KULIRA KWA A MALAWI - MUZAMULIRA BWANJI CHILIMA?

Ойын-сауық

KULIRA KWA A MALAWI
MUZAMULIRA BWANJI DR. SAULOS CHILIMA?

Пікірлер: 50

  • @patrickkusailemp3769
    @patrickkusailemp3769Ай бұрын

    Kungotchula mawu okhao oti malemu,,ndagwesa misonzi 😢😢😢R.I .P

  • @Shannie-uw4wm5fn8k
    @Shannie-uw4wm5fn8kАй бұрын

    Ndipo ineyo mmmm nayenda wapansi kukafika ku city center koz of this man nditsiku losaiwalika pamoyo wanga😊sleep well mr king man we shall forever remember you

  • @isaacbwanali4699
    @isaacbwanali4699Ай бұрын

    Ine aChilima ndidzawakumbikila chifukwa chakudzipereka kwao potumikila dziko- komanso potumikira Yehova pamoyo wao. Mzimu wao ndi ena onse omwe adatayika, pangozi iyi yandege iwuse mumtendere waYesu ❤🎉

  • @user-ql1fy2rc4t
    @user-ql1fy2rc4tАй бұрын

    Chitsime chija chinali chakuya now ic mmene madzi mulibemo chilima King of national unity

  • @user-bq5eu7xb8h
    @user-bq5eu7xb8hАй бұрын

    Anali munthu okonda kupephere koma anthu❤❤

  • @dysonfysonchifundo2284
    @dysonfysonchifundo2284Ай бұрын

    Tidzakumbukila potipangitsa kukhulupilila Munthu olakwika nkango uli pa mpando, koma mzimu wawo uwuse mu ntendele, kungodandaula Moyo wake wapita ngati mwanapiye eish

  • @samuelmanda6588
    @samuelmanda6588Ай бұрын

    Ndidzamukumbukira chifukwa cholimba mtima kuti dziko lino ndila wina aliyense, tikhale ndi chiyembekezo kuti zinthu zisintha ndipo tsogolo lathu ndi lowala tikakhala ndi masomphenya. Kudzichepetsa kunalu mwa akulu aja mmmmmmm ayi enafe titengeteko phunziro. Experience yawo pogwira ntchito ndi ma private sector he had results oriented mindset.

  • @dinganinedsontchongwe610
    @dinganinedsontchongwe610Ай бұрын

    Saulosi Chilima sitizamuiwala anali munthu amene anabwadwa munthu was mwayi munthu wokondweka country wide munthu wolimba mtima simple man no one like him

  • @ernestphiri5507
    @ernestphiri5507Ай бұрын

    Its a great loss to the nation he was a great man no wonder he was a threat to the leaders of Malawi RIP beloved leader

  • @LeendaDeborah2005
    @LeendaDeborah2005Ай бұрын

    Kwa ine he looked so brave nthawi ya campaign but I don’t know what happened to him when he got in power. Adangoyamba kukhala zii all of the sudden. I may have never liked him that much once he got in power koma ineyo ndikudana kwambiri ndi mtundu wa imfa yomwe yamutenga. Wafa imfa yosayembekezeleka ndipo yowawilatu. Ambuye mukatamandike

  • @user-ln4de7ke4j
    @user-ln4de7ke4jАй бұрын

    Chilima was a good man than the one who is in power

  • @glorynkhata1185
    @glorynkhata1185Ай бұрын

    Kungot wamwarira imfa yosakhala bwino koma kudziko ayi amaba kwambili chitukuko amapanga ku family kwake ndi ku ma party ndi amene amamudziwa za ubwino wake ine kulibe kungot mariro sitimasekerera RIP TO ALL CRASHED IN THAT BAD ACCIDENT

  • @MevisiWalani
    @MevisiWalaniАй бұрын

    Tizamukumbukila chilima chifukwa chakudekha kwake komaso kuopa Mulungu zachisoni wafa imfa yowawa imene dziko la Malawi silizayiwala

  • @DennmichSimb
    @DennmichSimbАй бұрын

    Mr Chilima was Genius man.The youth of Africa has lost the great leader.He had good visions for the country of Malawi.

  • @usumanidaudi
    @usumanidaudiАй бұрын

    Chirima anari munthu wabwino kwambiri ine ndikudandawura kwambiri 😢😢

  • @DavieMakwecha
    @DavieMakwechaАй бұрын

    Ndidzawakumbukira chifukwa sanadwale ena apanga naye njiru ndi nzeru zomwe anali nazo osati zambuli zili ku mcp ko akuuzeni tanthauzo ya democracy mchiwewa sizophana ngati nthawi ya kamuzu ayi sithani a mco ino ndi nthawi ina zosiilana za dziko izi

  • @JohnMbola-yp7fr
    @JohnMbola-yp7frАй бұрын

    We'll rimaid Mr chilima for everything

  • @GoodsonLindani-gf8pn
    @GoodsonLindani-gf8pnАй бұрын

    Nkhani yosakhala bwino ndiyamoyo wachokawo,koma pa nkhani yachitukuko sanachite chilichose mmalawi muno . RIP SKC.

  • @user-xg2ks9nw5q

    @user-xg2ks9nw5q

    Ай бұрын

    Palibe ku malawi angafane ndi chilima

  • @LindaKapito
    @LindaKapitoАй бұрын

    Mmmh kulila ndikulila ine ndikulila chifukwa chot nd moyo wachokawo,zinazo akudziwa mulungu koma rest in peace

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wtАй бұрын

    Ndimaonamo future bingu mwa saulosi

  • @SarahMusama-eu7wt
    @SarahMusama-eu7wtАй бұрын

    Taluza anthu anzeru awili saulosi and bingu

  • @RuthMazengera-yx8oh
    @RuthMazengera-yx8ohАй бұрын

    Ndizamukumbukila anali muthu olimba mtima wachikondi odekha mwa chilima munali chiyembekezo chaamalawife 😢😢

  • @georgephiri4181
    @georgephiri4181Ай бұрын

    Wayifeladi mbendela ya Malawi koma Chakwela ambuye amuwone

  • @PatrequeFanuelKaussiwa-nq9ou
    @PatrequeFanuelKaussiwa-nq9ouАй бұрын

    Mkulu ameneyi tidandaula kwambiri ngati munthu koma pa chitukuko anaika Malawi pa ma vuto polowetsa mcp mboma

  • @nkosikhonasiphiwemdlalose227
    @nkosikhonasiphiwemdlalose227Ай бұрын

    Ine siwandale ndipo kumalawi ndinachoka ndili wachichepele komano nkhani ya Chilima yandikhunza ndipo ndalira ndikulirabe kuona mmene afela atagwila colona manja Mulungu wa moyo tichitileni chifundo nkhondo iyiyi ndinu nokha mungaikwanitse palibe chinsisi panziko

  • @user-ol1hf7ru1v

    @user-ol1hf7ru1v

    Ай бұрын

    Amen 🙌

  • @user-ep6ro8uk6e
    @user-ep6ro8uk6eАй бұрын

    Zosayenda koma kunena mwachilungamo chilima ndamene anapeleka dziko lino mwadani kut anthu aziwona nyekhwe achinyamata akungokhala pano kusowa zochita zitchito kulibe

  • @henrychikuse1543
    @henrychikuse1543Ай бұрын

    Masiku omaliza ana amulungu adzakhala akuphedwa

  • @stevielee5404
    @stevielee5404Ай бұрын

    Ause mumtendele adatisinthitsa kaganizidwe

  • @mosesphiri8563
    @mosesphiri8563Ай бұрын

    Chitsime chimaera chakuya chikaphwa😢😢

  • @BrianAmbeswa
    @BrianAmbeswaАй бұрын

    Tizawakumbukira chifukwa anali munthu ozichepatse mzimu wawo uuse mutendela

  • @charitykambola
    @charitykambolaАй бұрын

    Ndidzamukumbukila ndimiyambi R.I.P

  • @DianaChimseu
    @DianaChimseuАй бұрын

    😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @bubakaramidu
    @bubakaramidu25 күн бұрын

    Ndizawakumbukila Achilima chifucha msso phenya aeo apita nawo

  • @GriffinaziziSoko
    @GriffinaziziSokoАй бұрын

    Rip my big man palibeso

  • @KalipentalaJamu
    @KalipentalaJamuАй бұрын

    Ndidzamukumbukila chifukwa chamiyambi chamudimadima mwana wambuzi anayamwa tonde

  • @user-yl3lg5fk8f

    @user-yl3lg5fk8f

    Ай бұрын

    Harry suliyani my classmate at nayizi primary bangwe good job bro

  • @ZaneleKhoza-cp1hi
    @ZaneleKhoza-cp1hiАй бұрын

    Malawi 😅😅

  • @saidiBerason
    @saidiBerasonАй бұрын

    Miyambi yake monga njoka saweta

  • @MIMIEZenga
    @MIMIEZengaАй бұрын

    Will meet other side of the life 😢😢😢

  • @MIMIEZenga
    @MIMIEZengaАй бұрын

    RIP BIG

  • @MorrisMapiri
    @MorrisMapiriАй бұрын

    Watichotsa Mantha moti even gun point mmalawi sazanjenjemera

  • @user-xg2ks9nw5q
    @user-xg2ks9nw5qАй бұрын

    Malawi talusa munthu ofunikira kwambiri palibe wina ofana ndi chilima

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailosАй бұрын

    Amatilimbikisa kuti tizikhala ogwirizana komaso kitilimbikisa achinyamatafe pakhani yachitukuko

  • @ZaneleKhoza-cp1hi
    @ZaneleKhoza-cp1hiАй бұрын

    😅

  • @PatrequeFanuelKaussiwa-nq9ou
    @PatrequeFanuelKaussiwa-nq9ouАй бұрын

    Zikomo kwambiri

  • @Zulupauljq2dz
    @Zulupauljq2dzАй бұрын

    Ntchito zabwino monga kuyimira dziko

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3qАй бұрын

    Koma chakwera kumutenga zako kukamuphera kumupoto komwe iweyo umadako kumupoto chakwera iwe sataniki wakulu chakwera

Келесі