiMaxwell-cz8ir14 күн бұрын

    Aaaaaa uyuyu sakuziwa kalikonse zambiri akungokaikila ngati akukanika kuzwa zomwe kunapita chilima b4 death aaaaaa uyu sanapasaneko even moni ndi chakwela

  • @user-ik5sz8hc6f
    @user-ik5sz8hc6f12 күн бұрын

    This one is not a politician

  • @Anthonymendos
    @Anthonymendos14 күн бұрын

    Kaplezidenti kuthawa munthu wamba kupelekezedwa malawi

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp15 күн бұрын

    Agalucha kwera 2025 you go

  • @user-us5hw4uy3t
    @user-us5hw4uy3t14 күн бұрын

    Kape wa munthu uyu mmangeni

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs13 күн бұрын

    Is this one of Government???

  • @ShaibuYussufu
    @ShaibuYussufu8 күн бұрын

    Ameneyo ndigalu kwambiri osadandaula athanyiwa ndakapolo achabe chabewa

  • @ExcitedCornflowers-nw9oc

    @ExcitedCornflowers-nw9oc

    7 күн бұрын

    Kapolo ndiweo zigewenga Inu.

  • @NickisonNkhoma
    @NickisonNkhoma15 күн бұрын

    kkkkkkk umbuli ndiwanga koma uyuyu ngat amayankhula nd mzake bwanj mzakeyo sanavekeko mawu or inakakhala VN bwez ma notifications akuveka ine ndimatsatilani gayez koma apapa mwamwetsa ai ai

  • @user-mj2te7vl6p

    @user-mj2te7vl6p

    15 күн бұрын

    Technology is higher

  • @neemahkapatamoyo9563

    @neemahkapatamoyo9563

    15 күн бұрын

    Munthu uyu amatumiza VN Kwa nzake

  • @NickisonNkhoma

    @NickisonNkhoma

    14 күн бұрын

    @@neemahkapatamoyo9563 malume VN sikhala choncho mmmm ilili vomelan nd bodza

  • @kingsleyhopematchaya5184

    @kingsleyhopematchaya5184

    14 күн бұрын

    Mbuzi ya muthu iwe ungayakhulane ndi presindent iweyo aaa

  • @kingsleyhopematchaya5184

    @kingsleyhopematchaya5184

    14 күн бұрын

    Mbuzi ya munthu iyi

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy14 күн бұрын

    Kkkkkkkk koma Malawi wafika povuta

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o14 күн бұрын

    Hmm awa simisala koma??? 😢

  • @MaryMakina-nh2eo
    @MaryMakina-nh2eo15 күн бұрын

    Makape kkkkkk bodza lokhalokha

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj15 күн бұрын

    Zabodza izi makape inu

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v14 күн бұрын

    Chakwera manyazi bwanji wapha Chilima chifukwa cha udindo galu iwe

  • @user-hg5oj3ko1o
    @user-hg5oj3ko1o13 күн бұрын

    Akuyankhulayu ndi ndani

  • @IsmailNdemanga
    @IsmailNdemanga14 күн бұрын

    100 % ndi boza ili 😂😅

  • @chifundopetro422
    @chifundopetro42215 күн бұрын

    Litchafo cabinet

  • @BrotherPaul-ln2ld
    @BrotherPaul-ln2ld14 күн бұрын

    English though 😂🤣

  • @morgansilungwe
    @morgansilungwe14 күн бұрын

    zilikotu zilikooo

  • @lindamalunjika6581
    @lindamalunjika658114 күн бұрын

    Yeremia 33:3

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo31527 күн бұрын

    Mumangeni munthuyu plz mcp murikuti

  • @Yahiya-wm8nd

    @Yahiya-wm8nd

    5 күн бұрын

    walokwa chani ?

  • @user-dk6yc8pl2m
    @user-dk6yc8pl2m14 күн бұрын

    Ayambapo

  • @user-xi2jz8ru1w
    @user-xi2jz8ru1w13 күн бұрын

    Bola mukudziwa kuti ndichipani chakupha

  • @user-hl3vl9nt1b
    @user-hl3vl9nt1b15 күн бұрын

    Simunati munya agalu inu

  • @jomochirwa
    @jomochirwa15 күн бұрын

    Kodi mwangoyesa sewelono?

  • @spargomw

    @spargomw

    15 күн бұрын

    Kkkkkkkkkkk sewero lake la Isaac nd Jacob😂😂😂

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo13 күн бұрын

    Zambiri ziululika

  • @TwalikiWisiki
    @TwalikiWisiki13 күн бұрын

    MCP yatha,we are done with you,, I will personally make sure

  • @jamesgama5489
    @jamesgama548915 күн бұрын

    Za satanic basi ku mcp ko ndale zawo amachita usiku chifukwa chani.

  • @tingo3155
    @tingo315514 күн бұрын

    This is the end of mcp

  • @sheila5812
    @sheila581214 күн бұрын

    Bodza😂😂

  • @Kilocssreaction
    @Kilocssreaction15 күн бұрын

    Nde mwanya nayotu mvamubebe 2025

  • @juliusnjerengo2610
    @juliusnjerengo261014 күн бұрын

    Nde zikumveka ngati akulima bwanji?

  • @user-ge5su6ex8k

    @user-ge5su6ex8k

    14 күн бұрын

    😂😂😂😂😂 akuveka dii akulima kkkk km zoonad

  • @SameKaposa

    @SameKaposa

    14 күн бұрын

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @ArnoldBinali
    @ArnoldBinali14 күн бұрын

    Kkkk kod

  • @IgnatiousFote
    @IgnatiousFote15 күн бұрын

    zitsilu zakumana

  • @joycechidzungu7047
    @joycechidzungu704715 күн бұрын

    Kagwele uko iwe

  • @user-um6yo6nc3e
    @user-um6yo6nc3e14 күн бұрын

    Zina ukanva

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no14 күн бұрын

    Inuso musatinyase

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp14 күн бұрын

    Iiiiiii Tamva nawo ambuye akudalitsen mwauzenso Kut iwonso adzafanso

  • @user-fq4kv8dj4t
    @user-fq4kv8dj4t14 күн бұрын

    Bodza ili

  • @Imraanjafali
    @Imraanjafali15 күн бұрын

    😅😂😂😂😂😂😂😂

  • @AminAbbass-xc4qk
    @AminAbbass-xc4qk14 күн бұрын

    🎉🎉🎉🎉🎉n😂😂😂😂😂😂😂

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo14 күн бұрын

    Dunderhead....empty tin.

  • @Luxemaven8686
    @Luxemaven868614 күн бұрын

    🤣🤣🤣🤣🤣🤣

  • @LucianoKapepuza-sy9wx
    @LucianoKapepuza-sy9wx14 күн бұрын

    Your time is over

  • @EvansJalisi
    @EvansJalisi14 күн бұрын

    You must be very useless ..wakutuma ndani???

  • @ChaibishuSwadck
    @ChaibishuSwadck15 күн бұрын

    Whatever we going to change government 2025 chakwera his must go

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa15 күн бұрын

    Anthu awawa zawo zada bansi akutitenga ngati ife ma Malawians we are very stupid ur time is over now

  • @allanmakwiti5145
    @allanmakwiti514514 күн бұрын

    Koma aMalawi tachangamuka

  • @cynthiakananji1608

    @cynthiakananji1608

    11 күн бұрын

    This Malawi heee palibeno chinsinsi.munyaaa

Келесі