Daughter of Zion-- song Kodi yesu asamala

Пікірлер: 210

  • @LaitoneJefitala
    @LaitoneJefitala2 ай бұрын

    Mulungu ndiwadongosolo anthu ena anawalengadi Kuti adzatumikile kudzera mkuimba ndimakumbukira imfa ya m'bale wanga amene tidaabadwa mapasa yemwe anafa ndimphenzi koma Mulungu amasamala ndizovuta kuiwara koma Yesu amasamala

  • @evetalikukuta1487
    @evetalikukuta1487 Жыл бұрын

    When my Dad passed away in 2020 11th February....i used to ask "kodi yesu asamala"? Coz i was not ready to face reality that my dad has gone....but God has provided us with more wisdom to take care of each other...Ambuye asamala

  • @ketamwalwanda6056

    @ketamwalwanda6056

    Жыл бұрын

    God really cares for Us

  • @manganisagonja9492

    @manganisagonja9492

    Жыл бұрын

    Amen and amen that's how our God is

  • @isaackaphuka

    @isaackaphuka

    Жыл бұрын

    Ndipo ine ndakhala ndikumuona Mulungu akukhala Mulungu pa Moyo wanga.

  • @newasomanje

    @newasomanje

    Жыл бұрын

    Zoonadi YESU amasamala Zaire

  • @newasomanje

    @newasomanje

    Жыл бұрын

    YESU amasamala nthawi zonse

  • @thokopangani7854
    @thokopangani78546 ай бұрын

    Today she came at our church ( Life Giving Spirit Church) to pray and ended up singing for us , The first song was Thanthwe , my sister you are minister .. The moment you started singing I felt the presence of the Holy Ghost.

  • @user-cr3is4yv2z
    @user-cr3is4yv2z16 күн бұрын

    Jesus christ cares I have story about my life and whenever I think of it I really appreciate to you Lord !🕷

  • @JosephChimwano-eu8sk
    @JosephChimwano-eu8sk10 ай бұрын

    Sometimes I ask my self "Kodi yesu asamala?" Looking at situation am passing through that all my agemate I used play when we were young they are are all rich and they stays in their own house

  • @JohnSelemani-me3sx

    @JohnSelemani-me3sx

    3 ай бұрын

    When am reasoning gospel songs am blessed

  • @hellinamwimba9839

    @hellinamwimba9839

    9 күн бұрын

    He cares for you. Have you ever asked yourself why God is keeping you alive while some whom you played with are dead?

  • @user-zz1qj7rx2p
    @user-zz1qj7rx2p Жыл бұрын

    Jesus 😢😢 thank you for everything 😢😢 im passing through alot but one thing i know is that you care for me alot

  • @lizwikhanyile5091
    @lizwikhanyile50912 ай бұрын

    Yesu amasamaladi ....ndimakumbukira mamuna wanga atamwaliw pa ngozi kundisiya ndi mwana wakhanda koma mwa zisomo mwana wakula shes 3 years old now yesu amasamaladi... May God bless u sis

  • @lizzyhuyser2768
    @lizzyhuyser2768 Жыл бұрын

    100/ kusamala kwake yesu ❤❤❤❤🎉🎉ndine bone amunanga namwalila kunisila tiana tatichepele koma you can't belive pano yesu asamala abale 🤗

  • @lindanimbewe1118

    @lindanimbewe1118

    Жыл бұрын

    Amen

  • @mwebembezijonas
    @mwebembezijonas Жыл бұрын

    I love the song from Uganda 🇺🇬 🇺🇬

  • @jobrahgreenafrica
    @jobrahgreenafrica2 сағат бұрын

    i heard your song kwa neighbour till i searched you here, Beautiful mama

  • @richardmalumba857
    @richardmalumba857 Жыл бұрын

    My greatest testimony. Yesu amasamala. We are coming from far. Only God knew where we will be.

  • @rejoicemagulumanya1240

    @rejoicemagulumanya1240

    Жыл бұрын

    Exactly 😭

  • @NdazionaKumcheza
    @NdazionaKumcheza3 ай бұрын

    Yesu amasamala amene amasamalaso za yesuyo mulungu ndi chikondi

  • @festerchinula7806
    @festerchinula7806 Жыл бұрын

    Ndimakhala ndi funso limeneneri kodi yesu asamala pamene makolo anga onse anamwalira chaka chimodzi 2022. Misozi sikutha maso mwanga koma poti mulungu asamala.

  • @christopherchilufya1954

    @christopherchilufya1954

    Жыл бұрын

    Indeed Jesus cares.Iam Bemba,thank God I can hear every word.

  • @rejoicemagulumanya1240

    @rejoicemagulumanya1240

    Жыл бұрын

    Yesu asamala, osadandaula.

  • @chrismazuwa

    @chrismazuwa

    Жыл бұрын

    Kondi yesu. asamala. Chonde ambuye Mukumbukile Malawi njala mulili wa Madzi

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson8 күн бұрын

    Yesu asamala ndadusa mnyengo zovuta ine kuyamba ndili wachichepere bambo ondipeza samandifunira zabwino pamoyo wanga koma yesu asamala

  • @daughterofzionphalycemalik1296
    @daughterofzionphalycemalik1296 Жыл бұрын

    Yesu akusamala nyengo zonseee

  • @thokozanimtokomaartist4614

    @thokozanimtokomaartist4614

    Жыл бұрын

    Amen

  • @chifundochimenya6368

    @chifundochimenya6368

    Жыл бұрын

    Favourite song of my late mother continue to sleep well mom l love and l miss you

  • @pemphokatembe443

    @pemphokatembe443

    4 ай бұрын

    Ndipo zoona❤

  • @Stewartchikoja
    @Stewartchikoja16 күн бұрын

    He cares indeed,,we having free air. Without paying anything He cares all the times.

  • @RashidDyton
    @RashidDytonАй бұрын

    He withdrawal not His eyes from the righteousness Thank you God for your care 🙏

  • @LeyahPhiri-sd9xj
    @LeyahPhiri-sd9xj8 ай бұрын

    The powerful worship song ever!❤️❤️❤️❤️

  • @ritabani274
    @ritabani274 Жыл бұрын

    Ooooh Yesu amasamala mai anga anamwalila 1996 tinali ana 10 koma Yesu anatisamala amen

  • @marthamafunga6329
    @marthamafunga6329 Жыл бұрын

    Yesu amasamaladi🎉ndipo amawona nyengo iliyonse yomwe timadutsa

  • @georgenkhoma6898
    @georgenkhoma68987 күн бұрын

    Songs that speak to broken souls, spirits and minds! Yesu Asamala, another excellent piece Phalyce! more grace to you!

  • @mwayikambiyayoutubekambiya3731
    @mwayikambiyayoutubekambiya3731 Жыл бұрын

    Indeed Jesus cares for us day & night🙏🙏

  • @user-lg6ym4hz3w
    @user-lg6ym4hz3w7 ай бұрын

    Nice song God bless you my sister

  • @HenryHenock-lz7wu
    @HenryHenock-lz7wu Жыл бұрын

    Yesu asamalad inalipo nthawi imene ndinali ndi mkuluwanga kuchipatala mpaka anamwalira ndikuona ...Ndinalira mosweka mtima mkumamufusa ambuye kut walorelanji 😭but mu zose yesu asamala

  • @TadalaChithope-yg9fo
    @TadalaChithope-yg9fo7 ай бұрын

    Zowonad yesu asamala l lost my dad 2014 eish moyo unali olimba koma yesu zowona amasamala 🙏🙏

  • @florachibambo9814

    @florachibambo9814

    6 ай бұрын

    Same group 2014 my dad pasd on

  • @estawilson9998
    @estawilson9998 Жыл бұрын

    Ndine mbon kut Yesu amasamala Amen amen kuyambira 2015 kuzafik 2020 mmmm moyo umawawa kwambir ndimagonera jolly jus ndiana anga ndasi limodzi kunyemana kkkk kma Yesu ameneyu zomwe anandichitira dziko silikumvetsa ,pano zakudya sinkhan azibale anga pano akudalira ine Hahaha Hahaha ,ngt mlipo ena mlindifunso ngt ili ayi ndingt Ambuye akuonekeren kut nanu mkhale ndiyankho Amen mdalitsike mama.

  • @lindanimbewe1118

    @lindanimbewe1118

    Жыл бұрын

    Amen and amen

  • @mercynina6288
    @mercynina62886 ай бұрын

    Asubuh na usiku huu ndio wimbo wangu! Mungu ananitunza kila wakati

  • @idahmasanjala6329
    @idahmasanjala632911 ай бұрын

    Inde amasamala umboni wa moyo wanga ku dziko lachilendo with my child Koma ndinamuona mulungu akusitha nyengo zanga Nyimbo zanu women of God zimandipatsa chilimbikitso

  • @hellinamwimba9839
    @hellinamwimba98399 күн бұрын

    My favourite worship artist ❤

  • @malingamussah5934
    @malingamussah5934 Жыл бұрын

    There is power in this song nyimbo yomwe amaikonda sister wanga rest in peace my lovely sister

  • @alinafesathawa-yr3gj
    @alinafesathawa-yr3gj6 ай бұрын

    God is faithful there times we feel God has left us but he's right there taking care.... Powerful song

  • @GraceKanyenge
    @GraceKanyengeАй бұрын

    Ambuye osakhumudwitsaa kwa iye kulibe cholepheleka 🙏🙏🙏🙏

  • @MauChipande
    @MauChipande2 ай бұрын

    Ijust love the performance today 😊 it was something else 😊 mudzibwerabwera mammie😊

  • @christopherchilufya1954
    @christopherchilufya1954 Жыл бұрын

    Yes Jesus cares.Nice song indeed.thou I'm Bemba I can get the message.

  • @SamiaManganda-gj3zh
    @SamiaManganda-gj3zh Жыл бұрын

    Komanso iyiyi ndi one. Mumatisuntha mama continue

  • @user-vy3cv1de7g
    @user-vy3cv1de7g Жыл бұрын

    I like this song almost every morning iplay this song

  • @oliviatbonongwe2544
    @oliviatbonongwe2544 Жыл бұрын

    I needed masamala dzinthu zikafika polimba ndi pamene wataya ciyembekezo.

  • @MaryChihana-bm9jo
    @MaryChihana-bm9joАй бұрын

    Yes, Jesus Christ always cares us whether the devil like or not

  • @aliceshawa3677
    @aliceshawa36779 ай бұрын

    My mother loved this song. 😢😢

  • @user-oh4dq3yp3e
    @user-oh4dq3yp3e8 ай бұрын

    God cares for us regardless of any situation

  • @user-st9zx5dc3e
    @user-st9zx5dc3e Жыл бұрын

    Wen my sister passed away in 2022 August....I used to ask Kod yesu asamala😢😢continue to rest in peace maria sis

  • @ceciliamakina3309
    @ceciliamakina3309 Жыл бұрын

    God cares for us day and night and in every situation that we pass through

  • @VeronicaKhuleya-zh1if
    @VeronicaKhuleya-zh1if Жыл бұрын

    This is my favorite song,I can listen to it day and night.

  • @natashaphiri2530
    @natashaphiri2530 Жыл бұрын

    He cares for us coz his the protocol breaker of all situations.

  • @MaulidiFebbie
    @MaulidiFebbie10 ай бұрын

    We may think that God has forgotten us but he still cares indeed he cares love this song

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq Жыл бұрын

    Wow!!!! ❤❤❤ Powerful powerful Mama athu mumatiimilira ndithu asamaladi nthawi zonse n Amen 🛐

  • @phillipchiotcha3197
    @phillipchiotcha3197 Жыл бұрын

    Nyengo zomwe zowawisa ndikudusa panapo ndinyimbo yomwe ndimamvera and kuonera everyday

  • @user-xg9wo1ru6y
    @user-xg9wo1ru6y3 ай бұрын

    Ambuye asamala aliye ofunta na fiti yonse kuti amuziwe mulungu ndi yesu

  • @chikondizimba9085
    @chikondizimba9085 Жыл бұрын

    There is anointing of God in your songs. Keep it up

  • @victoriakamowa1116
    @victoriakamowa11169 ай бұрын

    Ambuye musamala...ndlibe mau

  • @susankadulira4559
    @susankadulira4559 Жыл бұрын

    Indeed God cares what I am today it's all about God

  • @samueltkalima8317
    @samueltkalima83175 ай бұрын

    I enjoy listening to this song

  • @TinenenjiWakudyanaye-ib3zs
    @TinenenjiWakudyanaye-ib3zs9 ай бұрын

    My best song ever!!! I cry over it!!!!!

  • @tamikazulu7285

    @tamikazulu7285

    6 ай бұрын

    I shed tears too😢

  • @chiccahkatanga9359
    @chiccahkatanga9359 Жыл бұрын

    Nyimbo yotonthoza mtima

  • @user-wy6hs7vg1c
    @user-wy6hs7vg1c Жыл бұрын

    Yesu asamala nthawi zose AMEN

  • @eliechitaya7172
    @eliechitaya7172 Жыл бұрын

    In 2020 Nnadutsa mnyengo yowawitsa, ulendo wanga wa mimba unali owawa mpakana kubeleka, , koma inali nyengo yowawitsa😭😭😭😭 after all these sufferings mwangayo nkudzamwaliraso ali ndi miezi iwiri, nde mpakana pano ndimadzifunsabe mafunso kuti kodi Yesu Amasamaladi???

  • @lindanimbewe1118

    @lindanimbewe1118

    Жыл бұрын

    Yes amasamala Yesu... Munyengo zonse HE is there don't lose hope.... Ambuye akulimbikitseni nakupatsani mayankho mudzina la YESU CHRISTU

  • @clyviakalivea9188
    @clyviakalivea9188 Жыл бұрын

    Ooh yes amama powerful songs 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @JaneNgulube-rm2ot
    @JaneNgulube-rm2ot9 ай бұрын

    Your songs heals me

  • @MemoryZimba-tx5xp
    @MemoryZimba-tx5xp7 ай бұрын

    Kip on burning sis💪💪💪

  • @MaxonSonga-ve1ji
    @MaxonSonga-ve1jiАй бұрын

    Very powerful song

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz24 күн бұрын

    I remember my late mom rest in piece Joyce chisambi

  • @user-yn4hq8cs7y
    @user-yn4hq8cs7y4 ай бұрын

    What a powerful and soothing song

  • @ayandabanda2546
    @ayandabanda254610 ай бұрын

    AmaSAMALA AMBUYE🙌🙌

  • @henryphiri2901
    @henryphiri2901 Жыл бұрын

    Very true , Yesu Amasamala always 🔥🔥🔥🔥

  • @tamikazulu7285
    @tamikazulu72856 ай бұрын

    This used to be my mom favourite.... may her soul rest in peace 😢... i love this song becouse i know he really care about me..... he has been with me when i thought had no future 😢

  • @harrietkamwambeni-mv9ki
    @harrietkamwambeni-mv9ki Жыл бұрын

    Ngakhale mu nyengo ya cyclone ambuye atisamala👏👏👏

  • @user-dh8ho2qt4h
    @user-dh8ho2qt4h9 күн бұрын

    ❤❤❤❤ My favorite songs 🎉

  • @Martha1436
    @Martha1436 Жыл бұрын

    Mwanditsitsimutsa. Yesu asamala no matter what? 🙏🏾🙌🏾

  • @wezziebanda4986
    @wezziebanda4986 Жыл бұрын

    Yes he cares... Olo nyengo zibvute bwanji 😭😭😭😭 amasamala.

  • @MartinChilomo-hz6cs
    @MartinChilomo-hz6cs3 ай бұрын

    Ndine mboni, Yesu amasamala ndithu. Ndikukumbukila mu chaka chowawa Cha 2021 pomwe ndinadwala convid. Koma ndinaona Mulungu akundichilitsa. Yes Yesu asamala

  • @DorisNkwanda
    @DorisNkwandaАй бұрын

    Amen. Jesus cares about my family , my life

  • @smartchiotcha2558
    @smartchiotcha25589 ай бұрын

    In every situation he is always by my side,,, i don't loose hope in good and difficulty situation. Mbuye asamala

  • @user-nv4hi1zq7r
    @user-nv4hi1zq7rАй бұрын

    Amasamala yesu.. Satikhumudwira

  • @EstherManda-ex3bc
    @EstherManda-ex3bc Жыл бұрын

    Powerful message 🙏

  • @marthamandionga1919
    @marthamandionga19192 ай бұрын

    Inde Yesu asamala. Thank you Lord Jesus 🙏

  • @rashiemilanzie6910
    @rashiemilanzie69103 ай бұрын

    For that I know Jesus cares, as Phillipians states, I do all things through Christ who strengthens me

  • @user-tk8pd5bg4g
    @user-tk8pd5bg4g9 ай бұрын

    My favourite song❤❤❤❤

  • @user-um2zw2ju5p
    @user-um2zw2ju5p6 ай бұрын

    Ndinali mu nyengi yowawa kwabasi Koma yesu ameneyu wandidutsitsa ❤

  • @ManuelMalunga-fl3vq
    @ManuelMalunga-fl3vq Жыл бұрын

    Nyimbo zainu Mama ndimwala mwala zedi ulemu wanu ndithu keep it up❤❤❤❤🛐

  • @user-vu9cv1rp8w
    @user-vu9cv1rp8w2 ай бұрын

    Zoona Yesu asamala am a widow koma akundisamala

  • @JUDITHGANI-cu2oh
    @JUDITHGANI-cu2oh22 күн бұрын

    Yesu asamara my family

  • @fasweckbekete2006
    @fasweckbekete200610 ай бұрын

    lord we ask your blessings upon us day and night as you are loving God ,many thanks go to the daughter of Zion for the beautiful song indeed God bless

  • @daughterofzionphalycemalik1296

    @daughterofzionphalycemalik1296

    3 ай бұрын

    Amen

  • @user-xe5il4cg5d
    @user-xe5il4cg5d5 ай бұрын

    Ndinatchoka mwendo koma yesu anandichiritsa zoonadi yesu amasamala

  • @daughterofzionphalycemalik1296

    @daughterofzionphalycemalik1296

    3 ай бұрын

    Amen

  • @wligomeka1
    @wligomeka16 ай бұрын

    Ndipo nyimbo iyi imandipasa chimwemwe thawi zonse ndipo imandilimbikisa

  • @hytk4945
    @hytk4945 Жыл бұрын

    Andisamalira ine!

  • @FagessWilson-jt9nb
    @FagessWilson-jt9nb11 ай бұрын

    Yes amasamalirad ,since I lost my husband 2012 akundisamala pamodzi ndiana😱😱😱🙏🙏🙏

  • @lindanimbewe1118
    @lindanimbewe1118 Жыл бұрын

    Cast all your burdens unto JESUS for he cares 🙏🙏🙏

  • @tiwongehojaney5873
    @tiwongehojaney5873Ай бұрын

    Yesu asamala nthawi zonse😊❤❤❤❤😊❤😊😊😊❤😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊❤❤❤❤😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊

  • @wligomeka1
    @wligomeka16 ай бұрын

    Nice song ndipo kwambili kwake yesu amasamala amen

  • @AlefaChomanika-oh8ds
    @AlefaChomanika-oh8ds4 ай бұрын

    Zikomo chifukwa mumasamala ambuye😷😭😨🙏

  • @blessingsemulyn638
    @blessingsemulyn63811 ай бұрын

    Nyimbo iyi imandipatsa chiyembekezo nthawi zonse ndaimvera. He really cares.

  • @loysonmussah5295
    @loysonmussah5295 Жыл бұрын

    Am blessed keep it up my dear yesu asamala

  • @gladyMoffat-lh5vw
    @gladyMoffat-lh5vw Жыл бұрын

    Jesus care 4 us all the tym

  • @user-zz1qj7rx2p
    @user-zz1qj7rx2p8 ай бұрын

    Im here November 20/2023 i know ur there watching over us n you cares alot my darling Jesus

  • @eltonnankhwere3284
    @eltonnankhwere32847 ай бұрын

    Ineyo i had stress koma the moment istarted listening this song all the stress inapita Yes inde Yesu Asamala ndithu

  • @AndrewBiliat
    @AndrewBiliat21 күн бұрын

    His grace is sufficient

  • @shecksmsumba4741
    @shecksmsumba4741 Жыл бұрын

    Jesus cares indeed. Amen.

  • @user-oz6zj8ve7n
    @user-oz6zj8ve7n5 ай бұрын

    YEHOVA I know mukusamala za matenda anga 😭😭😭 May you take control Lord. thanks phalyce for this song it strengthen my heart

  • @daughterofzionphalycemalik1296

    @daughterofzionphalycemalik1296

    3 ай бұрын

    Amen

  • @chimzybottomani8079
    @chimzybottomani8079 Жыл бұрын

    Indeee asamala ....bi blessed phalayce I like all your songs eish umandilimbikitsa

  • @user-st9zx5dc3e
    @user-st9zx5dc3e Жыл бұрын

    Our God he is a caring God😢