MFUMUKAZI COMEDY SERIES..03/07/24..Flora Suya's👉+265883106798 strictly for business purposes only.
Жүктеу.....
Пікірлер: 124
@RonaldSaee5 күн бұрын
Zilibwino zd koma tamusowa gututu ndi Jami ❤
@TwawikeMwenelupembe-my4bs5 күн бұрын
13 Minutes Only,Why????
@FaithNgwalidi-hn8di5 күн бұрын
😮😮lero ndekakafupitu aaaaa
@user-zl1xz9kt5s2 күн бұрын
Anovahiwa! mtokuuzanitu! 🤣🤣🤣 this Novahiwa guy is so funny 🤣🤣 Manager Molosoni ndi kazitape kazitule, nthera kuwiri him self 🤣🤣 Giling'ande mphuma 2 much 🤣🤣
@EmmanuelBenjamin-p2y4 сағат бұрын
Watching from s a Durban zilibwino kwambili
@richardmuswavinda17415 күн бұрын
Watching from East London
@EmmanuelBenjamin-p2y4 сағат бұрын
Watching from S A Durban
@bernadettechoma5 күн бұрын
Lero ndalawira. Second to watch,💃💃💃💃💃💃💃
@user-qw2vo4xh4q3 күн бұрын
Mfumukazi ma plan anu ndiotani kodi 😂😂😂😂😊
@MichaelmapezaPhiri5 күн бұрын
Koma mfumukazi mwatiwonjeza,mpaka love is bland😂😂😂😂
@StephanoPaul-xv1ek5 күн бұрын
Lero lafupika kwambiri asaaa
@cassimyusuf6683
4 күн бұрын
Koma ku times apanga post ya full
@MaxwellKwenda4 күн бұрын
Watching from South Africa Delmas MPUMALANGA Province
@tepalameck95083 күн бұрын
osamalowelela za anthu omwe adyana kalibwasa kkkkk
Пікірлер: 124
Zilibwino zd koma tamusowa gututu ndi Jami ❤
13 Minutes Only,Why????
😮😮lero ndekakafupitu aaaaa
Anovahiwa! mtokuuzanitu! 🤣🤣🤣 this Novahiwa guy is so funny 🤣🤣 Manager Molosoni ndi kazitape kazitule, nthera kuwiri him self 🤣🤣 Giling'ande mphuma 2 much 🤣🤣
Watching from s a Durban zilibwino kwambili
Watching from East London
Watching from S A Durban
Lero ndalawira. Second to watch,💃💃💃💃💃💃💃
Mfumukazi ma plan anu ndiotani kodi 😂😂😂😂😊
Koma mfumukazi mwatiwonjeza,mpaka love is bland😂😂😂😂
Lero lafupika kwambiri asaaa
@cassimyusuf6683
4 күн бұрын
Koma ku times apanga post ya full
Watching from South Africa Delmas MPUMALANGA Province
osamalowelela za anthu omwe adyana kalibwasa kkkkk
Kkk am wishing you all the best
I'm already here for you guys❤
Mvahiwa aziona next kkkkkk😅
Komatu guys mukuyesetsa , love u❤
😂😂😂😂😂kwende kwamawo
That was a short one , anyway job well done 👏👏👏👏
Mmmmh mwayamba kubatu 13 minutes only 😂😂
Kufupika choncho bwanji 😂😂😂😂😂 aaaah
love you guys from America 🤣
Kafupika bwanji Gaye's mmmmm musatero
Mercy ndimakukonda❤
Koma ndi sewero kapena zenizeni 😂
Namoyo makani akut sindinathawe🤣🤣🤣🤣
Yafupika kwambili
Watching from Zambia
Mmmmmmm koma nde mwayamba kufupikisa
Wabwelesa character yamu dyangu Namoyo 🤣🤣🤣🤣
Vahiwayo muteme teme wakuonjedxa,,,naye Solomon kujijirika maboza ngat zimayi chimutu
Koma nde yafupikaditu
Km mushopritemu muli katundu?km kumpeza mwiniwache mmene amazipopelamo 😂😂😂😂
Ngati mwatopa ingosiyani
Taineneni yaifupiyo kkkkk
Kkkkkk kama fumukaz 😂😂😂
Please Madam Flora Suya onjezerani nthawi asaa mwationjeza mpakana 13 minutes
@baskatenis2014
5 күн бұрын
I think chifukwa Cha mwambo wamaliro a soja
Watching from 🇳🇱 Holland Netherlands
Koma Namoyo ndi Mai Padera aphana sure
Live from Ukraine
@user-zm9nl8zn2b
4 күн бұрын
Whch side ukraine
I'm here for Joshua
Next please 😂
Am the first one na lero
Love is Bland ..... mfumukazi akhale madam A English
13 minutes ngati nyimbo
Muzisamalira nthawe please
Koma manager shop yake imeneyi ndiye amalandila zingati pamwezi?😂
Zili bho kwabasi ❤
I like the name Nova😂
Lelo mwafupikitsa
Moto moto ma gyz nonse mumatiwaza koma lkumafupika nde kozani
Live from Afghanistan 🇦🇫
😂😂😂😂mr maliro project yanji yopanda cement
😂😂😂😂😂😂😂sosangalasa zedzi
2 short,and where is the mother to padera?
That is true today is too short
Lero mwatinamizatu ma minutes akewa
I like Mai Padera s behavior
Namoyo iweyo suopa
😂😂😂koma zilikotu
Mfumuksxi m wamuyankha bwino mvahiwa mumakwana paufumukaxi
Mwationjeza 13 basi mwapanga zozikonda
Yalero yafupikatu 😅😅😅😅
Kodi madam Frola msuya,movie ya season of a life ija ndingayipeze bwanji?
From Mozambique
Mfumukazi mwayankha bwino akapasule
Short time 😂😂
Yatalikabwanji week yamawa
Next please
Mvahiwa chidodo
13 minutes is enough why u reduce a time to 18 to 13 minutes?
Love is bulandi
Koma ndiye yachepaditu
Why 13mins
Lero yafupikadi bwanji
Mumatimvesa kukoma guys km mukuonjeza kufupikitsako
Watching 👀 From S.A Johannesburg Crosby
Lelo mwatibela nthawi
Km kafupika zilibwino
Km solomoni mmmm sulibwino ayi mmmm
10 minutes yokha basi aaah
Ukali❤
Nova amusanza katundu odyaidya ndiiithu
😂😂😂😂😂😂😂Mr Maliro project ilikuti?
Koma vahiwa😂😂😂😂😂😂
Zikuti bwanji kodi
❤ zilibhooo
Lero ndy lalifupitu 13 minutes??
From Pakistan
Guys mulibhoo kwambili
Charia ya jando 😅😅😅
Why today is to short
Zakusimba sopano
Sewero mwatopa nalo eti 13minutes
why short video,komaso yikuwoneka kuti yayambila panjila, and please improve image quality
@user-ql2rk3nq5m
4 күн бұрын
Vahiwa anakoza❤😂
Avahiwa avahiwa ok
Nofolobamani🤣🤣
Aaaaaa 13m nde zichani
Zayambikatu kunooooo
Guys namoyo tsazateka