Ndipo chulungamo chiwoneke ndithu za imfa ya atoht manje
@EddieChan-hj2ql9 ай бұрын
Sangagwire amene sayanjana nawo.
@user-sl5ko7iq1i9 ай бұрын
Amene. 🙏
@MaggieGondwe-vn2wx9 ай бұрын
Amen amen
@giftkanjuchi-qm8hf9 ай бұрын
Koma tu ukuzikolakola wekha. Ukusakanizani nkhani. Nkhani ya atoti manje tb Joshua yamukhuza pati? Nanga bushiri yamukhuza pati? Magalimoto a bushiri ndi za atoti manje zugwilizana pati? Bible limati aneneri onyenga muzawaziwa ndi ntchito zawo and you are one of them. Walakhula zosamveka
@InnocentFly9 ай бұрын
Uziloseleso wekha kuti umwalira iweyo osati miyoyo ya anthu ena
Ndi zomvesa chisoni ifaya atoti manje mlungu alowelelepo😅
@user-xq6vp1tx7z
9 ай бұрын
😢
@duncainjimmy9 ай бұрын
Koma tsopano band Kaya Rist band Kodi ikhala bwanji mphamvu yauzimu wabwino than yawoipa ? Kodi malemba atiuza Kuti mphamvu Yake tiziyivala Ngati Watch kapena covala ? Kodi pamenepa si uneneri wachinyengonso umenewu ?
@eunicemoyo60249 ай бұрын
Kod tsopano mwayamba kapeniso munayamba bwino mwayamba so kunena azazanuso eshiiii 😏😏😏 kom mapastar a masiku ano so mukujajaso azanu😐😐
@giftkanjuchi-qm8hf
9 ай бұрын
Chamba
@salimmkumakumakitombi-yc7pw9 ай бұрын
Tirankhureni bansi...koma kunena zoona chibwerereni akuruwa South africa Dziko mwathu nyasi zachuruka
@meganabigail-ye7fw
9 ай бұрын
Ndipo wina akumuikila kumbuyo iya watenga miImu ya osalakwa yambiri
@user-dk6yc8pl2m9 ай бұрын
Chitanpona Kathu oyipayo achite manyaz
@hashimmtelera95369 ай бұрын
Kodi prophecy yanu ndi imfa ndi zinthu zoipa basi? Mulungu amangokuonetserani kuti kuchitika zoopsa osati zabwino?
@JohnSalikuchepA-iy5tc9 ай бұрын
Pa zonse mwalankhulazo palibepo chauzimu chomwe mwanena ai but i thank you for your advice kuti anthu atuluke mu mautumiki abodz onse koma zinazo its a sign to show that you not matured in spirit. As know that anthu ali ma bondage a satana and akufunika mamasulidwe yet you know that ma waist band amamasula but you are selling it. Why don't you give them for free. Did you buy that gift of prophecy from God? . Kodi ndi aja ananena kuti adzabwera ena mudzina la yesu Khristu koma mphamvu yake anaikana kalekale
Why in malawi if u have money then you are satanic make money bro then left bushili with his money jealous its what we know than to work hard and be with him bushili work hard to be who he is today so wake up my brother and sister poverty it's what make us be jealous with people who have money
@KnowledgecGodwin-xo4pw9 ай бұрын
Tiuzeni zoona za imfa ya m'bale atot manje
@MikeWyson-cf9os9 ай бұрын
Zikomo maprofet nose koma muphuzire kut kuli nafusi zalika limaut chamoyo chili chose chizalawa ifa ine ngat msilamu ndingot palibe amene amapeleka moyo koposa mulungu komaso yemweyo amatenga yemwe nthawi yake yamulungu yamuthela
@meganabigail-ye7fw
9 ай бұрын
Yes aliyense azalawa imfa koma imfa yake amanena ngati mmene akufela oyimba masiku ano? Ambuye ndiwadongolo osamapangana force koma mulungu yekha akhale rhandizo
@aishahabdullah3660
9 ай бұрын
Haqq nthawi ikakwana ya kwana basi ndipo ngati nthawi yake inakwana olo iwe opusawe ukuyankhula zimenezi siungathe kusintha za ifa ya anthu
Пікірлер: 74
Test in peace my favourite
Akunena za Tb Joshua nanga iwo mulungu atawauza bwsnji sanadule imfayi bwanji mmmm
I trust in blood of Jesus I'm very happy for you information may Almighty GOD BLESS Malawi
Amen and amen ,may good lord be with you man of God
Go deeper prophet kondwani nyasulu. You are real man of God as you are saying openly. May God add more anointing to save the nation in Jesus name.
@PerpetuaBilliat-vz5pn
8 ай бұрын
Amen munthu wa mulungu
Akunena za Tb Joshua nanga iwo mulungu atawauza bwsnji sanadule imfayi bwanji mmmmm
Inu mulungu anati cha moyo chilichonse chizalawa imfa ....satana yo wangolowelerapo
Amen
Amen and amen dzinu brother uuse mumutendere
Amen and amen pastor
Ada bushiri sumagona naye tulo eeeeeee umphawi siwabwino ndithu limbikila kugulitsa marist bandiwo uiphula marist band amoto wanzimu oyera kkkkkk
Zikachitika chonchi ena amangofuna kutchukirapo,ndipo amaipitsa mbiri yayena ndikudzipanga iwo kuti akhale ambino,ndichifukwa chake pamapeto pake amachito business.imfazo amaziona bwanji sanazibweze, ngati ndi prophet oona monga wanena kuti amaona ifa yaoimba.
Mukuyakhula zowona abusa simukunama ndipo sipatenga nthawi umboni upezeka
Amen 🙏 Man of God
Ndye mukat ifayi smusiya akhalaso moyo chifukwa ine ndy mtima wanga sndikuupedza ayiii anali Dzanga muthuyi
Malangidzo abwino koma zogulisa wrist band kapena madzi sizinthu zoyenera kuzisatira chifukwa masiku ano aopya pa nkhani ya uneneri
Amen pastor
Amen man of God
Ameen pastor
ok
Let God be God...Rest Well Atoti
May his soul rest in peace
Kuyambila lero mapulofet nonse mukhar pans muzitchula maina moti apapa tiuzen amene akhar next...zinaz tatopa nazo
Amen Amen
Ndikufunanso mai Mawinfo chonde manambaka awo. Chonde
Iweyo ndiwe chiwanda cheni cheni bwanji ukufunaso zinthu zakozo kuti azikupasaso ndalama? Chokachoka mwana wanjoka iwe,
Ndipo chulungamo chiwoneke ndithu za imfa ya atoht manje
Sangagwire amene sayanjana nawo.
Amene. 🙏
Amen amen
Koma tu ukuzikolakola wekha. Ukusakanizani nkhani. Nkhani ya atoti manje tb Joshua yamukhuza pati? Nanga bushiri yamukhuza pati? Magalimoto a bushiri ndi za atoti manje zugwilizana pati? Bible limati aneneri onyenga muzawaziwa ndi ntchito zawo and you are one of them. Walakhula zosamveka
Uziloseleso wekha kuti umwalira iweyo osati miyoyo ya anthu ena
Choyamba nikupepheni kutingati munapasidwa ndi mulungu mulubguyo amati usaweluze sitiziwaso kutiutumikiwako wochokadi kwamulungu musanyoze winaaliyese mutumiki wamulungu tosefendife osalungama
Iweyo ndiwe chiwanda cheni cheni bwanji ukufunaso zinthu zakozo kuti azikupasaso ndalama? Chokachoka mwana wanjoka iwe, 24:03
CHOKA iwe mwana wasatana
Where can we find you man of God?
May ALMIGHTY ALLAH forgive you
Ndi zomvesa chisoni ifaya atoti manje mlungu alowelelepo😅
@user-xq6vp1tx7z
9 ай бұрын
😢
Koma tsopano band Kaya Rist band Kodi ikhala bwanji mphamvu yauzimu wabwino than yawoipa ? Kodi malemba atiuza Kuti mphamvu Yake tiziyivala Ngati Watch kapena covala ? Kodi pamenepa si uneneri wachinyengonso umenewu ?
Kod tsopano mwayamba kapeniso munayamba bwino mwayamba so kunena azazanuso eshiiii 😏😏😏 kom mapastar a masiku ano so mukujajaso azanu😐😐
@giftkanjuchi-qm8hf
9 ай бұрын
Chamba
Tirankhureni bansi...koma kunena zoona chibwerereni akuruwa South africa Dziko mwathu nyasi zachuruka
@meganabigail-ye7fw
9 ай бұрын
Ndipo wina akumuikila kumbuyo iya watenga miImu ya osalakwa yambiri
Chitanpona Kathu oyipayo achite manyaz
Kodi prophecy yanu ndi imfa ndi zinthu zoipa basi? Mulungu amangokuonetserani kuti kuchitika zoopsa osati zabwino?
Pa zonse mwalankhulazo palibepo chauzimu chomwe mwanena ai but i thank you for your advice kuti anthu atuluke mu mautumiki abodz onse koma zinazo its a sign to show that you not matured in spirit. As know that anthu ali ma bondage a satana and akufunika mamasulidwe yet you know that ma waist band amamasula but you are selling it. Why don't you give them for free. Did you buy that gift of prophecy from God? . Kodi ndi aja ananena kuti adzabwera ena mudzina la yesu Khristu koma mphamvu yake anaikana kalekale
Zaziiiii zokhozokha
Akondwani bwanji simunamuwuze poyamba asanamwarire. Azibusa inu. bwanji mkukonda zimenezi. Pepani. Akubanja. Nose nde. Sopano. Apitayo. Ndindani mtchureni plese munthu wamlungu mmmmmmm
Zoonad abusa satana walusa tikuenela kutembenuka mtima
Yesetsani.abusa
Zoonadi
Why in malawi if u have money then you are satanic make money bro then left bushili with his money jealous its what we know than to work hard and be with him bushili work hard to be who he is today so wake up my brother and sister poverty it's what make us be jealous with people who have money
Tiuzeni zoona za imfa ya m'bale atot manje
Zikomo maprofet nose koma muphuzire kut kuli nafusi zalika limaut chamoyo chili chose chizalawa ifa ine ngat msilamu ndingot palibe amene amapeleka moyo koposa mulungu komaso yemweyo amatenga yemwe nthawi yake yamulungu yamuthela
@meganabigail-ye7fw
9 ай бұрын
Yes aliyense azalawa imfa koma imfa yake amanena ngati mmene akufela oyimba masiku ano? Ambuye ndiwadongolo osamapangana force koma mulungu yekha akhale rhandizo
@aishahabdullah3660
9 ай бұрын
Haqq nthawi ikakwana ya kwana basi ndipo ngati nthawi yake inakwana olo iwe opusawe ukuyankhula zimenezi siungathe kusintha za ifa ya anthu
Timva zambiri apa eti
Zoonadi Amen
Sent your number pastor