NJINGA YA 14 MILLION KWACHA MMALAWI ALINAYO |

Пікірлер: 47

  • @D.RJALLI-qo6yd
    @D.RJALLI-qo6yd27 күн бұрын

    Ine ndikuikila umbone kuti ndi dzowona ndinapita ku 4ways around Johannesburg kuli shorp dzina lake ndi bike terk menemo njinga yodula ili pa R230000 limu loka menemo R17000 teyala R7500 ndidzowona

  • @StevenBwanausi
    @StevenBwanausi23 күн бұрын

    Mapazi ako khalanayo 14 milion akugula ambuyako

  • @JonathanMsiska
    @JonathanMsiskaАй бұрын

    Aphunzitse anthu aziziwa zinthu za original ndipo ya 14,000,000 ndiyotchipa kwambiri chifukwa Trek butterfly ndi 500,000 US dollars keep it up bro I will come to visit you.

  • @user-pf5hu2pd2b
    @user-pf5hu2pd2bАй бұрын

    Guys njinga idzidzi tsidzachibwana ayi idzodzo ndindege dzapansi njinga dzodula kwambili kunoko ku south Africa timagula njinga imodzi pa ntengo wa R30000 R40000 ina mwaiyo ndilinayo

  • @user-hg2cw1om1p
    @user-hg2cw1om1pАй бұрын

    Ndizoona njingazo zodura kuno almost R100, 000 ndiye a malawi kusayendaku mungathe kusamvesesa

  • @ChimwemweAsifa-wh4mf

    @ChimwemweAsifa-wh4mf

    29 күн бұрын

    Pa Jon pomwepa mpaka muzit amzanu sayenda?😂

  • @user-hg2cw1om1p
    @user-hg2cw1om1pАй бұрын

    Yes ndizoon ifeyo kuno tikuziwa ❤

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo7153Ай бұрын

    Mzanga adapatsidwa ndi mzungu wake njinga ngati imeneyi,adamuchenjeza kuti usakakwere ku location,komaso ukafuna kuyigulitsa Upite ku pawnshop ukapeza plus minus 15k, Iye kusadziwa kufika ku location weekend kuyikwela shaaaa adakumana ndi ma coloured qdampatsa makofi njinga adatenga, anathema atatupa nkhope

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5iАй бұрын

    I don't want to say too much, but let's just say, glory be to heaven

  • @SildaKatundu
    @SildaKatundu29 күн бұрын

    Zikutengera financial status yako to comment on this njinga kkkkkkkkk

  • @jacobchimtaka3057
    @jacobchimtaka3057Ай бұрын

    mabwana ameneyo sakunama sikuzikweza koma pachilungamo ngingazo ndizodula and ndizolimba

  • @scoobymatola8314
    @scoobymatola831423 күн бұрын

    Zili bweeee kuno ku stellenbosch

  • @JozzyJozzy-xt8tg
    @JozzyJozzy-xt8tg28 күн бұрын

    14 million mwadya zowawa eti

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nnАй бұрын

    Mmmmm matama akewooooo! ZOKHWIMA BASI

  • @user-uc1pd1tc2x

    @user-uc1pd1tc2x

    Ай бұрын

    😃😃😃😃

  • @Aaronnjunga
    @AaronnjungaАй бұрын

    Wathuwathu uyu phwetekere boy area 36

  • @mrsmoseskita9180
    @mrsmoseskita9180Ай бұрын

    Kodi ndiyazonse njingayo ngati toilet ilimomo

  • @MosesMbendera
    @MosesMbenderaАй бұрын

    Zoona izi ineso ndinali mmodzi mwaosavesesa km ndinaina ndipo or kukwera sizomwe momavaz km vuto or teyala eeeee ndiyamoto kale

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2xАй бұрын

    Komatu guys aaaaaaaaaa Ngati kuli kusuta 😂😂😂😂

  • @FosterChilumba

    @FosterChilumba

    Ай бұрын

    Kuno ndi R45,000 R 1 to K130

  • @user-uc1pd1tc2x

    @user-uc1pd1tc2x

    Ай бұрын

    @@FosterChilumba hahahahaha zovutatu😃😃

  • @user-ez1kc7zp9m
    @user-ez1kc7zp9m27 күн бұрын

    Aaaaa zachamba basi 14 mita economy yake itiyo??

  • @user-he4jv1sb1m
    @user-he4jv1sb1mАй бұрын

    Njingayo ikutchipanso

  • @Kambuzipaul7
    @Kambuzipaul7Ай бұрын

    Mpaka 14milion iwe chamba timasuta ndse ukubalalika ndwe

  • @user-tq8xi4jg7x

    @user-tq8xi4jg7x

    Ай бұрын

    14 million kwacha akunena zowona

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bjАй бұрын

    Zoonadi njinga zimenezo ndizodula kwambiri umboni ndilinawo South Africa

  • @user-uc1pd1tc2x

    @user-uc1pd1tc2x

    Ай бұрын

    Kuteroko uli ku South Africa, ndinkana usamadziwa ululu omwe a malawife tikuunva ndakuonani

  • @uzaleuzale8603
    @uzaleuzale8603Ай бұрын

    Ayipititse kwa chimwendo amugula ndamene ali ndi ndalama zoseweletsa😂😂😂

  • @abdulsalammkwepu3321

    @abdulsalammkwepu3321

    Ай бұрын

    Zikhale bwa? Iye sangagule? Kapena iye amakonda ng'oma? 😂😂😂😂

  • @ChimwemweAsifa-wh4mf

    @ChimwemweAsifa-wh4mf

    29 күн бұрын

    😂😂😂

  • @T0R1N0.
    @T0R1N0.28 күн бұрын

    This is bastard guy's....14 millions ...njinga akuyitchula ma dollar or makwacha

  • @StiveKantiki
    @StiveKantikiАй бұрын

    Kodi kumalawi kungovomeleza zoti anthu azilima Chamba mwayamba kulezela nacho ugule 14m ikakupezavula uzibisala kkkk km😂😂😂

  • @ChipiliroSpencer

    @ChipiliroSpencer

    Ай бұрын

    Abwana njinga imeneyo ndumvomeleza zamtengo umenewo kuti ndiyomduladi ngti muli kuno ku south kuno ku capetown ndinaiwona new 170thousand rand ndemuisingunule kwacha ndindalama zingati musalese abwana

  • @lastonekaponya7675
    @lastonekaponya7675Ай бұрын

    Mwakangotola uko mudziti 6 million kakkkkkkkk kwazungu amangotola izi

  • @user-tx7xz9kf1w
    @user-tx7xz9kf1wАй бұрын

    😂😂😂😂 wasota kumene ameneyo

  • @imransamson5308
    @imransamson5308Ай бұрын

    Wachamba uyu

  • @WysonChimtengo
    @WysonChimtengoАй бұрын

    Ayinakeo zimawapindulira not Malawi

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4scАй бұрын

    Ndiye,akaigule ndindani,akagulitsa,kwa chakwela 😅😅😅😅😅,akamugula

  • @user-uc1pd1tc2x

    @user-uc1pd1tc2x

    Ай бұрын

    😃😃😃😃😃😃

  • @alexmkolongo3089
    @alexmkolongo3089Ай бұрын

    Zoona zake ndimitengo yake sakunamaso

  • @LumbaniNeba
    @LumbaniNebaАй бұрын

    Bola kugula njinga yamoto iyaaa

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517Ай бұрын

    Herrod antipas

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507Ай бұрын

    😂😂😂😂😂😂😂koma gulizitu aaaaaaà

  • @WysonChimtengo
    @WysonChimtengoАй бұрын

    Eeee koma ay guys

  • @FrankAdonis-zl6qc
    @FrankAdonis-zl6qcАй бұрын

    Kkkkkk

  • @user-hg2cw1om1p
    @user-hg2cw1om1pАй бұрын

    Ndizoona njingazo zodura kuno almost R100, 000 ndiye a malawi kusayendaku mungathe kusamvesesa

  • @user-hg2cw1om1p
    @user-hg2cw1om1pАй бұрын

    Ndizoona njingazo zodura kuno almost R100, 000 ndiye a malawi kusayendaku mungathe kusamvesesa

Келесі