Ku Boma Penapake Mulankhula Mwachibwana Kwambili - Bon Kalindo

Bon Kalindo responds to a statement made by the Ministry of Information following the burial of the Late Vice President Right Honourable Dr. Saulos Klaus Chilima and eight other Malawians. He also calls on the Malawi Broadcasting Corporation to cease acting as a propaganda machine and instead urges them to strive for impartiality in their reporting.
A Bon Kalindo ayankha zomwe unduna wa zofalitsa nkhani unanena potsatira kuikidwa kwa wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Dr. Saulos Klaus Chilima ndi a Malawi ena asanu ndi atatu. Iye wapemphanso bungwe la Malawi Broadcasting Corporation kuti lisiye kupanga Propanga m’malo mwake akuwapempha kuti aziyesetsa kusakondera mbali imodzi.popereka malipoti.
#malawi

Пікірлер: 42

  • @George-zd5le
    @George-zd5leАй бұрын

    NG'ALULA BON AGALU AMENEWA AZOLOWERA KWABASI, NJOKA NDINJOKA

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2Ай бұрын

    Osafooka , osatopa kms Osachita mantha Dziko ndi lathu ( Thanks Mr Kalindo posachita mantha 🔥)

  • @TembohBaela
    @TembohBaelaАй бұрын

    I will be following you my freedom fighter Mr Bon Kalindo God bless you all of time

  • @PartsonMdeza
    @PartsonMdezaАй бұрын

    bon kalindo 🔥🔥🔥

  • @LaxAllison
    @LaxAllisonАй бұрын

    Kenako tipita ku ma station tikamatche aseke tidzasegula akachoka pampando moto kuti buuuu ❤

  • @dontreybanda278
    @dontreybanda278Ай бұрын

    Well done big boss the DC

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeonАй бұрын

    Freedom fighter 💪 🙌 president wa ife wosowa makwacha

  • @user-fn9si8yu3m
    @user-fn9si8yu3mАй бұрын

    Bless you 🙏

  • @user-mh4ht6tk2h
    @user-mh4ht6tk2hАй бұрын

    Ulemu wanu mr kalindo

  • @AliceChipo
    @AliceChipoАй бұрын

    Ndipo auzeni zoona

  • @FatimaLuwembe
    @FatimaLuwembeАй бұрын

    Sure

  • @Martinnguluwe
    @MartinnguluweАй бұрын

    Big up boss

  • @user-po9yj6io3c
    @user-po9yj6io3cАй бұрын

    Zoona DC

  • @CharlesMaulidi-if3nn
    @CharlesMaulidi-if3nnАй бұрын

    Malawi on 🔥🔥

  • @emmamdhluli2952
    @emmamdhluli2952Ай бұрын

    Nde akuti amumangilanji amenewa? Pachilungamo ngati ichii😅😅😅

  • @user-os7qt6lw2c
    @user-os7qt6lw2cАй бұрын

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321Ай бұрын

    Amene amaona za nyengo tsiku limenelo akuyenera kumangidwa, Chilima Uja munachita Kupha A MCP, tengani dzikoli muzilamula

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214Ай бұрын

    🔥🔥🔥🔥

  • @kurhikhoza8298
    @kurhikhoza8298Ай бұрын

    Anakachoka asapitirizesso

  • @user-nv3rf7bl7r
    @user-nv3rf7bl7rАй бұрын

    Anthu okupopani akupwetekesani a bon mukanangopempha unduna akupwetekesani ameneyi alangidwe nsanje yakula akalindo😅😅

  • @chimwemwematias6069
    @chimwemwematias6069Ай бұрын

    Go kalindo

  • @RobertMbayani-sf6yl
    @RobertMbayani-sf6ylАй бұрын

    Fact

  • @user-fz3gu2ez1o
    @user-fz3gu2ez1oАй бұрын

    Ng'alura Bon...

  • @DicksonMacheso-lr7oy
    @DicksonMacheso-lr7oyАй бұрын

    Kungolankhula chilungamo basi akuyetsa amalawi tikugona

  • @JaneChiwenda
    @JaneChiwendaАй бұрын

    Koma 😂😂😂 ati mwayamba kuikana ndege

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeonАй бұрын

    Bwana ndegeyo musayikane 😂😂

  • @user-fz3gu2ez1o
    @user-fz3gu2ez1oАй бұрын

    Akuti Namandege...😂😂😂😂

  • @LaxAllison
    @LaxAllisonАй бұрын

    Ang'alule mbale

  • @IssahBannet
    @IssahBannetАй бұрын

    Yah zoonadi the DC vuto ndiloti kumalawiko kulibeko president dziko lonvesa chisoni ng'alulani basi

  • @MemoryLikaka-to7ho
    @MemoryLikaka-to7hoАй бұрын

    The DC

  • @VincentMpokosa
    @VincentMpokosaАй бұрын

    😂😂 koma DCCC ndiakatundu

  • @Littlefair7
    @Littlefair7Ай бұрын

    Amalawi tilowe pansewu, kodi ma demo akuvuta bwanji ndi boma ili? Nthawi ya DPP ma demo samachewatu.

  • @user-fn9si8yu3m
    @user-fn9si8yu3mАй бұрын

    Ndipo asatinyaseso athu amenewa

  • @malawientertainment1556
    @malawientertainment1556Ай бұрын

    Dee See

  • @MariaMpinde-qy7ox
    @MariaMpinde-qy7oxАй бұрын

    Kkkkkk namandege

  • @DicksonMacheso-lr7oy
    @DicksonMacheso-lr7oyАй бұрын

    Tiyeni tonse timutsapote kalindo malawi yu wafika pa nyansi anthu oyipa awa a mcp ndipo mbiri imadzibweledza yonkha lero ndi izi achera nsapha patetete

  • @CaptainNyenga
    @CaptainNyengaАй бұрын

    DC unabwadwa bwanji 😂😂 ndikufuna ndizakuone

  • @hastinngschikafa-zf9bc
    @hastinngschikafa-zf9bcАй бұрын

    kkkk kwayaka

  • @LotiBanda-uo5vy
    @LotiBanda-uo5vyАй бұрын

    Mbuzi ya DPP kalindo uchedwa nazo

  • @SteveNkhoma-sz1oj
    @SteveNkhoma-sz1ojАй бұрын

    Chirungamo chiyende

  • @user-km8ni2yk2c
    @user-km8ni2yk2cАй бұрын

    Dc mwana wachabe

  • @Jongwenyirenda
    @JongwenyirendaАй бұрын

    DC kkkkk