Mayankho Azinsisi Zobisika za DRIEMO katakwe Yemwe wagwesa Namadingo

MBIRI YA WOYIMBA WOTCHEDWA DRIEMO
Driemo ndi woyimba yemwe wagwedeza ndi nyimbo zake zingapo mchaka chino chokha mdziko muno.
Atatulutsa nyimbo yake ya Weniweni kumayambiliro kwa chaka chino,
iyeyu sanasiyire pomwepo koma mkudzatulutsa nyimbo ina yotchedwa Compensation mmwezi wa July 2022.

Пікірлер: 60

  • @emmanuelchimombo6091
    @emmanuelchimombo6091 Жыл бұрын

    The young man is talented, yes, but let's not compare him with others....

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 Жыл бұрын

    This guy is very talented so there is no need to compare him with other musicians, Luso ili ndi lake lake bc, Big up mfwethu.

  • @asumanibizimana8095
    @asumanibizimana8095 Жыл бұрын

    Kodi mumasowa zochita eti osangokamba za amene mufunayo bwanji Namadingo osamamuyesezera ndi anthu wamba

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z4 ай бұрын

    Mayankho azinsinsiwo ndiati nanga popeza simunafotokoze

  • @josephmumba8277
    @josephmumba8277 Жыл бұрын

    Katakwe pa music. Man u are the best. 🎊🎊🎊🎊🎊👏🏾

  • @lithembajujwana5577
    @lithembajujwana5577 Жыл бұрын

    Mwana wa kwathu wa ku TC ukutiimilira keep it up Allah anakupatsa talent there is no need kuti muzipangadi compare ndi ena,🔥🔥🔥

  • @pilipiliallie8573

    @pilipiliallie8573

    Жыл бұрын

    Damzy komatu anamadingowo ndiakuti ameneyondiyebola gwaladi

  • @realsu7816
    @realsu7816 Жыл бұрын

    Zopanga compare'zi sizoona coz aliyense Ali ndi Luso lake losiyana ndi nzake komanso mbali. Let Driemo be & other artists be also.

  • @noahtsamdoka1172
    @noahtsamdoka1172 Жыл бұрын

    nyamatayu amatha kwabax ndiwaluso yachibadwidwe mwachidule ndingoti Khama lipindula NDI nthawi yavomeleza kukhala ku mvaliyake so mwene use ur time & talent wisely chofunika kusamala nthawi Bax pamene zikuyenda gwilitsanibe ntchito nzeruzo to kip moving 4ward but don't let ferm to let u down kip on giving us good staff & we should kip on supporting U too 🔥🔥🔥🔥

  • @phirimoses575
    @phirimoses575 Жыл бұрын

    Zowona ife kuno amen tili maico ene Rik zambia Mfanawo akuvek boh kuno Zambia

  • @khalifakandiona5990
    @khalifakandiona5990 Жыл бұрын

    Inde luso Ali nalo mwanayu koma Namabingo ndi Legend..............

  • @innocentfelexsteven2060
    @innocentfelexsteven2060 Жыл бұрын

    Mwazina mwa nyimbo mwatchulazi munayiwalaposo Be there mfanayu Ali Hot 🔥🔥🔥🔥 ineyo ngt myamata nzanga ndikumuyamikira kwambir ndipo apitilize kupusha

  • @brendadumisan2526
    @brendadumisan2526 Жыл бұрын

    Let God be God everyone has got on talent munthu ukatchuka sikuti wina aziti wagwesa wina namadingo Ali kuchikamwini Kaye Ku Zambia komanso so ife pakadali pano tikadamvera driemo yemweyo akutimvesa kukoma ife kumalawi kuno

  • @directorchris555
    @directorchris555 Жыл бұрын

    Mukamati wagwetsa Namadingo mulakwitsa uyu simungafananitse ndi Namadingo that man he has money and he is doing music for business

  • @shukulanalick57

    @shukulanalick57

    Жыл бұрын

    I͎w͎e͎y͎o͎ p͎a͎l͎i͎b͎e͎ c͎h͎o͎m͎w͎e͎ u͎k͎u͎d͎z͎i͎w͎a͎ m͎e͎s͎a͎ a͎k͎u͎w͎o͎n͎a͎ a͎d͎z͎a͎n͎y͎e͎n͎g͎o͎ k͎u͎t͎i͎ m͎w͎a͎n͎a͎y͎u͎ a͎l͎i͎ b͎h͎o͎ k͎w͎a͎m͎b͎i͎r͎i͎ m͎a͎s͎h͎a͎a͎l͎l͎a͎h͎

  • @BlessingTengule-nc9uv
    @BlessingTengule-nc9uv Жыл бұрын

    Keep it up

  • @amongenamu9372
    @amongenamu9372 Жыл бұрын

    To be speaking honestly without offending anyone who thinks differently from my point of view but looking seriously into this matter,, Doctor Namadingo a legend and don't compare him with this Dremio or whatever you call him! Compare him with Med C, Waxy, And many others but not Namadingo.. Please don't mislead people here.. 😬 😀 😀 😀

  • @patrickmacheso5062

    @patrickmacheso5062

    Жыл бұрын

    Namadingo is another level

  • @asumanibizimana8095

    @asumanibizimana8095

    Жыл бұрын

    Thanks for saying this dear hahahha

  • @oscarmsafibandah6311
    @oscarmsafibandah6311 Жыл бұрын

    The secret is behind his unique talent osati otherwise

  • @ShabilJames
    @ShabilJames9 ай бұрын

    ❤❤❤ nice

  • @chrissjunior8342
    @chrissjunior8342 Жыл бұрын

    Driemo amatha" ndpo ali ndi luso nfana uja

  • @Razarusmbavachakwera
    @Razarusmbavachakwera Жыл бұрын

    Namadingo ndi 1 ndipo sumungamuphatikize ndimatope kapenakuti manyaka omwe mukuwanenawo

  • @Razarusmbavachakwera
    @Razarusmbavachakwera Жыл бұрын

    Namadingo 8 million viewers on his KZread so wena hanifa what are u talking about

  • @chippiephiri4505
    @chippiephiri4505 Жыл бұрын

    Chilungamo chake ndichokuti sakutchuka ulele ayi...... There is secret behind his talent.....

  • @patrickmacheso5062

    @patrickmacheso5062

    Жыл бұрын

    Which secret? tell us to know more.

  • @richardbanda5172

    @richardbanda5172

    Жыл бұрын

    Awa ndiye maganizo achimalawi omwe ndimawadziwa kuganizilana zoyipa basi

  • @bernardmwale5501

    @bernardmwale5501

    Жыл бұрын

    The secret is the guy is very talented. Let's just appreciate the guy . It's not easy to be who he is now

  • @patrickmacheso5062

    @patrickmacheso5062

    Жыл бұрын

    I get you guys, let's support this guy, he's putting up our National flag.

  • @lonnythom6944

    @lonnythom6944

    Жыл бұрын

    I agree with you

  • @astrofreeimkush2189
    @astrofreeimkush2189 Жыл бұрын

    Namadingo is legend for long time how do u resemble with upcoming artist

  • @innocentfelexsteven2060
    @innocentfelexsteven2060 Жыл бұрын

    inde namadingu amatha komano mwanayuso wadza Hot kumayamika nzanu akachita bwino bwanji ma jealous anthu akuda kikkkkk

  • @frankstephano4860
    @frankstephano4860 Жыл бұрын

    Amakwanira ameneyo ndpo wafikapo.....

  • @fathemamussah631
    @fathemamussah631 Жыл бұрын

    Namadingo ndiye ndaniso ananyo amalawi akagwere

  • @user-lj7lm6ly7z
    @user-lj7lm6ly7z4 ай бұрын

    Musiyenu driemo azipanga zake mwantendere ,mutu wankhaniwo ndizimene mukufotokoza sizikugwilizana mchifukwa ndakufusani kuti mayankho azinsinsiwo ndiatii popeza simunatiuze?

  • @emmanuelkalera6547
    @emmanuelkalera6547 Жыл бұрын

    Iyi ndi misala ndithu ,Namadingo ndi star wawa not zomwe mkuyankhulazi ai

  • @patricknamatumbo7591
    @patricknamatumbo7591 Жыл бұрын

    Hie

  • @chippiephiri4505
    @chippiephiri4505 Жыл бұрын

    Hanifa umatha

  • @wisdomthomson8436
    @wisdomthomson8436 Жыл бұрын

    Kod simungangokambako zenizeni?

  • @marianjeleka900
    @marianjeleka900 Жыл бұрын

    Muli nd nthawi

  • @lawrencekasawala2736
    @lawrencekasawala2736 Жыл бұрын

    🔥

  • @jonathanmandah294
    @jonathanmandah294 Жыл бұрын

    DRiemo

  • @micksonsaid5997
    @micksonsaid5997 Жыл бұрын

    Driemo amatha

  • @angelmalawiofficial9172
    @angelmalawiofficial9172 Жыл бұрын

    Afana oooyitha

  • @ririvilla1423
    @ririvilla1423 Жыл бұрын

    Namadingo amadzimva ananyoza Malawi akhale ku Zambia komweko

  • @mariocj9419
    @mariocj9419 Жыл бұрын

    🇲🇿

  • @eunicekansungwi7843
    @eunicekansungwi7843 Жыл бұрын

    Namadingo nde ndan😂😂😂

  • @kelitakanjila8678
    @kelitakanjila8678 Жыл бұрын

    Amatha koma

  • @adamogamah
    @adamogamah Жыл бұрын

    Komatu

  • @seth7778
    @seth7778 Жыл бұрын

    So that has made you say, he has dethrone namadingo? 😒 Anxaa

  • @EBBOY-nl7gr
    @EBBOY-nl7gr Жыл бұрын

    Namadingo ndi ndani komanso ndi wakutiko

  • @alinafekoloviko3438

    @alinafekoloviko3438

    Жыл бұрын

    Driemo Nde uti? Uja amaimba zokonda amayi? Amaimbira Kuti?

  • @amidumussa3814
    @amidumussa3814 Жыл бұрын

    Mukusowa zotumiza eti??

  • @directorchris555

    @directorchris555

    Жыл бұрын

    Kusowana zokamba

  • @wemmahjohn7492

    @wemmahjohn7492

    Жыл бұрын

    Koma Driemo ndi more keep up dear

  • @bridgetmithi140
    @bridgetmithi140 Жыл бұрын

    😂😂😂😂

Келесі