Пікірлер

  • @marykaunga-cm1dd
    @marykaunga-cm1dd Жыл бұрын

    Kumalawi chilichose chokanika😅😅😅

  • @listongelocechisundakaro4901
    @listongelocechisundakaro4901 Жыл бұрын

    Mwayankhula bwino kwambr 🤙🤙sitikupitad patsogolo.

  • @mollymasangano473
    @mollymasangano473 Жыл бұрын

    Zowona achimwene, koma ife a Malawi 🇲🇼 ♥️ timayimba za akunjako,koma akunjawo sayimba Zathu yetsetsani kusitha ndikuti Malawi 🇲🇼 ♥️ 😀 Akhale Map.

  • @Wholelottadynasty
    @Wholelottadynasty Жыл бұрын

    For that international artist to promote your song its due to an agreement most of the time akumalawi akapanga collabo they don’t pay that particular artist to promote their song bola collabo yatheka 😢

  • @user-id1qw2zv4g
    @user-id1qw2zv4g Жыл бұрын

    Ndavumelezana nawe bro kwambili kwake koma anthu samazawa, wokha ngati ma artist amagofuna kuchuka kuti anayimba ndiwakuti basi 😢😢tikusalila kwambili serious

  • @user-lb5ev2ob8l
    @user-lb5ev2ob8l Жыл бұрын

    Is true

  • @grantmphamba6772
    @grantmphamba6772 Жыл бұрын

    Vutonso lina kubera kwambiri amalawife mwa chitsanzo nyimbo ya ku zambia kungoinva kuma yambiliro umatha kuziwa kuti iyi ndi zambian music pomwe kwanthu kuno mmm nyau king mwina

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Жыл бұрын

    Ku Malawi palibe otchuka....kuimaiko akunja..Bolaninso AGIDDES CHALAMANDA.

  • @petersenlameck955

    @petersenlameck955

    Жыл бұрын

    Uncle nkhani siyam'gwirizano ayi anthu mukuwatchulawo ndioti amagona kukhomo kosaseka ndye akapanga collaboration with Malawian artist amangoti ana awa atimitima tankhuku 😂😂

  • @KaSoKa-tr1rf
    @KaSoKa-tr1rf7 ай бұрын

    only gemin major

  • @jcolbeatsmw6348
    @jcolbeatsmw6348 Жыл бұрын

    Bola namadingo

  • @jameswajumpha6790
    @jameswajumpha6790 Жыл бұрын

    Umakwana zoona zenzeni

  • @Kassamajibu
    @Kassamajibu Жыл бұрын

    Ndizoona km ma Artst Athu Ndiozikonda kwambri coz or mmodz sangabwere poyera mkunena kut mwakambazi ndzoona ay palibe chomwe chingasinthe coz aliyense amathamangira Fame mwachangu mchifkwa tikumagwa.

  • @phermade1000
    @phermade1000 Жыл бұрын

    Music is spiritual, its business it needs investment and risk taking

  • @fkizy-9547
    @fkizy-9547 Жыл бұрын

    Khan ndiyoona, , MLW, evn south Africa siima player or nyimbo ya Gwamba yomwe anaimba ndi Ermtee, yo, , nditokhatokha bac, , tieni tiesele ma artist a2

  • @phermade1000
    @phermade1000 Жыл бұрын

    Talk about Gemini major bruh

  • @ezekieldecember3005
    @ezekieldecember3005 Жыл бұрын

    Mawu akulu kwambiri

  • @dannkerrfinily9571
    @dannkerrfinily9571 Жыл бұрын

    Zoona zokhazokha chachikulu ndikungonsintha maganizidwe ndi machitidwe athu a Malawi. Tiziyamba ndi kuzimaliza

  • @Rafique948
    @Rafique948 Жыл бұрын

    Kkkkk kom amalawife nde basi sitidzatheka😅😅😅😅

  • @futsomoliati6033

    @futsomoliati6033

    Жыл бұрын

    😂😂😂

  • @frasernjaidi7462
    @frasernjaidi7462 Жыл бұрын

    Samatha kulemba nyimbo za mutu

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 Жыл бұрын

    Iwe gwelo la zonsezo sukudziwa ..Amphawi dzikolo andale aliwononga

  • @jermahkell8538
    @jermahkell8538 Жыл бұрын

    Ife ndosauka man mayiko amangophweketsa akamva dzina lathu

  • @ShsrfBASHIR-jm7hk
    @ShsrfBASHIR-jm7hk Жыл бұрын

    Nkhinks Sam maveta

  • @jeffmalizan9878
    @jeffmalizan9878 Жыл бұрын

    Umbuli kwathu kuja ndiochokera pakathawi ndipo sindikukhulupilaso kuti pangadzakhale kusinthika kayaa mwinaa

  • @amabhohlela.3492
    @amabhohlela.3492 Жыл бұрын

    Aaaaaah oimba aku Malawi ..koma Chmanga chokazinga

  • @habibuburhani6688

    @habibuburhani6688

    Жыл бұрын

    Mani azazakunamidzeni kuchuka itanachoni dzimachokera ku midima wallah sono amalawi ambili safuna

  • @amabhohlela.3492

    @amabhohlela.3492

    Жыл бұрын

    Absolutely...like achina DAVIDO,,Platinum..Tecno ndiena ambili achina Realwayn ndi oimba oti they sold there souls.

  • @user-jx5kb8pt1m

    @user-jx5kb8pt1m

    3 ай бұрын

    Kkkkkkkkkk kom iiiiiiiiiiiiii amalawi muli nd vuto mukhalila kukamba zazanu kom muthu akachoka maso mwanu nd pamene muti uja amayimba bwino kom pano muli bz kumunen

  • @user-cg2qv4fr5o
    @user-cg2qv4fr5o Жыл бұрын

    Ndizowonadi

  • @ronaldbysonchisale2110
    @ronaldbysonchisale2110 Жыл бұрын

    Mkasa waimba kale zomwe zinachitika zaka zapitazo

  • @MrTubeme3333
    @MrTubeme333311 ай бұрын

    Illuminati sanaidziwe basi...they need to sacrifice more

  • @user-fe2rq6to6z
    @user-fe2rq6to6z Жыл бұрын

    They have to carry a Malawian genre in there music and promote it and not copying from others ,,try to copy amapiano beats and go to South Africa to perform you will see the different between SALT and SUGER

  • @raffiqmohmoud1997
    @raffiqmohmoud1997 Жыл бұрын

    Mwaiwala Gemini major Malawian based south Africa

  • @sajamalawi6978

    @sajamalawi6978

    Жыл бұрын

    Ase Gemmi Ali pa international and He is from Malawi

  • @raffiqmohmoud1997

    @raffiqmohmoud1997

    Жыл бұрын

    @@sajamalawi6978 that's y. Ndafusa coz akuti kumalawi kulibe wa international,azinena zoona osati kutinamiza cz ifenso timazisata

  • @sammalvitha

    @sammalvitha

    Жыл бұрын

    Koma. Sakhala ku Malawi et?

  • @sajamalawi6978

    @sajamalawi6978

    Жыл бұрын

    Nanga wende Halawa ukumutchulayo amakhala ku Malawi???? Iyeso sakhala ku Malawi koma zimamuvuta choti muziwe ambili Ali pa international aja satanic is only secret

  • @sajamalawi6978

    @sajamalawi6978

    Жыл бұрын

    Diamond mukukambayo tafufuzeniso bwn bwn si colabo yokha inapangisa fame yake note that

  • @kelvinkay2090
    @kelvinkay2090 Жыл бұрын

    Nkhaniyo ndi yoona

  • @user-fo7tc7ti7q
    @user-fo7tc7ti7q Жыл бұрын

    Mukuona kwanga khani ndiyoti alimbikire ku imba nyimbo za English chifukwa ndiichi Tanzania amaimba swahili ndichiyankhulo chomwe chili ndimaiko angapo mu Africa pomwe South Africa dzikolawo limatsatidwa ndianthu ambili chifukwa choti dziko lawo muli anthu ambili obwela mayiko osiyana siyana ndi pomwe ganah Nigeria amaimba English

  • @chigokhalid9420
    @chigokhalid9420 Жыл бұрын

    Main point ndiyakut zimafunika kumaimba mwa chizungu, munthu akukaimba mu chichewa wa ku Nigeria anvela bwanj ngat akunva

  • @amunaachisale6120

    @amunaachisale6120

    Жыл бұрын

    Diamond Platnumz unamuva akuyimba chizungu??

  • @amunaachisale6120
    @amunaachisale6120 Жыл бұрын

    Zanzeru

  • @Prince_Luda_145
    @Prince_Luda_145 Жыл бұрын

    😂😂😂kumalawi mkokoma

  • @ChisisiMaliko-xu6qf
    @ChisisiMaliko-xu6qf Жыл бұрын

    Kkk zowonadi

  • @francokaunga2707
    @francokaunga2707 Жыл бұрын

    Problem is language chewa is nonsense language! Every one must sing in their own Language.

  • @Razarusmbavachakwera
    @Razarusmbavachakwera Жыл бұрын

    Kupitapatali khaya osapita ndilibenazontchito zmenezo

  • @noelmaere6595
    @noelmaere6595 Жыл бұрын

    Zimafunika record company for promotion

  • @lovemorebishop-ud7ir
    @lovemorebishop-ud7ir Жыл бұрын

    Kma taygrin atleast amaesesa

  • @ibrahimtutini5862
    @ibrahimtutini5862 Жыл бұрын

    Zoona

  • @mussahthemba9397
    @mussahthemba9397 Жыл бұрын

    That's truths

  • @jameskaponya6275
    @jameskaponya6275 Жыл бұрын

    Well said

  • @umalibakali9033
    @umalibakali9033 Жыл бұрын

    😄😄🔥🔥🔥🔥🔥

  • @amosimvumaamov3840
    @amosimvumaamov3840 Жыл бұрын

    Zowona ku malawi kulibeoimba video sizabwinoso

  • @jayjayb065
    @jayjayb065 Жыл бұрын

    That is true

  • @vanalphamphaya3518
    @vanalphamphaya3518 Жыл бұрын

    Thanks that's true

  • @ChikondiGasten-wv5lk
    @ChikondiGasten-wv5lk Жыл бұрын

    Enawa ndi zakumadzi bas chifukwa pamene anafika Gemini major (rudebwoy) mmm guyz samayenera kubweleraso mmbuyo ngat apap

  • @sajamalawi6978
    @sajamalawi6978 Жыл бұрын

    Ndesukuziwatu zanechill anaimba kut ndachokera kwathu ku Malawi Ali pa international market

  • @sammalvitha

    @sammalvitha

    Жыл бұрын

    Hahahahaha

  • @kljmw2023
    @kljmw2023 Жыл бұрын

    amatidyesa ma blue tick ndie tizitani

  • @charleschaponda5390

    @charleschaponda5390

    Жыл бұрын

    First you must be signed to a certain record lebel. Dont use your effort to approach an international artist let ur mananger do that

  • @SirpromiseMatabwa
    @SirpromiseMatabwaКүн бұрын

    China Satanism yake ikhale yokwanira😅😅😅😅

  • @gracianbinali2272
    @gracianbinali2272 Жыл бұрын

    😂😂😂 Koma Yap Kulankhula2 Km Janta Chanel O Nyimbo Ya Khumbe Bwanji Timaonera Ku SA Chanel O

  • @sibubrightcmasulanphiri3652
    @sibubrightcmasulanphiri3652 Жыл бұрын

    Mwathoka ngamo bro ndipo ndi zedidi zomwe mwanenaz

  • @GSyphi_mw
    @GSyphi_mw Жыл бұрын

    😤😤😤

  • @LigaalexAlex-zp7yj
    @LigaalexAlex-zp7yj Жыл бұрын

    That is true

Келесі