Mwana wa dzaka 13 wagwidwa ndi ng'ona kudzera mu matsenga

Пікірлер: 47

  • @mollymtawanga9952
    @mollymtawanga99527 ай бұрын

    Ali mu njira by Great Angels may his soul rest in peace .Pepani akubanja

  • @user-kq9gz3jh1m
    @user-kq9gz3jh1m4 ай бұрын

    Okhala akumtundu malomopanga zoti ayikoke khaki kuti tikafike paradise akuziwapodi kathu

  • @louiskk100
    @louiskk1007 ай бұрын

    You are doing a good job, koma muzitsitsako background song. #Phokoso kwambiri#

  • @user-ob1of8nd7k
    @user-ob1of8nd7k7 ай бұрын

    Ambuye muwapatse anthu akufa chiusiro chosatha ndipo kuwala kosatha kuwalitse maso wano ause ndi ntendere...amem

  • @hortenciosamuelofessi-qo9ty
    @hortenciosamuelofessi-qo9ty7 ай бұрын

    Pepani wofedwa pepani mzimu wa malemu uwuse mutendere AMEN

  • @joegibsonzulu2599
    @joegibsonzulu25992 ай бұрын

    Ndangoyiona kumene nkhani yomvetsa chisoniyi.Mzimu wa mnyamata ameneyu upitilile kuusa ndi mtendere. Pepani akubanja.

  • @user-ol3un7vv8b
    @user-ol3un7vv8b7 ай бұрын

    Si matsenga ayi ingakhale kuti yamupititsa ku Malo ake amene imakhala

  • @QuisitoAugustoNthewa
    @QuisitoAugustoNthewa3 ай бұрын

    Bamboyu ndi mfiti. Akudziwapo kanthu.

  • @pioireneuvictorpio1391
    @pioireneuvictorpio13917 ай бұрын

    Zosakhara buinoi Mzimu wake uwuse muntendere .zinazo musiireni mulungu muini zonse

  • @BenedictChikaoneka
    @BenedictChikaoneka7 ай бұрын

    Palibe zamuwanthu apa. Aliyese amadziwa kut ng'ona ndichilombo. Ine SI wakumeneko koma nkhaniyi ikudzinena yokha palibepo ufiti apa. Ifa yowawa ndithu ndipo zandikhudza .Mulungu amuyang'anire

  • @bilimonmazon4114
    @bilimonmazon41147 ай бұрын

    Abambowa awa andiyankhira mwa mzeru kwambil. Everything osamangoti zamuwanthu kod bwanji sitifuna kuvomereza

  • @user-kq9gz3jh1m
    @user-kq9gz3jh1m4 ай бұрын

    Ambuye akufungatileni nonse anamfedwa

  • @Charlieelieq
    @Charlieelieq7 ай бұрын

    Sizawathu nthawi basi inakwana munthu aliyense Mulungu adamulembera zithu zitatu 3 .chayamba kubadwa, 2 kukhala ndimoyo,chachitatu 3imfa

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn7 ай бұрын

    😭😭😭😭 pepani abale imfa iyi simayiwalika ,nafe zinationekera 2022 yi mpaka lero ,

  • @LUCKYM4787
    @LUCKYM47877 ай бұрын

    Sadness 😢

  • @mordecaikachale2497
    @mordecaikachale24977 ай бұрын

    Pepani pepani imfa zotelezi zimakhumudwisa kwa anthu osala komaso chiopsezo chifukwa anthu amaopa kuchita zinthu zikafika potere

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj7 ай бұрын

    Komano osathamangisa kuti zamasenga chifukwa ndavamo kuti ming'ona irimo menemo

  • @sharifujoe7633
    @sharifujoe76336 ай бұрын

    Da guy in water he know what is going on?

  • @hethermvula4156
    @hethermvula41567 ай бұрын

    Next time low the volume of background song

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    7 ай бұрын

    Thanks for information

  • @user-nf9zh1os4f
    @user-nf9zh1os4f7 ай бұрын

    Zachisoni kwambili

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo7 ай бұрын

    A Govate ulemu wanu ntchito mumaigwira tikuonera nao kuno ku malawi 🇲🇼

  • @user-ul5wx6kb4f
    @user-ul5wx6kb4f7 ай бұрын

    Sizoona khani yachisoni kumasekelera ngati ya ukwati bambo inuyo mwandikwisa mwachita chimo😭😭😭

  • @user-ul5wx6kb4f
    @user-ul5wx6kb4f7 ай бұрын

    bambo awa akuti sizamuwathuwa akuziwapo kathu

  • @PatriciaMkwenda-xc4mh
    @PatriciaMkwenda-xc4mh7 ай бұрын

    Zosakhala bwino koma pepani anafedwa mwana muzimu wake owuusa mtendere

  • @alinafesalima5597
    @alinafesalima55977 ай бұрын

    Bambo awa akuti sizamwawathuwa akuziwapo kanthu za ifa ya mwana ameneyu ndithu

  • @JOSEPHYSHAWA-vh9jd
    @JOSEPHYSHAWA-vh9jd7 ай бұрын

    Sory anamfedwa nonse. Zosayenda ndithu nzimu wake uwuse mumtendele

  • @user-ou7ug9lq8i
    @user-ou7ug9lq8i7 ай бұрын

    Bambo uyu akuziwapo kanthu ndinthu mwinaso ndi yemwe wapeleka mwana ndinthu mulungu odziwa kulanga walange onse agwira ntchito pa mwana

  • @andresakambewa7103
    @andresakambewa71037 ай бұрын

    aaa zosakhala zandivetsa chisoni

  • @user-bw7oc4ht5p
    @user-bw7oc4ht5p7 ай бұрын

    Pepani anamalira nonse😭😭😭

  • @user-ul5wx6kb4f
    @user-ul5wx6kb4f7 ай бұрын

    bambowa akuti sizamuwathuwa akutanthauza kuti Chan akuziwapo kathu chifukwa khani yachisoni kumasekelera ngati ya ukwati koma kulakwa 😭😭😭😭😭💔💔

  • @Joy-zx3lv

    @Joy-zx3lv

    7 ай бұрын

    Inesotu ndikudabwa nawo ndy paja poti amati khondo nd anasi

  • @user-hp8du2lx3z
    @user-hp8du2lx3z7 ай бұрын

    Zovuta mmm

  • @HalisonPhiri-jf7gr
    @HalisonPhiri-jf7gr7 ай бұрын

    😢

  • @justinjason7262
    @justinjason72627 ай бұрын

    Zosakhala bwino pepani akubanja komanso a BS channel potidziwitsa

  • @NaduMbewe-zz6iw
    @NaduMbewe-zz6iw7 ай бұрын

    Zosakhala bwino

  • @user-ju8qf1li9j
    @user-ju8qf1li9j7 ай бұрын

    Pepani pepani

  • @DhfdFufd
    @DhfdFufd7 ай бұрын

    Pepani

  • @user-lg6ym4hz3w
    @user-lg6ym4hz3w7 ай бұрын

    Koma abale zovutatu izi

  • @liki-likiladies---lilongwe6963
    @liki-likiladies---lilongwe69637 ай бұрын

    Mudzi uliwonse umakhala ndimunthu ofunika panthawi yake

  • @user-hs5xv6bk2f
    @user-hs5xv6bk2f7 ай бұрын

    Pepani kwambiri chonde nyimbo muzisisako ndithu kuti mau azimveka

  • @balancosemanalckgovate8464

    @balancosemanalckgovate8464

    7 ай бұрын

    OK , zanveka , zikomo kwambiri

  • @user-ye8os3ze2u
    @user-ye8os3ze2u7 ай бұрын

    Zomvetsa chisoni ndithu 😭😭😭😭😭😭😭

  • @chifunirogoliat4630

    @chifunirogoliat4630

    7 ай бұрын

    Mwini mbumbayo wandikaikisa

  • @user-rz3eb9ri7k
    @user-rz3eb9ri7k7 ай бұрын

    Ifaikutenga ana an,gono pepan kwambiri mzimu wake uunse muthendere😭😭

  • @pioireneuvictorpio1391
    @pioireneuvictorpio13917 ай бұрын

    Zosakhara buinoi Mzimu wake uwuse muntendere .zinazo musiireni mulungu muini zonse

  • @ChrissyKazinga-jd8dx

    @ChrissyKazinga-jd8dx

    7 ай бұрын

    Abale bambowa anena mwazelu tisamagoti zamasenga ai mulungu ifa anaivomeleza bwanji timakaika tonse tizafa ndithu

Келесі