Koma ndiye Umphawi ndivuto lalikulu, Komanso Kamuzu anatipusitsa Azimayi achimalawi ndiotengeka ndi zaziii Anthu akuwawona awawika mumavuto ndiiwowo, koma nkuapasa so sapoti kuti apitilize kugwetsa Malawi mpaka tione K20000 note zomvetsa chisoni pa Mangochi apo.
@FaisonLukiyoАй бұрын
Auawo sagwira ntchito
@user-fm8ed7eo3iАй бұрын
Mmmmmmmm moto wake uti poti akufuna kuti awadyere ndalama zomwe akubanzo, ndi wa kumangochinso
@user-ti2ct8ts8dАй бұрын
Zitsiru kuvinila chitsilu chinzawo
@user-ww9rj2wx8dАй бұрын
Zakutumbo basi kusowa zochitatu uku hiyaaaa
@user-pt8wb4vw6rАй бұрын
Mcp mito kuti buuuu❤❤❤
@usumanidaudiАй бұрын
Inuso a hanifa mwayamba kujama ya mcp anthu atatuwo paka kwawonesa apa muzawona apm pa 12 pano
@BonganiCharles-ju4tyАй бұрын
Azimayi angododoloka zili zonse maka achiyao eeeee mavuto kufika kunyumba kungo ona poto wauma
@AleksaWilliams-qc6cnАй бұрын
Mmmh shame on you mangochi women😢
@salimmkumakumakitombi-yc7pwАй бұрын
Ayao a 2 sim awa not a 1 sim .muyao wa original angamasapote idzi
@user-dh8ml4bv4wАй бұрын
Azimayi Ali ndiivuto kutengeka zaziiii
@APOSTLEBJ-tc5fpАй бұрын
Ayao alibe nzeru alibe kaya chifukwa cha umbuli wosapita ku school kaya.mcp idapha ndi kuwocha nyumba za anthu aku mangochi ku malindi kwa amoto pofuna kumupha chipembere koma lero ayao ndikumasapota mcp zoona?
@user-gj4li2gc8oАй бұрын
Mzakhumudwa even mavoti a 2025 a chakwera azawinanso kwambilinso
@user-gj4li2gc8oАй бұрын
Pa Malawi mpovuta ena akulila ena avotela yemweyo chakwera
@BerlindaJetel
Ай бұрын
Kkkk etietii zomvesa chisoni
@LovelyBlini-cu3iuАй бұрын
Ena ndi obwela MCP ndiyochenjera apasidwa ma 5pin adyeleni
@alexsumani6823Ай бұрын
Azimayi amenewa Ali ndi ma banja ndithu koma, zitsilu za wanthu
Пікірлер: 71
Azimai saganiza zamavuto alipo ndife opusa kwabasi
Ko ma njala imeneyi kumakhala busy ndichakweraso😂😂😂😂😂 Amalswi si muli serious 😂😂😂
Mahule. Osowa amuna awa mwina awonedwe usilu watundu wanji uwu
Ndi ufulu wawo basi asiyeni tikumana 2025
Mabadzi Apita apa 😅😅😅
Asamangodya zomba bwanji.
Wadya omweu chakwera 😊
Chuma chomadya ena, osauka busy ku vina. aaaaa zomvetsa chisoni kwambili
Umbuli kumalawi sudzatha anthu ngati akuyimbira kuvinira mutsogoleri wopanda tsogolo mukuganiza ziko lingasinthe mbuli ndizambiri kumalawi
Dyera.... Ma K2000 basi😂😂😂
Moto wake mukunenao ndiuti wayakao
Nkazi wayine never kupita kusongano wa MCP
Kukhala mkaziwanga ndimve kuti analikomweko kukamuchapa makofi kunyumba uku mkupusa zedi .
Zaziiii chimenechiso ndi chipani kusasa Mai mukatero mukagone ndinjala
Azimai ovetsa chisoni kwambili mmm koma
Nambo kwereko
Anakawatenga kulilongwe kukawavinisa ku mangochi... Amangochi sangapange manyi ngati awa
Zisilu agalu chosecho mwagona ndi njala mulibe sugar kufela 2 pin mahule
Koma umphawi siwabwino , anthu akuvutika ndikukwera mitengo yazinthu ,ndikumamchemelera.ana awo sukulu ikulepheleka kulipila ,ayi awa popeza anawo amakhala kowenza mnsomba.
Aaaaa mangichi
Mbuzi za dzimayi
Koma ndiye Umphawi ndivuto lalikulu, Komanso Kamuzu anatipusitsa Azimayi achimalawi ndiotengeka ndi zaziii Anthu akuwawona awawika mumavuto ndiiwowo, koma nkuapasa so sapoti kuti apitilize kugwetsa Malawi mpaka tione K20000 note zomvetsa chisoni pa Mangochi apo.
Auawo sagwira ntchito
Mmmmmmmm moto wake uti poti akufuna kuti awadyere ndalama zomwe akubanzo, ndi wa kumangochinso
Zitsiru kuvinila chitsilu chinzawo
Zakutumbo basi kusowa zochitatu uku hiyaaaa
Mcp mito kuti buuuu❤❤❤
Inuso a hanifa mwayamba kujama ya mcp anthu atatuwo paka kwawonesa apa muzawona apm pa 12 pano
Azimayi angododoloka zili zonse maka achiyao eeeee mavuto kufika kunyumba kungo ona poto wauma
Mmmh shame on you mangochi women😢
Ayao a 2 sim awa not a 1 sim .muyao wa original angamasapote idzi
Azimayi Ali ndiivuto kutengeka zaziiii
Ayao alibe nzeru alibe kaya chifukwa cha umbuli wosapita ku school kaya.mcp idapha ndi kuwocha nyumba za anthu aku mangochi ku malindi kwa amoto pofuna kumupha chipembere koma lero ayao ndikumasapota mcp zoona?
Mzakhumudwa even mavoti a 2025 a chakwera azawinanso kwambilinso
Pa Malawi mpovuta ena akulila ena avotela yemweyo chakwera
@BerlindaJetel
Ай бұрын
Kkkk etietii zomvesa chisoni
Ena ndi obwela MCP ndiyochenjera apasidwa ma 5pin adyeleni
Azimayi amenewa Ali ndi ma banja ndithu koma, zitsilu za wanthu
Zisilu za anthu ndipo ndakhumudwa kwambili😊
Komatu azimayi polani moto kwanuko zikuyenda anzanthu ayi zikomo 💔💔💔
Zitsiru kuvinira mbava ngati akudya mmakwawo
Umbuli.kudzapita.kusukulu.ndizimene.zikufuta
Mangochi nsimungawine MCP loko patamvuta bwanji mungodzita anthuwo akuyimba chimene akamvotele akuchidziwa siyaguletu awa adzingokudyelani k5000 pin chitsango akudziwa mamvuto akomana nawo zaka 4 ulamulilo wa MCP ndi UTM mwadxudza dzedi iiiiiii
Ndiye yayaka moto di. Mangochi ndi Mangochi yo anthu ake amenewo kkkkkkkkkkkk Zomvetsa chisoni.
Inu mangochi sipanga zachibwana akungofuna ndaramayo basi osati angavotere mcp asa chakwera ndi fiti
Abeleni abwera okha oskana ndalama
Who is here with me
30 people only
Anthu ovesa chisoni kuvinila mbava chosecho akugona ndi njala koma umphawi ndi wa chabe 2 pini basi anga gule chani sugar yemwe sikwanaso echeee
@BerlindaJetel
Ай бұрын
zitsiru zaanthu
Koma zakuti sugar akugulitsa K6000 akuziziwa koma ayaowa?
@buttbutt6690
Ай бұрын
Iweyo opuza😅😅
Waiting
Wakupasani ma k2000 wakulakwilani mudya matsiku angat? Paja azimayi mmatipwetekesa kwambiri
Zisiru za azimayi izi shame on you mukhawura ndi njara Chaka chake ndi chino
Awawo sakumvutika Sali Malawi momomwemo amzimai opanda zochita taweremukani muchangamuke kusaphuzira sikwabwino ndithu
Koma ndichifukwa chiyani abale ....anthu tikuvutika koma kumachemelela chakwera ....Kaya ndi umbuli koma mavuto alipo .....ma 5000 akupasaniwo akubweleselani mavuto osati masewela ......
@user-lf6qf2tw5o
Ай бұрын
Uchisiru
Koma azima ndichani mukuchita zoonadi kusowa kwanu chochita pochoka pompo mimbamo njala yokhayokha
Palibe ogwetsa MCP maka chilima akaima payekha nankhumwa payekha basi DPP yathapo azimai alindi mphamvu awuza azimuna awo kuti bambo sapoteni tambala wakuda
Azimai okhaokha bwa?
@Pangolinimw
Ай бұрын
anyamata safuna sauzilu
Zisilu ndithu
Kunali mnsonkhano?
Anthu ache atatuwa.asogoleli,alipowa akuchiononga,chipani cha kamuzuchi.bolatso, mwini wache chifukwa iyeyo,safuna amalawi azigona ndi njala olo adzigula sugar K5000
@eliffagondewe8214
Ай бұрын
Shame on you azimayi kwanuko zikuyenda eeti💔💔
@user-nn9bg3ve3g
Ай бұрын
A Malawi anthu womvetsa chisoni kwambiri amagulidwa ndi 2000
@HarrisonMwanga-xy4sc
Ай бұрын
@@eliffagondewe8214 azimai kwathu kuno anasiya,anachangamuka,bola anganati azibvina ili UDF olo afford.
@HarrisonMwanga-xy4sc
Ай бұрын
@@user-nn9bg3ve3g kkkkkkkkk malawi ziko lolemela kwambili,koma olemela ache ndi azitsogoleli.ku kalonga sugar K6000 pomwe ena akuthamangila andale omweo akuononga malawiwo'kumaomba manja.malawi,poyamba anali the home❤️of Africa lero shame
@IdaCMwale
Ай бұрын
Ndi ufulu wawo azimai asiyeni