Chiyambi Cha Udani Wa Kell Kay Ndi Provoice

Ойын-сауық

Chomwe chinachitika kut Kelly amubloke Lameck
#kellkay #provoice #malawi

Пікірлер: 66

  • @user-xp8kr7si4q
    @user-xp8kr7si4q7 ай бұрын

    Province lameck ngat anawona cholakwika kwa kky anakamufiklra pafupi monga nzake ndikumufusa zaphekesela zikuveka after ndikumupasa malangizo kwinaku akumulibisa ntima ziphekesera yoipayo

  • @clydenyasulu7642
    @clydenyasulu76427 ай бұрын

    Aaaa oyipa athawa yekha

  • @memoryyusufu
    @memoryyusufu7 ай бұрын

    Olakwa ndi Kelly key wakupha martse ndipo nzakeyo sanalakwe Ndipo adzabweza ndi mwin wake mulungu

  • @memoryjames-po7xl

    @memoryjames-po7xl

    7 ай бұрын

    😮😮😮

  • @NoelMasala
    @NoelMasala7 ай бұрын

    Mene ndamvela muti uyu provoice analakwitsa

  • @GraciousPricenyirenda-dh3tz
    @GraciousPricenyirenda-dh3tz7 ай бұрын

    Well. I knew provoice way back. Pokopoko chiphokoso muwallet.. kumazitsata mbobaaa

  • @memorykilofasi1165
    @memorykilofasi11657 ай бұрын

    Orakwa ndi Kelly key nayeso coz anatchukisidwa ndi martse😂😂😂

  • @Kvbwoy07
    @Kvbwoy077 ай бұрын

    Inuso amavita simukuzisata provoice anaziwika kell kay tisanamuziwe

  • @jonasbanda5605
    @jonasbanda56057 ай бұрын

    Kell Kay amafunika amuze nzakeyo zomwe analakwitsa osat ku brocker

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson14437 ай бұрын

    Mr Sam thanks for your job search mumati segula Mitu bg

  • @JoyceGondwe-dw2em
    @JoyceGondwe-dw2em7 ай бұрын

    Mzimu wa munthu ndi oopsa

  • @franklinmauwa2256
    @franklinmauwa22566 ай бұрын

    Kell kay ndmwana woipa nanga anamu blocker nzake cifukwa chan

  • @chiefjusticie
    @chiefjusticie7 ай бұрын

    Ulemu wanu Sam timakunyadilani

  • @DonGoliath-uh9gp
    @DonGoliath-uh9gp6 ай бұрын

    And kell kay siamene anacgukitsa provoice mwanama apo madala😂

  • @MushyBuay
    @MushyBuay5 ай бұрын

    Sindigaloze munthu

  • @malawimuahmmed5941
    @malawimuahmmed59417 ай бұрын

    Keep up the good work🎉

  • @ChifundoSiliya
    @ChifundoSiliya7 ай бұрын

    Oblocka nzake ndamene olakwisa apa

  • @user-ny7we5bt3b
    @user-ny7we5bt3b7 ай бұрын

    Inuso mwaoneka kuti muli mbali ya kell ...

  • @DonGoliath-uh9gp
    @DonGoliath-uh9gp6 ай бұрын

    Bro tinaonela ma videos onse ife ndipo provoice simuthu olakwa ngakhale inuyo muli mbali ya kell kay

  • @EkariNamate
    @EkariNamate7 ай бұрын

    Stop adding fuel to the fire let them sort out their shit ,osawayambanisa anthu rather mangan mudzi

  • @user-qz2uw3qy3l
    @user-qz2uw3qy3l7 ай бұрын

    Only God knows

  • @gilbertmtenje9157
    @gilbertmtenje91577 ай бұрын

    Lameck anablower nd pokopoko fada... That time kellz asanadzwike coz ambri tinamudzwa nd ndlole ndipite Koma anatrenda kwambri nd mwano

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d7 ай бұрын

    Utsi sufuka

  • @JayKawereMw
    @JayKawereMw7 ай бұрын

    Olakwa kelly kay

  • @smedia9049
    @smedia90497 ай бұрын

    This is disturbing 😢

  • @webstermphunda3421
    @webstermphunda34217 ай бұрын

    Olakwa ndi kell Kay amwene provoice sanalakwitse by saying ngati zikuwakhudza Mulungu adzabwenza coz that's what God do to such people nde kell Kay dragged him self like he truly knows something on Martse's death

  • @DanzedaDanielAlbert
    @DanzedaDanielAlbert7 ай бұрын

    Olakwa ndi Kell Kay Cz Munthu nzako Ngati akukuyenda pansi ,let him done with it after all azakupezani Ndichifukwa chake Provoice akunena Kuti Kell Kay anamublocker after Martse's death cz nayeso analiwodabwa ka Provoice kuyika status yonena Kuti *R.I.P MARTSE ONLY GOD KNOWS. Nkusonyeza Kuti zilipo zimene ankazinva eniso zimene amanvazo Munthu yemweyo nkumublockerso , exactly Kell Kay anazilakwitsira pomubloka Provoice.........

  • @basheerrazack7976

    @basheerrazack7976

    7 ай бұрын

    Anachita bwino ku mubrocker chifukwa ngati zawo akanafutsa kaye zakeyo osamapanga third kuwiri

  • @Kvbwoy07
    @Kvbwoy077 ай бұрын

    Olakwa ndi kell kaya sanamuze nzakeyo kuti wam blocker chifukwa chani Coz zifukwa zimene mkunena inuozo zongoganizraso

  • @ChifundoSiliya
    @ChifundoSiliya7 ай бұрын

    We've known provoice since 2013 b4 even we knew Kelly kay

  • @KelvinChipezeni-nw1fo

    @KelvinChipezeni-nw1fo

    7 ай бұрын

    Fact

  • @waltermaziya4474

    @waltermaziya4474

    7 ай бұрын

    and...?

  • @user-oz9mr6rc5d
    @user-oz9mr6rc5d7 ай бұрын

    Kell Kay Ndi opilila province ukuyenela Kuti apepese

  • @josephkaliati9100
    @josephkaliati91007 ай бұрын

    I knew I could depend on u to knw abt this feud😂, I wasn't in the mood to watch tima back n forth video tawo pa social media pages pawo no

  • @user-gv7pq8zr1q
    @user-gv7pq8zr1q7 ай бұрын

    Okuphayo bac ,

  • @user-yd3ew4vm8o
    @user-yd3ew4vm8o7 ай бұрын

    Kodi kumalawi munthu wotchuka akangofa basi akupha akhale Gwamba, Bushiri ndi Kelly Kay! Why? Ngati zili tchochi ponyani evidence tiwone apa. Osamango panga create zaboza apa. Vuto la atola nkhani nanutso mukongodya nkute kwanuko then mumawona ngati ngati basi anthu wotchita bwino.. Zachamba yeti limbikilani mupenze zanu.

  • @damascuszimba8784
    @damascuszimba87847 ай бұрын

    Olakwa ndiyemwe anapha matse

  • @user-yi6rq4gm6u
    @user-yi6rq4gm6u7 ай бұрын

    Olakwa ndi kelly Kay chifukwa chamayenela kumu block provoice ndipamene analakwisila zithu bwezi akungomuyangana

  • @Fasakiudhu-ub2we

    @Fasakiudhu-ub2we

    7 ай бұрын

    Mau ofeka

  • @HopeSoko-zr4ez
    @HopeSoko-zr4ez7 ай бұрын

    Kelly kay

  • @VeronicaSekobi-is6dk
    @VeronicaSekobi-is6dk7 ай бұрын

    Keep up the good work 🎉🥳

  • @sammalvitha

    @sammalvitha

    7 ай бұрын

    Thanks, ❤️

  • @VeronicaSekobi-is6dk

    @VeronicaSekobi-is6dk

    7 ай бұрын

    ​@@sammalvitha❤

  • @EdwibBenHara
    @EdwibBenHara7 ай бұрын

    Kell Kay ndi wachochi Nanu inu

  • @MlangeniZ.E.C
    @MlangeniZ.E.C7 ай бұрын

    Ulemu wanu bigy

  • @benjaminbanda2534
    @benjaminbanda25347 ай бұрын

    Following

  • @yungtingo420
    @yungtingo4207 ай бұрын

    😂

  • @brightkwenje-ib7yo
    @brightkwenje-ib7yo7 ай бұрын

    Let's forgot about this

  • @user-zc2iq1ep3k
    @user-zc2iq1ep3k7 ай бұрын

    Provoice

  • @ChisomoKapanda-jg2uf
    @ChisomoKapanda-jg2uf7 ай бұрын

    Kumupanga block provoince anachita bwino kupewa phikoso kelly key siwamapokoso

  • @KaSoKa-tr1rf

    @KaSoKa-tr1rf

    7 ай бұрын

    wamoyo wachikazi

  • @chimwemwengangala
    @chimwemwengangala7 ай бұрын

    Kuona kwa khaniyi zikuonesa kuti inachuluka ndi sanje chabe provoice being Kell Kay's friend he supposed to stand by him and I think he knew why Kayz broke him that's why samafuna kumufusa komaso zikuonesa kuti amafuna iye awoneke wabwino kwa anthu kuti amukonde,,, koma funso likanakhala kuti anthuwa ngati anali ma bestiez nde pomwe Kayz amapanga ma plan opha matse iyeyo anali kuti?

  • @basheerrazack7976

    @basheerrazack7976

    7 ай бұрын

    Exactly ndipo kell kay anachita bwino ku broker cos amapewa zambiri

  • @jomomagombo9085
    @jomomagombo90857 ай бұрын

    Amu broker bwanji munthu. anga kuti provoice sadabwele poyela kunena kuti kell ndiyemwe wamupha mats .to confirm oyipa athawa yekha. Kell nde olakwa😂

  • @basheerrazack7976

    @basheerrazack7976

    7 ай бұрын

    Inu choyipa ndi chabwino mumasiyanitsa bwanji?

  • @KaSoKa-tr1rf
    @KaSoKa-tr1rf7 ай бұрын

    kape iwe uzizitsata staff wanva wandithera bundle ndi maboza akowo .provoice sananene kut Mulungu adzabweza no ukufufuza za Bodza ayse ONLY GOD KNOWS samatanthauza kut kellz anapha Martse koma a Kellz amangozinyumwa okha bas pot amat choipa chitsata mwini

  • @sammalvitha

    @sammalvitha

    7 ай бұрын

    Invetsen nkhan Yonse kachiwiri big

  • @KaSoKa-tr1rf

    @KaSoKa-tr1rf

    7 ай бұрын

    @@sammalvitha big muli ndi mbali inuyo vuto lake

  • @thokojona9686
    @thokojona96867 ай бұрын

    Osamaikira kumbuyo zilizonse

  • @CharlesBanda-lb4kw

    @CharlesBanda-lb4kw

    7 ай бұрын

    Mponso

  • @user-rr2yo3hy7i
    @user-rr2yo3hy7i5 ай бұрын

    Eeeeeeh zakumva zipweteketsa mutu koma nkhan ndiyot best frnd sangakubloke

  • @auspiciousmackinah2565
    @auspiciousmackinah25657 ай бұрын

    Iweyo Samu Uli Mbali yandani... provoice ndi Oimba kuyambila kale wanva... Ngati ukuopa achina kell usamakambe nkhani zabodza Wanva

  • @CharlesBanda-lb4kw
    @CharlesBanda-lb4kw7 ай бұрын

    Only God knows

  • @TendaiBongololo-fh6uk
    @TendaiBongololo-fh6uk7 ай бұрын

    Following

Келесі