Келесі
- 17:19
- 163 М.
- 16:28
- 153 М.
- 00:27
- 4 МЛН
- 2 күн бұрын
- 00:13
- 2,6 МЛН
- 19 сағат бұрын
- 00:25
- 25 МЛН
- 7 күн бұрын
- 00:18
- 22 МЛН
- 22 күн бұрын
- 10:42
- 218 М.
- 10:50
- 155 М.
- 11:48
- 94 М.
- 1:00:16
- 63 М.
- 8:11
- 80 М.
- 12:37
- 111 М.
- 22:39
- 86 М.
- 24:27
- 71 М.
- 0:50
- 4,9 МЛН
- 0:39
- 3,8 МЛН
- 0:46
- 1 МЛН
Пікірлер: 491
Mumakwana guys mlelemba ndiwe katundu mwana wamtonga from uk keep it up
This girl called Ma Mayili she’s so best in acting I mean best actress🔥❤️🙌
Ine ndimakhala ku nkhotakota ndingatani kuti ndipeze nao malowo
This lady acting as Mandota's wife is a good actor.
Koma ziribwino guys koma mlelemba plz osamamusiya kupanga naye comedy plz
Koma maliro awawa anali obebesatu🤣🤣🤣🤣🤣we need such honesty maliro walira yekha mkazi
Mandota ndi wa sirious komaso nkazi wake ndiwolimbikira zedi. Zimenezi ndizomwe zimafunika, osamalekerana popanga zinthu!!
Waojo bulasa ngani jine big up those who dont apreciate your work are just burukenges bro
Ma actor nonse plus make Maili ndinu madolo. Eee Mlelemba kukakamila🤣🤣🤣🤣
Welcome back ma maili...u are my favourite in this
Yomweyo big mumatipatsa chilimbkitso
Mlelemba my favorite...big up Mandota🔥
😂 😹 🤣 😂 🤣 Komatu Tisiya kubwerekana ndalama.
Ma mayili ua so beautiful
Big up🥰😘😘🥰 next time ndizakunjambuleni ndi ine ndthu for free🥰😘🥰
nice bro munasowatu mwabwera ngt coming inuyo mandota born again respect to u
Ati palibe zokwela kabaxa povaya ku chipatala uyenda yachimuna ❤😀
Ndita ndi Dolo ndinthu ❤
Nane ndiyambe sewero ndizamtenga mleremba
A very good concept, however it needed a warning to medical personnels not to get involved to such acts pang'ono, or kumapetoko ka langizo kameneko kamafunika kwambiri coz kuchipataku may be zimachitika in one way, orelse akanangomwalilira kunyumba kuja ndi Traditional doctor uja, it would have matched with the ending..... my views
Bp ya bwinobwino,ma sats abwino bwinobwino,si Hysteria imeneyo😀😀😀😀
Che Mandota unandisisimusatu ndimawon ngat so wona kkkkk usamapange zimene so usandifa ndi mtima kkkkkkk
Angelo avala chani ngati mwamwaliradi komaso Angelo Gabriel pano alikuti😂😂😂😂😂 only these two questions from mlelemba make me lough
@martinfrancis57
Жыл бұрын
Eeeee mlelemba si munthu wamba kkkkkkkkk
Aubrey Matiki is on a different level 🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Mwaitha guys ulem wanu ndithu
Ukukomesa Malawi koma zikuvuta sapot broo ndinu 1
Akudwala chani, akuti akudwala zonse🤔😅😅😅 safe container. Takufilani ndithu
Mumayitha ankolo 😆😆😆😆 thanks for bringing mlelemba madala
Ma Maili is briant. Get your flowers. The whole act is awesome. Big up. Waiting for more
@DysonChimbalanga-vv5qq
Ай бұрын
Kkkkkkkk mandota ur best act😅😅😅
Okwenya ngongole akhale mlelemba hahaha
She Mandota mukonse mbiri yanu. Bayizoni Mulelemba zi mundu wozeweleza.
Mwachena jesi ya fulemus kkk
Amati tisaope ngongole kma na apa pa ofunika kuiopa
Nkhani ya Malo ija akufunika Ku Blantyre so tiuzeni machitidwe ake
Njomba waonjo ni moreee
The good one 🤣🤣🤣🤣utenda wakula mpaka mundu kumuyendeza waphazi🤣🤣🤣🤣
Mandota bwezani ndalama za ngongole🤣🤣🤣🤣
Big up Mandota kmano pliz pliz mwayazo nde ai zsiya kukoma sopano, macheza olowa m'bokosiwo ai Che Mandota
Adha angongolewo akungofunika khofi basi😂😂😂💔
Kumaona anthu owabwereka ndalama mphakana amulelemba kkkkk
Mandota you're the best wish to meet up with u bredah ulemu wenu mmwejo lafuzi yu tumachi
This is funny, anyani mpaka kutenga fridge
Unabwera kuzakhala receive ur flowers while u r alive❤
Mlelemba is a legend, big chemandota mwayatsa moto pa Mw,
😂😂😂mandota bwezani ngongole😂 koma episode iyi nde yandiwaza🔥🔥
Kkkkk munalowa mu libokosi kkkkkkk
Umakwana tinakusowani ife kwabasi mwabwela kuzakhala
Mandota amakwana ngat la 40.
Eish Mandota usazafe uzangophululuka phrrrrrrruuuuuhh🤣😂😂😂
Koma ma Maili, mpakana duu Bokosi la maliro nkhwapa ku Bakila a Bambo kikiki. Ayi mukutha.
Sanakhalepo wabwino🤣🙌
😭😭😭😭Rip azibambo tipume kkkkkk
This is very awesome! Mlelemba n Che Mandota more faya
U guys muli mwala heavy mumativesa kukoma
Iweyo ndi more 🤣🤪💯 mandota umakwana
Nice one with your manager that's a great act🔥🔥🔥 Taphunzirako as well
You are number one che mandota since I started watching you eish non stop laughing 😂😂😂😂
Good concept 👍 big up to all performers,,, it has been sounding beautiful from the start..... Keep on coming with other teaching , advising, warning n entertaining ideas just like this 🔥🔥🔥
Mukafa muziti bushiri,,, zadara zooo kupanga act izozo muzifusa azanu ku Nigeria ana opusa kwambili
Koma mulogeni, malonjewo ndiyetu
100% creativity
Zikuchitikadi zimenezi kkkkkk keep it up
Ma maili ndi nkazi mbambande coz kukhara ndi mamuna ngat mandota eeeh ndi minyama yayikulu😂🤣
@ChisomoNgoma-sd9md
3 ай бұрын
🤣🤣
Kkkkkkkk iyi yokha guyz eeeeeee ndiye mwapha mkuchita kukhumba kuti ikanakhala ya ola lathunthu ndithu........Jabilu, Mulelemba, make Maili, Kankhani, and mwini wake Mandota muli super guyz respect
Palibe emwe amakharadi oipa akamwalira 😂😂😂😂🤣
Umu phangala zinakumana kikikiki eeeeh koma naweso Mandota kotenga ngongole kunasowa Chan? 🤣 🤣 🤣 Mulelemba siopanga naye Masewera 🤣🤣🤣
Ngongole kumaona kotenga 😂😂😂😂
Koma wangongole wake kukakamila eeeeee
Welcome back mamaili
Muleremba eeeeeeish I don't know how I can say big up u r so brilliant
The whole cast was on fire!!!
Abwana amatha malowo tafuna
Mpaka ndapanga comment kawili 😂🤣ur taking Malawi comedies at higher place 🙏
Kulowa mu libokozi uli nd moyo zisopweka🤣 well done👏👏
Ili bwino video
Eeeeh kuthawa ngongole mwati😂😂
Very nice to watch, proud of you mandota and crew
Eeeee koma anthu inuyo mumaganiza heavy mumatha
Big up bro Mandota.... You always make me laugh with your good comedies 😂😂😍😍
This is nice, keep up the good work,
Big up elder 💓
Kodi a inno build sakumapezeka ndi Malo ku Mulanje? Koma ndisaname umantha mandota keep it up
Zonse BHO, kma mayiwo action adzikhalako serious
Ati munene kuti ambuye anatikonda😂😂😂😂
Welcome back mandota, you made my night as you used to do masiku apitao 🤣🤣🤣🤣🤣
@yohanejosephkamanga7934
Жыл бұрын
You are best comedian here in Malawi big up mandota and crew without you gyz Malawi is nothing
Mlelemba ndi G.O.A.T
Wow!!!malowo akufunika..BT
Komaliza wakamela akuonetsa zala
I can't stop laughing. This is nice
Ndiwe doro ndipo suzantheka ndinthu 🤣
Kkkkkkkk😿😂😂😂😂😂mumatha gyz
Mandota umakwana mubokosi eti
Mumakwana ...mudabwera kudzakhala inuwoo✌️🤣😂😂😂
Apa ndiye panakumana mabig oziwa acting
💗💗💗💗💗🇲🇼🔥🔥🔥🔥🔥 more fire mandota squad... I loves you
Akut usapange zimenezo koma mulelemba kkkkkkk
😂😂😂😂😂 koma guys mujatha acting
Koma amandiye mwabwera ndi ina yachilendo more fire taikonda
Mmmmmm zili bwino koma zonamidzila kufazi zikundiopsa
Mandota waumapo kuthawa ngongole kkkkk