Келесі
- 12:20
- 71 М.
- 24:27
- 70 М.
- 01:01
- 319 М.
- 10 күн бұрын
- 00:54
- 55 МЛН
- 10 күн бұрын
- 00:16
- 110 МЛН
- 23 күн бұрын
- 00:11
- 11 МЛН
- 18 күн бұрын
- 27:38
- 38 М.
- 10:39
- 89 М.
- 4:50
- 3,6 М.
- 11:03
- 56 М.
- 13:10
- 247 М.
- 11:48
- 93 М.
- 14:24
- 2,8 М.
- 0:31
- 1,7 МЛН
- 0:24
- 1,2 МЛН
- 0:59
- 3,5 МЛН
- 0:51
- 4 МЛН
- 0:31
- 1,7 МЛН
Пікірлер: 83
Komansotu ka mkazi ka Che Mandota ko nkolongolola
Che Mandota kufuna kwawomba a Land land,
Kkkkkk Mandota mpaka kusiyana njila ndi adona kuopa thabwa
The lengend in mw MAndota team 😃😃😃😃😃
kkkk kuyigula pang'ono pang'ono
😂😂😂😂 Chemandota mumatha inuyo ndi madam anuwo
Mumakwanila end mumandizangasa
I like the professional acting and maturity in this yellow hurt guy
Tili pa map big....izizi osazasiya mukutiimirila Chemandota 💓
2024 here
Eyaaaa,, my opinion che madota , clara akuyenera azkhala ur wife in each and every episode cz amakita bho ndipo mumakhalana akspanga play rule imeneyi,,,, gud advice keep up ,,, osafooka
Zilibwino pitilizani
Chemandota 😅😅😅 mwasewera yosathekatu apa
Che mandota 😃😃😂😀kuchuluka mnzeru ndi nyumba ya Eni akewo... kkkkkkkk
Iwe umakwanira mandota
Adha ndinakusowatu
Mandota number one
Usanilosele kasi wafaa not bad bro UAE
Keep up the good work
Iweo umatha every Wednesday ndimadziwa kut ndiseka basi 😂 😂 😂
i like. this Kamnkhani guy. he knows acting .....
Nice one
😂😂😂🤣🤣🤣😂😂🔥🔥🔥🔥Mmaitha uncle mandota,,, akulu ao alibe nzeru akanakhala azeru akadamasungira ndalama mkukwana 2 Mita yomwe amafunayo😂😂🤣🤣,, nde apa aliso ndi ngongole 400pn ta Mandota🤣🤣😂😂
@elizamalikebu
Жыл бұрын
Koma amai amairi kuthamanga pakana mendo kmangunda khongo pamenepa mwaiphula ndi lnuyo
Kkkkk kma nde mwathamangatu madam kuwasiya mbuyo kkkk nice Mr mumatimvetsa kukoma
Kkkkkkkkk zili bwino kwambili .... ndikufuna 2 yankhe
Ngongole simakhala ndi malamulo choncho chemandota
Machoni, prolong Mr we all proud of you 👏 ❤
Mandota umatha
Kkkkkkkkk koma yeah, kalibhoo
Salute
nice mathematics
Umakwana Mandota
Mundisungile nyumba🤣🤣🤣✊
@tripmateluggage1217
3 жыл бұрын
Mandota upitirize
Umatha aise
Koma mandota Mesa umalipila ngati rent kkkkkkk ukufuna umubere mzakoyo
Nyatwa kwambiri basi
Kkkkkkkkkkkkkkkk koma chemandota
U teaching them 😃😃😃
Chemandota
Kkķkkk so fanny Koma ndaseka kkkk inu mumakana kwambili boss
Irmã mais força 💪💪
Che Mandotawo kodi..kkkkkkeep it up
Nyumba mpaka lay-by 🤣🤣🤣🤣🤣🤣😍😍
inuyo ndi one
Ndimakinyadira che mandoto
Big boss always salut to you
Chemandota mulibho
Kkkkkk che Mandota ndi akazi anu simulibwino😂
Kkkkk
It's lit !!!
Ishiiiii koma ma guys mukuyatsa moto kumalawi kkkkkkkkk always love your comedy mandota 😂😂😂😂
Manchoni...
This video is so much lit🔥🔥🔥
Kkkkkk 🤣
Kkkkkkkk
Kkkkkkkkkkkkk ndikuloza wathawa 😃😃😃
Hello pipo
Hahahaha kodi nkaziyo dzina lake ndindani?
😂😂😂😂
Che Mandota mwandichititsa manyazitu mu bus ndimangoseka ndekha ngati wamisalatu klkkkllkkkkkkk mukamapanga upload muziwona kaye kuti anthu alipati kodi 😅😅😅😅😅😅😅😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@CHEMANDOTACOMEDY
3 жыл бұрын
pepan
Well done che mandoda👏
Mandota wabwelako ku Uganda kuja ?
Epizode inali bwino iyi ngati Zomba ya chambo
🤣🤣🤣 tachedwatu comment 🔥
Ngalusaaa
Clean basi kkkk.
Kkkkkkk very funny
Kkkkkk usaloze mkazi wanga kkkkk
Kkkkkk koma kubaaa ukuu
🤣🤣🤣🤣🤣🤣❤️❤️❤️❤️
1🤣😂😂😂❤❤
Mandota
Che mandota km kuba Kkkkkk mumatha
Landlord kawawa
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Kkkkkkkk a mandota
koma kkkkkkkk
You've made my day 🥰
🤩🤩🤩🤩🤩🤩