LERO KWAGWANJI?17 May 2024

Пікірлер: 17

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m22 күн бұрын

    Sife zisilu chakwela musamanamizile nkhondo tazingobani nthawi yanu imeneyi ndi abale anu

  • @chrisschikozera7271

    @chrisschikozera7271

    20 күн бұрын

    Kunamizila chani kodi ?

  • @user-bt3qi1gt8b
    @user-bt3qi1gt8b22 күн бұрын

    Zoonadi nthawi zina zimanthandiza koma thawi zambili magotaya nthawi anthuwa Ndiye magothi mvuto lazosezi ndi bodza basi tigopeza njira yothana ndi bodza basi

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l18 күн бұрын

    Amwene zinthu zomwe zinali mu budge kale it is easy to go ahead

  • @owenskabazanechiumia3543
    @owenskabazanechiumia354322 күн бұрын

    Ineyo Mfundo zanu Achunga ndi anzanu Asewunda zandigwira Mtima kwambiri, ndikumvetsera bwino pano pa Randpark Ridge, Randburg RSA

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l18 күн бұрын

    Tanzania project ya fast train was on a track before COVID

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l21 күн бұрын

    Enock ndiwe galu wawononga chipani cha Afford, munthu wopanda nzeru... Ukufuna udindo basi not to fix Malawi

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w22 күн бұрын

    Bayana Chunga simukunama , kale kunali kusunga mwambo osati zapanozi. Atsogoleri ku Malawi kulibe.

  • @KENETHMAJASA-ud5ee
    @KENETHMAJASA-ud5ee20 күн бұрын

    MCP ndiye yaononga kwambiri, bola enawo

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l21 күн бұрын

    Chihana nfi Peter muthalika mose ndi galu Loma nyasi, ndifukwa chiyani chihana mu 2020 why did join tonse alliance

  • @DICKSONBanda-ic4mf
    @DICKSONBanda-ic4mf22 күн бұрын

    zonse zaveka bwino ndithu

  • @homeremedys3748
    @homeremedys374822 күн бұрын

    Finally, Born kalindo the DC walowa MCP, Viva malawi Viva

  • @user-nx7yz4qo8f

    @user-nx7yz4qo8f

    22 күн бұрын

    😂😂polopaganda ,pepani michira mochedwa

  • @DylesMtenje
    @DylesMtenje22 күн бұрын

    Chakwela ndi wakuba

  • @WanangwaMunde
    @WanangwaMunde22 күн бұрын

    Hy

  • @evelynmaliro1206
    @evelynmaliro120622 күн бұрын

    Mukunena zoona

  • @MisheckChinjala
    @MisheckChinjala22 күн бұрын

    From your RSA Cape Town Stellenbosch.... anyamata mwayakhula , Koma Ndine wa DPP ❤