Manganya Si M'thira Kuwiri? | Zioneleni Nokha

#chilima #manganya #utm #chakwera #mcp #malawi #trending #viral

Пікірлер: 53

  • @hawardmkandawire673
    @hawardmkandawire673Ай бұрын

    Amasulidwe ndithu a Bon kalindo ndi a kamplepo ❤❤❤ They are not guilty for speaking out their mind

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano😅🎉😅❤

  • @WhiteRichard-cw2fo
    @WhiteRichard-cw2foАй бұрын

    Ndizonadi zimene mukunenezo osamanga Muthu chifukwa chonyoza Muthu ayi zimenezo sizoona wina aliyese Ali ndiufulu bon kalindo atuluke sinakwane khani imeneyo

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4iАй бұрын

    Osewo ndima nkhruku chilungamo akuchiziwa kuva wava chakwela kuti boni kalindo ndi akaluwa amangidwa whay osatuluka nkulesa zomanga athu akuziwa kuti amila koma pasana pakuwoneka pangatalile pafupike tikufuna chilungamo chieoneke ndipo ovumbulusa zose ndi mulungu yekhatu basi

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4scАй бұрын

    Ndiye,zimene timaziwa amalawi zimenezo,kutha mau ku ma Media koma action ataaaa iya.khondo,ukatibulidwa,popo nawe bwezela.osati,tidzaonana ndiwe galu aaaa amalawi tiyeni tisiye matha tionetseni action.

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2egАй бұрын

    Komaso chakwera adziyamika chilima chifukwa samadziwa kusetela tissue amkangoziwa kusetela dzidina ndi dzisononkho Lero akumupha what is that😢😢😢

  • @NACNAC-fg5yd

    @NACNAC-fg5yd

    Ай бұрын

    Social media osaitenga ngati yakwanu. Sipotukwanila apa, muzafunsidwa nazo izi

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vnАй бұрын

    Michael Usi ndi mthira kuwiri komanso angathe kukhala nawo mu gulu lokupha Chilima

  • @LindaKapito
    @LindaKapitoАй бұрын

    Manganya nd wa mcp kuyambila kalekale

  • @user-tw2zf7bj3e
    @user-tw2zf7bj3eАй бұрын

    Ndidzandale ndithu simukunama

  • @macmsiska2937
    @macmsiska2937Ай бұрын

    Wanandi wakukana kuti Usi akhare vice president even mpoto's said that 😂😂

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vxАй бұрын

    Michael usi ndi thira kuwiri and akukondwera ndi imfa ya chilima

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWiliАй бұрын

    Uyuyu munthu muyiwareni ku utm

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865Ай бұрын

    Mnafiki uyu bombocrat

  • @user-gd7xm7xr9v
    @user-gd7xm7xr9vАй бұрын

    Kodi a Hot 265 Inu ndinu Yani? Mukungobwereza nkhani za anzanu. You repeat zimene TV zina zaulutsa. Kungomatula.

  • @VitumbikoChinoko-n7x
    @VitumbikoChinoko-n7xАй бұрын

    Amasulidwe abon kalindo alibe mlandu

  • @MadalitsoShuga-no8ix
    @MadalitsoShuga-no8ixАй бұрын

    Ndiomwewa adzipani 9 omwe akati akutichotsa ku iguputo kukatisiya ku kenani kkk ndie leloli akuti chani

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395Ай бұрын

    I am not sure there is no collaration unless you say the flight data recorder which come from Mozambique, have been put in that interviews

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1qАй бұрын

    Manganya ndi oipa mmesa iyeyo anali vice president wa chilima Koma bwanji sanalankhulepo za infa ya chilima thila kuwiri uyu

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda8711Ай бұрын

    Aaaa nde MCP ineneyi ulamulilo wa chipani chimodzi 2025 ikawina inuyotso simupedzaka pamenepo kumakambilana nkhani basi mudzibwela kumudzi tidzizalima fodya basi

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Check just my opinion the ok from mjfim

  • @SaviourTepu
    @SaviourTepuАй бұрын

    My mother Malawi

  • @OsmanMisolo
    @OsmanMisoloАй бұрын

    Gwakuba iyu.

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANIАй бұрын

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @JaneMoyo-ws2di
    @JaneMoyo-ws2diАй бұрын

    Zoopsya kwabasi, khoswe ali chilili pa mkhate.

  • @OsmanMisolo
    @OsmanMisoloАй бұрын

    Ndimthila kuwiridi zowona

  • @LindaKapito
    @LindaKapitoАй бұрын

    Akudziwana anthuwo zisakudwalitseni mutu

  • @EmaxGraceFanTV
    @EmaxGraceFanTVАй бұрын

    Aaaa

  • @user-rf4br1fv2z
    @user-rf4br1fv2zАй бұрын

    Kodi amalakhulila a kalindo ndizabwino tsiku ndi tsiku kunyoza anzao ndibwino kodi

  • @IssacMateyo

    @IssacMateyo

    Ай бұрын

    Big Mani sizabwino ayi ndipo akulu aja akufunika adzimangidwa amene uja alive khalidwe boni kalindo

  • @user-xf8xb2iq9i

    @user-xf8xb2iq9i

    Ай бұрын

    Kuyakhula kwabwanji kumene akalindo amatimenyera ufulu ife amalawi

  • @JafarAustin-zj6rj
    @JafarAustin-zj6rjАй бұрын

    Malawi is not personal property and you will not silent people use by arrested you achakwela

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bjАй бұрын

    Kwaine sindikuwonapo vuto naye ndi munthu palibe chomwe inu mungachite ngakhale atalowa mcp palibeso vuto

  • @EddieMoyo-wm2lm
    @EddieMoyo-wm2lmАй бұрын

    Kalindo saziwa ndale iyeyo amaziwa kutukwana munthu wa chochi ndiwosathandiza

  • @LeendaDeborah2005

    @LeendaDeborah2005

    Ай бұрын

    Ngati ali munthu osathandizatu nde mungozinyengapo. Vuto lake munthu amadana ndi anthu oima pa chilungamo nde timakunvetsani

  • @user-xs3pk1vp8i
    @user-xs3pk1vp8iАй бұрын

    Kalindo amangonyoza basi and anachita bwino kumumanga

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano😅🎉😅❤

  • @VitumbikoChinoko-n7x
    @VitumbikoChinoko-n7xАй бұрын

    Amasulidwe abon kalindo alibe mlandu

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano😅🎉😅❤

  • @VitumbikoChinoko-n7x
    @VitumbikoChinoko-n7xАй бұрын

    Amasulidwe abon kalindo alibe mlandu

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

  • @sikefaMoesaMoeza-kn2sn
    @sikefaMoesaMoeza-kn2snАй бұрын

    Mayikoio Wu's achoke popano

Келесі