The song "Ungandiuze chani" from the great malawian artist Joseph Nkasa
Uyu suoyimba wamba koma waluso loopsa kumasula komanso kuphinzitsa ndikulimbikira anthu ansanje osamawafookerayi tiyeni tizingopushabe pamene zikuwanyasa inu amalawi miziponyerabe kwakuya ndizomwe akunena nkasa apaaaa ndipo ndiphungudi wa anthu osauka osati waolemera❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Nyimbo iyiyi imandikumbusa malemu bambo anga amayikonda heavy mzimu wawo uzipitilila kuwusa mumtendele
Am David from Zambia i like the songs of this man keep it up
Kkkkkkkk kalipila cisilu mwaucisilu wake ,mau amphabvu kwambili ,nkasa i love you and yo musis,.kenz morris in lsk Zambia
This song reminds me my first radio in 2007...good message and i still love it. Zambia
Nkasa atalusa.....auzeee....!
Angakuzed chani matumbi iwe kkkk big up
Loving it,reminds me of my beloved country. Keep it boys. May GOD bless Malawi.
Uyu ndi Nkasa katundu owopsa zedi mmmmm nyimbo yokoma zedi❤❤❤❤❤❤
One of my best musicians 🔥🔥🔥🔥
This is so amazing
I like this.You are a human being ndiye osamapsatira pomasula munthu
11 years ago ?? Anthu munabwera kale eeeih🔥🔥🔥🔥
yimbo za nkasa Nimazi konda kwa basi,keep it up nkasa
Akuti ukanunkhire kutali . via . respect big man
Nyimbo imodzi mwa Nyimbo zabwino za a Nkasa
Nice song ❤️
nyimbo ziwemi za ching'anamulo even after 20yrs,lutizga
Sazabwerezanso
Very good and educative songs.
Wow keep it up Mr Nkasa i love ur songs
Achikulire J Nkasa
Achimwene aakulu.🥰
I love this song akulu amyuxiki
Abwana mumatha
Mumkabifana ndindani kkkk chinayankhulatu
He is talking about Chicco Kalirani...anamuyimba kuti Watewe Galu amulume, then Wamasagwidi Walemera......anangomutopera!
Ndimafuna nyimbo yake yachithekere
Amazing song
Nkhonya yobwezera kuzuna
🔥 Legend
Kkkk me loving this song mweee
songs with meaning .nice and sweet
Send it plz
Mkasa ndiphungudi amakwana
💪💪💪💪💪
The teacher
Annie matumbi anasambwazideatu munyimboi
Ndi Chiko Kalirani.
Nc encouragement man.
keep it up nkasa
Yomweyo
ungandiuze chani iweee
Chonena ine ndilibe mingolili ikumveka
legend
tamuuze nkasa ameneyo, wausilu anamunyengeranso ng'ono wanga
wati bwanj aise??
Zoona athuam ili amakala ndichizolowelo ngati sunamlakeile kuksmbskamba
kkkkkkkkk uthenga umapita kwa chicco Kalirani, momwenso chicco sanayerekedwe, anakomana ndi eni ake alalata hahahahhha
Kkkk koma munalusa ankolo
kulalata phungu..kaya umalalatira mkulu anakunamiza pick up
Mkasa
zoona phungu wa anthu osauka
Muuze azazolowera!!mkasa umatha zedi kkkkkk
Respect phungu
🕺🏿🕺🏿🕺🏿🕺🏿🕺🏿🕺🏿🕺🏿❤❤❤
Yes.is.beutful.chanel.thwe.learn.more.things.thanks
Auze phungu
kkkkkk koma mpaka pamenepa?
joseph nkasa-ungandiuze chani
Rafailo thamangani
100 brother
sarina gurewankuru
Ankolo imeneyi Biff kspena Beef? ?
Zinamuwawadi nkuluyu hahahahahaha
kodi ndindani amene umamunena? onga ngati awo kumauzadi momveka kumutukwana kumene wauchisilu kukulira kuuzimwale ndichoncho amati ndiye ndani nkasa sangafooke ndizochopa
Chiko Kalirani, anaimba wamaso aphwiti walemera wathetsa banja lake.
Luciani salatiele
Message send boss
kkkkkkkkklk koma anthunu mwaunjeza
Bulutufu
You make me feel home & friendly
Bwanawa amakwana
Tha legend kept up ,ur songs z good advice song
Пікірлер: 76

@MathewsDozola-ce2hv
10 ай бұрын

@johnbullyohanittokasikizim7127
6 жыл бұрын
Ndimafuna nyimbo yake yachithekere
Amazing song
Nkhonya yobwezera kuzuna
🔥 Legend
Kkkk me loving this song mweee
songs with meaning .nice and sweet
@haroonmpund6053
4 жыл бұрын
Send it plz
Mkasa ndiphungudi amakwana
💪💪💪💪💪
The teacher
Annie matumbi anasambwazideatu munyimboi
@MathewsDozola-ce2hv
11 ай бұрын
Ndi Chiko Kalirani.
Nc encouragement man.
keep it up nkasa
Yomweyo
ungandiuze chani iweee
Chonena ine ndilibe mingolili ikumveka
legend
tamuuze nkasa ameneyo, wausilu anamunyengeranso ng'ono wanga
@mouricesaidi5348
3 жыл бұрын
wati bwanj aise??
Zoona athuam ili amakala ndichizolowelo ngati sunamlakeile kuksmbskamba
kkkkkkkkk uthenga umapita kwa chicco Kalirani, momwenso chicco sanayerekedwe, anakomana ndi eni ake alalata hahahahhha
Kkkk koma munalusa ankolo
kulalata phungu..kaya umalalatira mkulu anakunamiza pick up
Mkasa
zoona phungu wa anthu osauka
Muuze azazolowera!!mkasa umatha zedi kkkkkk
Respect phungu
🕺🏿🕺🏿🕺🏿🕺🏿🕺🏿🕺🏿🕺🏿❤❤❤
Yes.is.beutful.chanel.thwe.learn.more.things.thanks
Auze phungu
kkkkkk koma mpaka pamenepa?
joseph nkasa-ungandiuze chani
Rafailo thamangani
100 brother
sarina gurewankuru
Ankolo imeneyi Biff kspena Beef? ?
Zinamuwawadi nkuluyu hahahahahaha
kodi ndindani amene umamunena? onga ngati awo kumauzadi momveka kumutukwana kumene wauchisilu kukulira kuuzimwale ndichoncho amati ndiye ndani nkasa sangafooke ndizochopa
@MathewsDozola-ce2hv
11 ай бұрын
Chiko Kalirani, anaimba wamaso aphwiti walemera wathetsa banja lake.
Luciani salatiele
Message send boss
kkkkkkkkklk koma anthunu mwaunjeza
Bulutufu
Achikulire J Nkasa
@kapenakapena6882
5 жыл бұрын
You make me feel home & friendly
@inosentmachado9974
4 жыл бұрын
Bwanawa amakwana
@alexdicky2275
Жыл бұрын