Kwachema ndi mayi Shokoshoko. Waying'alula yamwana😂😂😂😂😂😂😂
@WonderfulFish-ru1wi2 ай бұрын
Gan your are good husband, umatha ku defender mkazi 😂😂
@jackbello21702 ай бұрын
❤🎉 mumakwanila inuyo team yonse
@HassanElias-wy2du2 ай бұрын
A prophet akufuna popempherapo kkkkkkkkkkkk
@lemanissa11252 ай бұрын
Mmmmm ndachedwa ine guys but I love you guys ❤️❤️❤️
@user-el3yo9sf2s2 ай бұрын
Mumatha inuyo keep it up
@user-rh1jw8hg7d2 ай бұрын
Achuma ndpo. Ali ndi chipongwe😂
@stevenkapanda63622 ай бұрын
Am first to Watch ❤
@user-lx8ow6ek6k2 ай бұрын
😂😂😂 mercy nthaw yako tsopano thamangitse queen 😂
@user-oo7gp9mc7j2 ай бұрын
Kmano Mai shokoshoko ndimaonekedwe ao ANGAKHALE voice yao mm part yomwe munawapasayo ai simawakhala asithilen ndthu asakhaleso mai ovuta coz ndiooneka bwino serious
@YusufMaganga2 ай бұрын
Koma ma banja amachitika pa mudzi wa mdyangu😂😂😂😂 eeeeee .kumango pasilana basi😂😂😂
@dannymangawa7511
2 ай бұрын
Chimpwirikiti chake ku mpanda uwu chiri ngati ngati chamu filimu ya landlady Anabanda mmwambamo kapena kuti Lameck Lameck maganyu adzakupha, chikabudula!! 😢
Пікірлер: 126
Koma Mercy is funny!!! ayayyaayaya kumeneku kujiyilira ndewu? hahahahahaha She just made my day
Koma Mercy nd nkhan zina kuchemelera ndewu kumeneku 😂😂😂😂 nkhawano ikupita kwa Queen zithana bwanj nd Mercy Mdyangu nd 🔥
Cicilia❤ ukhale nzanga iweyo.umandinvesa kukoma iweyo mayi shokoshoko
Kkkkkkkkkk mayi shokoshoko mumatha, mwa ing'alula, zatheka zofuna za mwana wa m'kango.
Best comedy ever❤🎉
Mercy and queen more fire 🔥🔥🔥 this is so interesting , job well done guys 👏👏👏👏😂😂😂😂
Me wait wait day Gan azaziwe kuti mwana siwake hiya todikila
Mudzamufuna Pastor Mulelemba kumpaladizo kkkk
Palibe chitsisi pa dziko laposi,mwana wa nkango wakodwera❤
Haha ati Military Mercy ikulandila motani hahaha best comedy series in Malawi now trending.
Kkkkk chokani pa khomo pa Sasoka madolo ❤
Koma iyi ndiyeyayaka mototu 😂😂😂 mercy alandile alendo
😂😂😂abro mlelemba ati ambuye anapanga bwanj ntchalitchi😂😂😂😂eish makwana ❤
😂😂😂 km mayi shokoshokoo
Mulelemba kwake ndikusokoneza basi😂😂😂
Kodi mercy yoo MA bum short apanda pake woo bwanji ndi mendo youma yooo mumuuze azivalako bwino aaaa
@VictoriaNyirenda
2 ай бұрын
😂 ndi sewerotu ili 😂
@user-uh6jg2ni4d
2 ай бұрын
Kkkkkkkkk ndipo inu @@VictoriaNyirenda
@fredabasi-vw5fv
2 ай бұрын
Koma part yomwe amatenga Mercy angavale molongosoka?
Mleremba ndiwotopesa koma eeeh 😂😂😂
Munyanyiwa ndi personal favorite
Gosto muito de vocês ❣️ kuini e Messi vocês são top
😂😂😂😂koma mercy umakwana kuchemelela ndewu kumeneko kkkk
I love it
Mwana WA mkango kubwera poyera tsopano😅😅😅😅
Waying,arura Mrs chokochoko kkkkkkk 🎉
Kwachema ndi mayi Shokoshoko. Waying'alula yamwana😂😂😂😂😂😂😂
Gan your are good husband, umatha ku defender mkazi 😂😂
❤🎉 mumakwanila inuyo team yonse
A prophet akufuna popempherapo kkkkkkkkkkkk
Mmmmm ndachedwa ine guys but I love you guys ❤️❤️❤️
Mumatha inuyo keep it up
Achuma ndpo. Ali ndi chipongwe😂
Am first to Watch ❤
😂😂😂 mercy nthaw yako tsopano thamangitse queen 😂
Kmano Mai shokoshoko ndimaonekedwe ao ANGAKHALE voice yao mm part yomwe munawapasayo ai simawakhala asithilen ndthu asakhaleso mai ovuta coz ndiooneka bwino serious
Koma ma banja amachitika pa mudzi wa mdyangu😂😂😂😂 eeeeee .kumango pasilana basi😂😂😂
@dannymangawa7511
2 ай бұрын
Chimpwirikiti chake ku mpanda uwu chiri ngati ngati chamu filimu ya landlady Anabanda mmwambamo kapena kuti Lameck Lameck maganyu adzakupha, chikabudula!! 😢
Queen ndi katundu🥰🥰🥰
Kmtu mayi shokoshoko ndimakina oyankhula eeee mwamdiposa
Munthu wa mulungu mlelemba😂😂
Ati music man🤣
Koma makwangwala awiri pa polo lamagetsilo nde munawakondatu...mix nkhunda ziwiri Zija
@LucasBetiasseJairosse
2 ай бұрын
mr charles mukutukwanatu sanena choncho amati phaulo kkkkk
@peterbakuwo1249
2 ай бұрын
Polo la magetsi 🌟👍
@LucasBetiasseJairosse
2 ай бұрын
@@peterbakuwo1249 bola mr peter kkkk
Queen akumpha iwe
More fire mabomba mumakwana
Well done guys
Number 7 here💃💃💃💃
Nice
Friday likuchedwa ndithu military mercy alandila alendo motani😂😂😂😂
Kodi nanuso ma movie anuwa sakulola download bwanji aaaah
May shokoshoko aying'alura😂
Km mumatisiya ikutiwadzaa tu ❤❤❤😂😂😂
Kkkkkk hehedee uluuuuu
pena ngati yizingopitilila😂🙌
Beautiful
Achokochoko ndi mwana wamkango mwana ndiwandani .koma achokochoko ndiwawo chifukwa akhala ndi queen kwanthawi
iiiiiiii mercy 😂😂😂😂😂
Mnyanyiwa wabwerano😂😂
Number one guys
Zili bho guys ipatseni 🔥 🔥 🔥 🔥
munyanyiwa 🤣🤣 sazasith km
Mamamaaaaa queen kudoderana uona mbwaza
Koma a chumawo akanasinthako system yojamajamayo ikuziziritsa zinthu aaaaaa
Chuma iwe ndi one...
qeen zadapo
0:33 Mayi shokoshoko osamaphyatima chocho 😅😅😅😅
Mlelemba umandisangalatsa
Nep man umatha😂
Muli nyatwa guys ❤
Aaaaa biggie 🙏 kkkkk km chiphwanya ayiboh
Nepman ndi dolo 😅
Mayi shokoshoko 😩😩😩😩😩😩mwampereka mphwanu 😰😰😰😰
A mercy pezani mamuna
Mai Shokoshoko ma hope anga
Chumaaaa🎉
😂😂😂😂😂 koma mercy
Salute guyz
Mumakwana guys ❤❤❤❤
Koma zabeba koma mercy ❤❤❤❤
Mukuyitha nomse pitilizani
😂😂😂🔥🔥
Koma Mai shoshoko mumatha ❤
Mumakwana maguyz
Pamene nthawi ikuti 02:31 ndiangati tikuonerabe? Gani game Yamulakwira uku
Munyanyiwa ndi Dolo
Mulelemba amatha
💞😘😘😘
Kkkk😂😂😂😂😂
My tchokochoko mumandimvesa kukoma
Kod adyangu alikut?
Km muli anthu obhebhetsa kwambiri
Quin be careful adzakupha mayi Shokoshoko😂
Kukula movutika kumayambisa nkhaza
😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂
Good job
❤ all mdyangu guys
Kkkk
Nkhondo ndi anazi
Thanks all for watching!! Without u this channel is useless. We ❤❤❤❤❤uuuuuu alllllllll
87 here
Tionele apa
Masve guys
Kķkkk km murelemb n palibe