From comedy to Vice President

Ойын-сауық

MICHEAL USI ACCEPTANCE SPEECH
this is both English and chichewa

Пікірлер: 9

  • @PaulMwachande
    @PaulMwachande29 күн бұрын

    Chilima anafela mbendela ya malawi lelo mwasankhana dyelelani basss

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz29 күн бұрын

    kkkkk yudasi lemba taliona 😅

  • @user-mo5od8cy3n
    @user-mo5od8cy3n29 күн бұрын

    Of course kma asamale ndi moyo wake

  • @robertchitsulo8006
    @robertchitsulo800629 күн бұрын

    All the best Michael usi . Work hard.

  • @PaulMwachande
    @PaulMwachande29 күн бұрын

    Pafa nzako pali malo olo malemu bigu atamwalila panabwela may joice banda izi mwakonzazi ndizomwezo bas malawi walandila bas

  • @JamesChimera-hw1nv
    @JamesChimera-hw1nv29 күн бұрын

    Ambuye amasintha nyengozamunthu titha kunyoza kunyogodola koma zake zasintha ndithu munjira iliyonse

  • @user-nu1dj3jh7b
    @user-nu1dj3jh7b29 күн бұрын

    Michael usi ndimunthu wanzeru kwambili.

  • @PeterThomas-lw3io
    @PeterThomas-lw3io28 күн бұрын

    Zako anazuzika ndi kampeni kuti akhale VP komano wangotola ndikukhulupirila kuti imfa ya chilima unapanga umpandu iwe ndi Chakwera Mulungu akuwina zonse u VP imeneyo ndiwa mpasi pomwepa komano kumwamba zilango ndimene umanenala wekhamo ukuziziwa zimene wapanga

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y28 күн бұрын

    Chilima anali mufana oganiza boo not this Galu mwapha muzanu

Келесі