Kuyakhula mosaopa Chakwera wamupha Chilima. Chifukwa cha udindo

Пікірлер: 185

  • @user-fm8ed7eo3i
    @user-fm8ed7eo3i7 күн бұрын

    Akulu eeee apa pa kanakhala kuti Pali anthu 10 ngati inu ayi dziko bwenzi likuyenda bwino. I like your style brother ❤

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem15 күн бұрын

    Manganya ndi mfiti yotheratu ndagwilizana nazo

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b7 күн бұрын

    Mizimu ya wonse omwe adawapha pa ngozi ya ndege ija iwanzunzedi anthu amenewa

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py15 күн бұрын

    Posatengera CHIPANI chilima adachita kuphedwa kumene achakwerawo akudziwa Koma pot CHOIPA chimakanidwa sangamvomere Koma MULUNGU akudziwa

  • @DorrahBanda

    @DorrahBanda

    7 күн бұрын

    Zoona

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os15 күн бұрын

    Mwandiyankhulira bwino kwambiri. Ama radio onse sakuthandiza a Malawi. Kulephera kunena chilungamo zoona??? Amalawi muzichangamuka please!!! Ku Church ko mumapemphera chani? Ama Wailesi simunathandize or pang'ono, ndipo tataya nanu chikhulupiliro ma Radio 📻 oyipa panokha.

  • @manfredzalirabetha2440

    @manfredzalirabetha2440

    6 күн бұрын

    Ma radio osathandiza a mmalawi muno bola limpopo basi iyaa

  • @user-be5fc3ed1i

    @user-be5fc3ed1i

    2 күн бұрын

    Bora Limpopo FM yoha basi komanso ndi imene inasegula maso amalawi kuti ndege yagwera kuchikanga komaso anthu amwalira shame mawayiesi oyima panokha Lero ndimasiya kalekae kunvera hot current.yanga ndi Limpopo FM, Bakili muluzi tv ndi Boooorn kalindo ndi okha amene akutiuza chiungamo

  • @MercyKachenje
    @MercyKachenje15 күн бұрын

    Mau amphavu awa vuto anthufe nsanje too Mulungu apitilize kitiululira zinsisi

  • @LamieTiger
    @LamieTiger15 күн бұрын

    Vuto ndilot athu ena akuikira kumbuyo athu afitiwa athu ot akudalira mitsokho yathu Kut antchedwe olemera mipando akupheranayo nditimisokho tathu toja deleri kuzolowela Moyo osagwira ntchito Moyo opatsidwa zaulele chakwera wayetsa Kuno Ku church Kut udzilandila chakhumi mabatile ako

  • @GiftKananji
    @GiftKananji15 күн бұрын

    But how manganya did this? he looks like a sheep but he is a bad person, here Boni Kalindo is being punished because of this man eish that's very sorry

  • @ThomasKaphwiti
    @ThomasKaphwiti12 күн бұрын

    Ndipo manganya siwakuno mayi ake ndi aku Zimbabwe muzikaona kuchenjera ngt akuba nkhuku😅😅

  • @samueljuma4452

    @samueljuma4452

    6 күн бұрын

    Kkkkkkk ngati akuba nkhuku???koma ndaseka

  • @ChimwemweBottomani-hc5ju
    @ChimwemweBottomani-hc5ju5 күн бұрын

    I was wondering how mr michael usi allow to bi a vice president as he was a vice president to late chilima😢😢 we was all.shocked to bi honest usi sanaganize bwino ...indeed they need to comfess ngati amakhulupiliradi Mulungu ....i salute you my brother n may u always bi protected

  • @PaulMinofu
    @PaulMinofu15 күн бұрын

    On point❤❤❤❤

  • @OsmanBakali-s5x
    @OsmanBakali-s5x7 күн бұрын

    💔💔💔💔mpaka pano ineyo ndmangoona ngati a CHILIMA alipo sanamwalire ai.. I will still missing him in my heart ❤️ forever 😭😭😭

  • @InnocentMlowoka-ew4lo
    @InnocentMlowoka-ew4lo15 күн бұрын

    Chilungamo kuwawa

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du7 күн бұрын

    Amene anapha chilima panya pake 😢😢😢

  • @cacksygustarf6260
    @cacksygustarf626014 күн бұрын

    Voice ya nzeru❤

  • @user-yo9rw8tr4s
    @user-yo9rw8tr4s15 күн бұрын

    Dosanama munthu Uyo walankhula mau wogwilika kwambile

  • @BensonChilundu
    @BensonChilundu7 күн бұрын

    Micheal Usi ndi munthu ozikonda kwambiri.zoona zake zaoneka zokha chifukwa iyeyu sakadalolera kukhala Vice President.Koma abale ndalama zovuta ndithu

  • @YusufuKaifa-fr4wt
    @YusufuKaifa-fr4wt7 күн бұрын

    ❤❤❤❤❤❤my point president chakwera out

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s14 күн бұрын

    Muli speech yamphavu ndipo boma ili Mulungu achite nanu

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano4733 күн бұрын

    Well spoken my brother we can't keep Quite on what happened in our National, we are still mourning all who died on that day ,it SAD.

  • @HameedahMasambuka
    @HameedahMasambuka15 күн бұрын

    Ndipo kukumangan inuyo. Ndizakhala numbar one kusonkha ndalama yokuombolelan mmmmmmm

  • @user-jn2oc3cn3q

    @user-jn2oc3cn3q

    7 күн бұрын

    Kkkk km support iyi

  • @user-be5fc3ed1i

    @user-be5fc3ed1i

    2 күн бұрын

    ​@@user-jn2oc3cn3qkkkkkkk kwachema

  • @user-be5fc3ed1i

    @user-be5fc3ed1i

    2 күн бұрын

    Chilungamo chiyende ngati madzi 😂😂😂

  • @ThomasKaphwiti
    @ThomasKaphwiti12 күн бұрын

    Ndipo zoona tatiyeni a Malawi tionetse mkwiyo wathu Maliro ndiye tinayika kwa tsalano tithane ndizigawengazi😢😢😢😢

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du7 күн бұрын

    Manganya ndi fiti panya pamake plus chakwera 😢😢

  • @MtokomaYohane
    @MtokomaYohane7 күн бұрын

    And is true chakwera akukhunzidwadi and i have more questions

  • @paulinekayuni1621
    @paulinekayuni16217 күн бұрын

    As for radio and tv extension I can agree I was expecting too for them kupangitsa conference yofusa mafuso representing people mafuso amene akufusa. Koma zinazo kaya

  • @Aisha-db6ds
    @Aisha-db6ds7 күн бұрын

    Iponden fadah 🎉

  • @LoveHawabwa
    @LoveHawabwa5 күн бұрын

    Inu mwayakhula mawu ife tikuwopa kuyakhulapo mwatilakhulira mulungu awakanthe kopotsa

  • @ibrahimalfred6539
    @ibrahimalfred653914 күн бұрын

    The power of massage and the power of prayer indeed

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire7 күн бұрын

    Sanayankhuleponso amangophwisa mkhutu wa udindo usi

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira970814 күн бұрын

    Mulungu akuona zonse,,, ndipo samagona tulo. 😭😭😭😭😭

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma7 күн бұрын

    Manganya mpando kumeneko sanjoya akachita chibwana mkwiyo wa Mulungu umukantha koopsa tikupempheratu magazi a Chilima aja ayankhula usazione ngati wachenjera

  • @FelisterNgwira-op7rr
    @FelisterNgwira-op7rr14 күн бұрын

    Deotoronomy 29 ; 29 verse the secret things belong unto the Lord our God: but those things which are revealed belong unto Us and to our children ever, that we we may do all the words of this law

  • @LovelyBlini-cu3iu
    @LovelyBlini-cu3iu15 күн бұрын

    Mau amphamvu

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati316615 күн бұрын

    Inu ndiye mwanena zoona brother mmmmmh ulemu wanu Inuyo shaaaa Ndamva nanu kukoma zedi❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @AmandaConstance-fx8cr
    @AmandaConstance-fx8cr15 күн бұрын

    Not all days are Sundays God is watching and may there souls rest in peace 🙏

  • @MichaelWilliamsNyirenda
    @MichaelWilliamsNyirendaКүн бұрын

    Powerful message Duuu may their souls rest in peace ✌️

  • @ackimChiumia
    @ackimChiumia9 күн бұрын

    U are talking sense

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma7 күн бұрын

    Koma izizi tu we are praying kuti Mulungu alange aliyense amene anatenga gao lokupha chilima pompano asadikile chiweluzo

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b15 күн бұрын

    So heartly broken dear

  • @ruthkundwe7448
    @ruthkundwe744812 күн бұрын

    Yesu anapelekedwa chifukwa cha ndalama yochepa,God have mercy

  • @mariamahamadu8402
    @mariamahamadu84027 күн бұрын

    Nawoso mayiko usi mbusi yamunthu kukonda ndalama kumeneko mpaka kulolela Kuti munthu ampedwe ndalama abale God bless you mukutidzegula mithu

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire7 күн бұрын

    Chi Michael usi manganya that why amuika pa mpando iyeyo kuthamanga kukakwera pa mpando pakamaso gwaaaaa manganya

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b15 күн бұрын

    It's true my brother that's sad

  • @GodisoneNoel
    @GodisoneNoel15 күн бұрын

    Zoona ❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-ml8lk9dr7t
    @user-ml8lk9dr7t2 күн бұрын

    Yes may God perform wonders that the truth must prevail

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto6 күн бұрын

    Osaopa osafooka tizafera mbendera yathu😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @MichaelWilliamsNyirenda
    @MichaelWilliamsNyirendaКүн бұрын

    Bakili muluzi tv yekha akalowa kumwamba bro kuyankhula mowonatu

  • @georgejere2922
    @georgejere292215 күн бұрын

    You will pay for it, what's wrong did our SKC do to you😭😭😭😭😭 the day will come 😢😢😢

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g15 күн бұрын

    manganiso anu ameneyo okay alibwino

  • @WellingtonHowahowa
    @WellingtonHowahowa7 күн бұрын

    Basi poti kulibe mulandu okupha ndimphezi ...mudiyeni chakwelayo azasowa omusumila

  • @user-er7ub4ug7y
    @user-er7ub4ug7y15 күн бұрын

    Osaopa osafooka tiime pa chilungmo dziko lino nditose ndopo mbendera yake ndiii🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼situkukuopami😢😢😢😢

  • @user-uv5rf4zt5q
    @user-uv5rf4zt5q23 сағат бұрын

    Chilima anaphedwa chifukwa cha jealousy eishiii Malawi will never change for better.

  • @FelixBoss-yn9pe
    @FelixBoss-yn9pe13 күн бұрын

    Enanu mudakangosiya kucommenter Ngati sizikukumvekelani bwino Ife nde tikumva kusekemela chipepeso chathu timachipeza kuzela kwaanthu amenewa chilima wathuuuu tizamfela

  • @user-hm9nc7lz6e
    @user-hm9nc7lz6e15 күн бұрын

    Zoonadi manganya ndi munthu oipa sanayakhulapo za imfa ya chilima

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js15 күн бұрын

    Ndi Ana omwe akudziwa

  • @user-fm8ed7eo3i
    @user-fm8ed7eo3i7 күн бұрын

    Zoona awa ndiye mau bro end I love you so much brother ❤🎉🎉

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika678412 күн бұрын

    Ambuye tipheleni Chakwera 😂😂😂😅😅😅

  • @Hellenistic109

    @Hellenistic109

    7 күн бұрын

    AMEN 🙏

  • @YamikanChirwa
    @YamikanChirwa11 күн бұрын

    Ndpo mabala akutiwaw

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e5 күн бұрын

    Ameni amen misonzi ya wanthu osalakwa simapita pachabe

  • @MirajiYusuf-vx5ux
    @MirajiYusuf-vx5ux15 күн бұрын

    Zoonadi brother ife tikulira ndithu esh infa ya chilima mmmm😢😢😢😢 mulungu 😢😢😢😢

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw15 күн бұрын

    Zoonadi inenso ndikusiwa cho cho

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b7 күн бұрын

    Komad manganya anatidabwitsatu palibe chimene anayankhula pa za imfa ya Chilima an angokhala pheeee ngt sizikunkhudza zombvetsa chisoni kwabasi Mulungu yekha ndamene akudziwa zonse

  • @Marymahendra
    @Marymahendra2 күн бұрын

    That’s true brother if it was khozi ya ndeka suit no trousers no shoes my

  • @samsonpadiwa9185
    @samsonpadiwa91853 күн бұрын

    Ndipo inu ka pangolin kamakhala chikwama mpaka kumugwira ndege ikulu ikulu osayipeza😂😂😂

  • @NoelLangwani
    @NoelLangwani7 күн бұрын

    Ndipoh zoonadi mwalakhula bwino ndithu broz man

  • @NaomieBanda-t6g
    @NaomieBanda-t6g7 күн бұрын

    Ndava chisoni

  • @PraiseCedar
    @PraiseCedar15 күн бұрын

    Unali bho koyamba kuja koma zalowa nsanje kwinako

  • @Trancy-xt4py
    @Trancy-xt4py15 күн бұрын

    Atola khani afikapodi apasidwat ndalama kut akhale chete ndipo mulungu agwesere mulili mkabudura mwawo Kuti zokozera zawo zinyenyeke kuti AZIWE phamvu ndiukulu WANU mulungu wanga chilimat sadakwake ,osalakwq kwambili ndiuyu chakwerayi

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i2 күн бұрын

    Manganya umuziwe yesu ndiukachenjede wakoyo kupusa kwako Michael usi Mzimu wa chilima ukusate ndikukantha kwambiri

  • @AjudantFombe
    @AjudantFombe11 күн бұрын

    Mudziwa bwanji chilungamoa Malawi ambili ndi osaphuzila ndipovuta

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire7 күн бұрын

    Eyadi ndemweyooooo

  • @user-so7wg6ii5m
    @user-so7wg6ii5m2 күн бұрын

    Bambo inuo ambuye akutetezeni mwayankhura mau amphamvu kwambili ndipo mizimu yanthu amene anamwalira pangozi imeneija iwazuze achakwera komaso onse amene anatenga po gawo ambuye muchite nawo

  • @user-rk4ch1ly3z
    @user-rk4ch1ly3z6 күн бұрын

    Pokhapo pokakamila u president next term, munawonesa kuti chilima simumamufunila zabwino.mukayakha kwa jahjah.

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto6 күн бұрын

    Inu ndiye mwandilizaaaaa ineeeeeeeeee maliro awa ,A chilimaaaaaa inuuuuuuu😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @FelixBoss-yn9pe
    @FelixBoss-yn9pe13 күн бұрын

    Kkkkk mimba zilikhutchu Ngati ogulitsa tomato oola kkk Koma big man

  • @InnocentnMbale-zq8pk
    @InnocentnMbale-zq8pk15 күн бұрын

    Ndipo Inu eee ziko ili likupita kuti ndipo ine zundiwawa ndisaname ngati ndikufa ndife koma kumalawi anthu tili ndi mantha kwambiri

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du7 күн бұрын

    Amalawi ndi amantha size😢😢😢

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp7 күн бұрын

    Chichakwera chakupa galu wacha be chabe kupa andu osa lakwa chaka chamawa ndipa fup mtikumana mbusi simenesi achakwera 😢😢

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda589111 күн бұрын

    Kulankhula chilungamo mopanda kuopa

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i2 күн бұрын

    Tiyeni tisiye kumvera ma wayilesi akumalawi chifukwa wonse anaguidwa kale Bora Limpopo FM radio, Bakili muluzi tv ndi Boooorn kalindo ndi okha amene akutiuza chiungamo

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b7 күн бұрын

    Koma nde zoonadi ndithu watsala iyeo akuwona ngt sadzafa

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e5 күн бұрын

    Zimenezi amalawi onse akuziwa zimenezi koma akuopa kuyankhula chilungamo monga chimenecho Mulungu akuteteze kuti upitilize kutiya khulila ku Mtundu wathu..

  • @user-wl4nd7ic1s
    @user-wl4nd7ic1s15 күн бұрын

    ❤❤

  • @jamessheki4293
    @jamessheki42937 күн бұрын

    Iwe ndiye munthu, Malawi tulo anthu kutipusitsa chonchi,tingoyang'anila ngat nkhuku mkhola ikaphedwa imodzi zina zimangoyang'ana. Mmmmm

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe821415 күн бұрын

    Yes ambuye atithandize abale eesh💔💔so sad

  • @user-gi1gh9ry6h
    @user-gi1gh9ry6h14 күн бұрын

    Zoona anthu oyipa kwambiri magazi alimanji mwawo 😅😅😅

  • @AbnormalMk
    @AbnormalMk2 күн бұрын

    Nkhani ya Straight 200%

  • @user-rk4ch1ly3z
    @user-rk4ch1ly3z6 күн бұрын

    Iwe ndiye walasa!

  • @ChilangoNdalama
    @ChilangoNdalama12 күн бұрын

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona14 күн бұрын

    Bambo ndithu mwapeleka mitu akanakhala kuti amawelenga kapena kumvela ma media mwina akanaphuzira zina

  • @RaymondKaumba
    @RaymondKaumba7 күн бұрын

    Ufulu umeneu wa anthu a misala

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira970814 күн бұрын

    Ili ndi pemphero la Ana a Mulungu,, ndipo akuona ndi kumva msozi wa aliyense... Mudzalira nonse munatenga gawo pa imfa Ya anthu amenewa 😭😭😭😭

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime163215 күн бұрын

    Ndifiti Manganya mwana oyipa kwambiri chisilu chamunthu ichi galu kwabasi nkhankhankha uyuuuuuuuuuuu ndimapulani awo opusawo abvutika okha mitima mwawomo

  • @HamidavioletYassin
    @HamidavioletYassin7 күн бұрын

    Akuti pangolini imakhala chikwama koma mumayigwila kukanika kuyipeza ndege koma yayikulu ngati imeme ija eshiii malawi walila ndithu

  • @HopeSaka
    @HopeSaka15 күн бұрын

    Mwatilankhulila father 😢😢😢

  • @SebastianSauwa
    @SebastianSauwa11 күн бұрын

    Akuopa kumangidwa

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo7 күн бұрын

    Osawopa osatopa osafooka 💪🔥🔥🔥

  • @user-wl4nd7ic1s
    @user-wl4nd7ic1s15 күн бұрын

    🔥🔥🔥

  • @TressLuka
    @TressLuka14 күн бұрын

    Nkhaniyo ndiyonaaa kapena 😂

  • @manfredzalirabetha2440
    @manfredzalirabetha24406 күн бұрын

    Mpakana kumupha mzunu kamba ka mpando wa u president ngati kuti malawiyu ngwa amanu mukuona ngati mupitilizabe kulamulako?? Anyani agalu inu anthu oipa