God bless you brother Steve, there is greater life ahead
@idalisamalembo265
3 жыл бұрын
That’s true, Steve Spesho is a legend in making. God bless you too Brim Ngosi 🔥❤️🇲🇼
@brimngosi1533
3 жыл бұрын
@@idalisamalembo265 AMEN
@peterbanda54253 жыл бұрын
Ayi ndi mwana ozichepesa ukuchita bwino mulungu amakukweza
@johnsong10482 жыл бұрын
I feel bad for these guys Steve,Miracle and Israel Their mum died so early before she had something that her Children could relay on The way you we know These guys is far different the way they live But God will make a way
@victormulingo80464 ай бұрын
Naye akungomugulila chips 🍟 no drinks waganiza bwanji
@daudyusufu37503 жыл бұрын
The boy is very humble
@idalisamalembo265
3 жыл бұрын
Very very humble 🔥❤️🇲🇼
@patrickkamanga17333 жыл бұрын
you are such a humble man steve
@shiddyadhagrossman29983 жыл бұрын
😂😂😂😂 Wamupeza Asanaphodetu munakhala bwanji inu
@medsonchimwazamonkey-bayma97183 жыл бұрын
Malawi music TV you must prepare before you go to ask artist usamangozifila pa TV ayi Koma kumafusa mafuso ogwira mtima osati kumangolubwalubwa ayi
@tekogeneral2318
3 жыл бұрын
Kkkkk true
@blessingchimowa2354 Жыл бұрын
My boy
@mercinansongole52963 жыл бұрын
Guys please make sure you inform people before visiting them Azikhalako ready kut lero ndilandira alendo
Пікірлер: 37
God bless you brother Steve, there is greater life ahead
@idalisamalembo265
3 жыл бұрын
That’s true, Steve Spesho is a legend in making. God bless you too Brim Ngosi 🔥❤️🇲🇼
@brimngosi1533
3 жыл бұрын
@@idalisamalembo265 AMEN
Ayi ndi mwana ozichepesa ukuchita bwino mulungu amakukweza
I feel bad for these guys Steve,Miracle and Israel Their mum died so early before she had something that her Children could relay on The way you we know These guys is far different the way they live But God will make a way
Naye akungomugulila chips 🍟 no drinks waganiza bwanji
The boy is very humble
@idalisamalembo265
3 жыл бұрын
Very very humble 🔥❤️🇲🇼
you are such a humble man steve
😂😂😂😂 Wamupeza Asanaphodetu munakhala bwanji inu
Malawi music TV you must prepare before you go to ask artist usamangozifila pa TV ayi Koma kumafusa mafuso ogwira mtima osati kumangolubwalubwa ayi
@tekogeneral2318
3 жыл бұрын
Kkkkk true
My boy
Guys please make sure you inform people before visiting them Azikhalako ready kut lero ndilandira alendo
@gsmmalawi1741
3 жыл бұрын
This is behind the scene nde sitikozekela ayi
@deluxeanimation1957
3 жыл бұрын
Yeah ndibwino kumudziwitsa munthu kuti azikonzekeletse, nanga mpaka munthu kumpeza akugona
Kkkkk he is not already for this
Kkkkk koma a brz ndiko ku bedroom yanu emeneyo😝
@Mpesuwa
3 жыл бұрын
komatu ma upcoming artistswo mukanawaninkha chips olo chopanda salad...kikikiki
Kkkkk
Mafuso ake abale
Kkkkkkkkkkkkkkkkkk
Ganja is talking bra
Muzikozekeletsana Kaye kut munthu azikhala ready
@gracezulu6115
2 жыл бұрын
Ndipo inu eeee kkkk
iyeyu amagona kuchipinda kumenekuku kapena amangopangilako za music?
@unclepaulmw1506
3 жыл бұрын
Kkkkkkkkk mwatani kodi?
@peterkamtambe2741
3 жыл бұрын
@@unclepaulmw1506 ndati ndifunse ine chifukwa mnyamatayu amaoneka osamba bwino...
@marthakumwenda836
3 жыл бұрын
Kkkkk
@unclepaulmw1506
3 жыл бұрын
@@marthakumwenda836 mzanu ndi office yake yimeneyo kkkkkkkk
@elbeys783
3 жыл бұрын
Koma ngati amagona apopo nde mmm social media yonamiza
Uyoo asiye kumayendera ma musician cos sanali olimbisa oyimba apo akupasa nkhawa oyimba.. pls better to stop