MFUMUKAZI COMEDY SERIES..08/05/24..Flora Suya's👉+265883106798 strictly for business purposes only.
Жүктеу.....
Пікірлер: 95
@user-vl5on2lj8bАй бұрын
Lululuuuuu Moto Moto moto kuti buuuuu ntchito ndiyosayamba chifukwa ndikuona mbali inayi danken ndi achisime Pali kukhulana mbali inayi chisime ndi nkadzi wake Pali kufunsana mbali inayi padera kubwalo ndi namoyo palibenso xoonoera macomedy akunja mfumu nkadzi tirinayo buuuuuuu ❤❤❤❤❤. Nankha kubwera kwa masamba pakhomo lamfumu zitha bwanji ? Nankha giring'anthe kokatenga Maninjala nankha farai mankhwala uyiwalisa kokatenga Maninjala anapedza?
@user-ns1lc4tw3bАй бұрын
Padela my guy.... Ati simunaoneko mzungu 😂😂😂
@gilbertkumlinde-id9ncАй бұрын
Frora suya and the whole team, great work!!!
@KumbukaniChalundaАй бұрын
Izo ndi za pa mtundu wanu 😂😂😂😂😂 wandipangira chiyani iwe 😂😂😂😂baibulo makati😂😂😂😂😂
@pybenmbewe8462Ай бұрын
Very interesting comedy 😂😂😂 keep it up guys 👍
@chifundokambakaeraАй бұрын
Akazawo ndakazawo basi namoyo pola moto
@SurprisedDriftwood-ef3lc
Ай бұрын
24:31 atayisa nthawi Namoyo
@kaiimbansofwa9154Ай бұрын
I would love to have the songs in this drama. Where and how can i access them.
@harrisonmkandawire1510Ай бұрын
Ndaluza ndi bayern ndionere izii😂😂
@user-ns4oy9rb1gАй бұрын
Loud and clear,Padera ameneyo
@bilalisipikini8061Ай бұрын
I'm first view and like ❤🎉
@OliveaMapangaАй бұрын
Apadela banja lakoma kwambili mwanva ,zoti nsima ispa ndakaika 😂😂😂😂😂
@alinafekadango2596Ай бұрын
Afumukazi kulakhura kwambanji😂😂😂😂 mpaka pantundu pa......🤭🤭🤭
@Mamaza-tr6ziАй бұрын
Panotu masamba abwela kkkkk
@DONNEXKhama-bk1gyАй бұрын
Kkkkk kma banja LA giling'ande iiii khan ya masamba mpka konseko kkk
@BethsiderTavares-ug4svАй бұрын
I watch this soap because if the Angolan therapeutic drums. Very soothing and calming in a way. African drums beats rhythm is really connected and the same.
@user-ql2rk3nq5mАй бұрын
Kamba wa chabambo alipobe🤣🤣
@kondwanienockАй бұрын
Komatu upindi eeee😂😂
@maliyusuf4629Ай бұрын
Padela musitheko ka t shirt next mfumukazi aaaa😅
@HastingsChilimaАй бұрын
Apa anakumana onkhaokha amfumu kazi ndamunaowa mmmmm aiboo
@macjames3611Ай бұрын
Padera, ati simunamuoneko mzungu😅😅😅😅
@Chrissiefadwick-cu4seАй бұрын
namoyo akuchedwesa pakufunika compazet
@user-ql2rk3nq5mАй бұрын
Kma banja lapangolini😂😂😂
@OliveaMapangaАй бұрын
Amfumukazi ndi banja lawo woyeeeeee 😂😂😂😂😂
@LevisonMaluluАй бұрын
I like this production of flora suya
@CollinsLinguАй бұрын
😂😂😂 mwachidule I have got not money Mr pangolin original kkkkkkkk
Пікірлер: 95
Lululuuuuu Moto Moto moto kuti buuuuu ntchito ndiyosayamba chifukwa ndikuona mbali inayi danken ndi achisime Pali kukhulana mbali inayi chisime ndi nkadzi wake Pali kufunsana mbali inayi padera kubwalo ndi namoyo palibenso xoonoera macomedy akunja mfumu nkadzi tirinayo buuuuuuu ❤❤❤❤❤. Nankha kubwera kwa masamba pakhomo lamfumu zitha bwanji ? Nankha giring'anthe kokatenga Maninjala nankha farai mankhwala uyiwalisa kokatenga Maninjala anapedza?
Padela my guy.... Ati simunaoneko mzungu 😂😂😂
Frora suya and the whole team, great work!!!
Izo ndi za pa mtundu wanu 😂😂😂😂😂 wandipangira chiyani iwe 😂😂😂😂baibulo makati😂😂😂😂😂
Very interesting comedy 😂😂😂 keep it up guys 👍
Akazawo ndakazawo basi namoyo pola moto
@SurprisedDriftwood-ef3lc
Ай бұрын
24:31 atayisa nthawi Namoyo
I would love to have the songs in this drama. Where and how can i access them.
Ndaluza ndi bayern ndionere izii😂😂
Loud and clear,Padera ameneyo
I'm first view and like ❤🎉
Apadela banja lakoma kwambili mwanva ,zoti nsima ispa ndakaika 😂😂😂😂😂
Afumukazi kulakhura kwambanji😂😂😂😂 mpaka pantundu pa......🤭🤭🤭
Panotu masamba abwela kkkkk
Kkkkk kma banja LA giling'ande iiii khan ya masamba mpka konseko kkk
I watch this soap because if the Angolan therapeutic drums. Very soothing and calming in a way. African drums beats rhythm is really connected and the same.
Kamba wa chabambo alipobe🤣🤣
Komatu upindi eeee😂😂
Padela musitheko ka t shirt next mfumukazi aaaa😅
Apa anakumana onkhaokha amfumu kazi ndamunaowa mmmmm aiboo
Padera, ati simunamuoneko mzungu😅😅😅😅
namoyo akuchedwesa pakufunika compazet
Kma banja lapangolini😂😂😂
Amfumukazi ndi banja lawo woyeeeeee 😂😂😂😂😂
I like this production of flora suya
😂😂😂 mwachidule I have got not money Mr pangolin original kkkkkkkk
Km banja la mfumu kazi lilibe mtendere 😂😂
@user-ob1of8nd7k
Ай бұрын
Kkkkkkkkkk
@peterchikwakwa8476
Ай бұрын
Kikikiki
Koma namoyo mpaka kwa mfumu mmmmmm 🙌🙌
Pangolin wakalipatu😂
Kodi Agiling'ande ubulutu chani 😂 Namoyo ikoke nkhan Apadera akutaisa nthaw 😅 Mr & Mrs Giling'ane always mapokoso eeeeshhh
Kodi palibe Malaya omwe angawakwane apadela?
Mfumukaz ndi giling'ande mumakwana❤ pitilizani mumatinvesa phalombe kuno ku Capetown
Giling'ande and Mfumukazi mmatimvetsa kukoma I love you all Can't wait for next episode this coming Wednesday
😂😂koma namoyo
I love watching this again and again
Ai mkazi padera anasiya yekha banja zake anatola akueneleka alipire namoyo😂😂
Yap mzungu padex wayiponda mfadah😂😂😂😂😂
Mr shoprite busy kukoza radio 📻 kkkk
Ndikubwela konko next year wanna be part of this team, watching from cape town 😂😂😂😂😂 the original Pangolin
Kkkkkk anamoyo mufera zayeneake bwanji
Namoyo usaimve
😂😂😂😂😂😂 padela
😂😂😂😂 banja la angiling'andeli iiiiii lowondesatu
tili pano nthawi zonse😀
Uwona ngat kuchipindako ine sindimalowako😂😂😂
Kom giling'ande ndi amfumukazi nthawi zonse kumangokangana 😅😅
koma falaii ndi manager wake 😂😂😂😂😂😂😂😂
Koma madandu aNamoyo sitidawamalize kuwamveratu😊
Mwati maliro😅
Namoyo ndi one
Ati zimenezo zapa mtundu panu😂😂
Tiyeni tiyeni
😂😂😂😂😂Namoyo koma ndaseka
Padera uli shap kkkkk ulumbira bwanj kut satana mmozi waboza iwe kkkkkkkkk😂😂😂😂
Mpaka kuwafumu
Giling'ande ufuna umusamuse mfumu
Afumu kazi ulemu alibe ndamunawo
Next pls
Malilo osamutola amatha plus padela
Kkkkk koma man padela apo nde mwandijailatu 😂😂😂😂 isaaah
Agiling'ande ??? Weee mayi kikkkkkkkkkk
Pena pake camera simuendetse bwino
😂😂😂😂abiti nanyoni
Padela akazi ako unawadyesa chan😅😅
😂😂😂😂Eeeh Kom Mr shop rite 2025❤❤❤❤
Mai padela 😂😂😂😂😂mr padela
Koma guys nkhani ya masamba mpaka konseko a aaah Ayi mikaka imadyedwa
😂😂😂😂 km na moyo
Pangolin is pakachana
Namoyo zamvuta
Mumakwana
Koma padera louder and clear 😂😂
Namoyo umatimvesa kukoma
Eee nanyoni ndimoto
Kkkkkkk
😂😂😂😂😂😂 farai
Shop nde yatha 😂😂mwayeratu
Great performance
Kubwalo kuzavutatu
Namoyo phuma,nkazi amakaonekela?
Padera oyeeee
Koma pangolin asa nzako mbila???
😂😂😂😂😂Shop right ikusunthad??? 🤣🤣🤣🤣🤣
❤
Zapatundupanu😂😂😂
Giling,ande amantha
😂😂😂😂😂
a.ve got not money 😂😂😂😂😂😂 giring.ande umakwana
🤣🤣 km namoy
Giling'ande more 🔥 auzeni chilungamo amvumu mkhazi
Mfumukazi kumukana namiyo kk
😂😂😂😂
😂😂😂😂😂