Chenjerani Ndi Akuba Pa Internet

#malawi #trending #news

Пікірлер: 24

  • @TimothyMoyendah-ih1qq
    @TimothyMoyendah-ih1qq17 күн бұрын

    😢😢😢😢pepani kwambili

  • @MuhaShaibu
    @MuhaShaibuАй бұрын

    Akaidi awa ..amankhala anthu akundende ..ma prisioners ..

  • @user-kw2do9wf3c
    @user-kw2do9wf3cАй бұрын

    Ndiye paliso ena pa social Amati ndi azising'añga ine ndiye andibera mokwana okwana 7

  • @user-ei2yt3kf4x
    @user-ei2yt3kf4xАй бұрын

    Olo ine ndabeledwa ku besa R2000 kenako kuyamba kusowa ndiwo iiiii ayi

  • @FrancisStima-sc7zs
    @FrancisStima-sc7zsАй бұрын

    Kkkkkkkkkkk kufuna ndalama yosavutikila et mudziona

  • @ChiefJustin-cl8jl
    @ChiefJustin-cl8jlАй бұрын

    Basi kulimbikila kugwila tchito ndi njila yokhayo basi pangako ganyu kapena ayi kabisinesi kangachepe

  • @user-kw2do9wf3c
    @user-kw2do9wf3cАй бұрын

    iiii alipo ambiri. akubawo ineso umboni ndili nawo ndikukupaseni ma nbr ndibupasani

  • @AlexAlexandla-vr1wh
    @AlexAlexandla-vr1whАй бұрын

    Ndi ayawo akumapanga zimenezo

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6noАй бұрын

    Adzapezeka ndi mneneri wabodza

  • @samsonyuda674
    @samsonyuda674Ай бұрын

    Babo asapesa ndi zoonadi ineso zinadichitiki ndili ndi umbone ose moti ndinabesa ndalama

  • @user-xq2mv7jl5m
    @user-xq2mv7jl5mАй бұрын

    Chonde abale anga, chinsinsi choti ukhale ndi moyo ochita bwino ndi chimondzi chokha "KUCHIRIMIKA, KAPENA KUTI, KUGWIRA NTCHITO NDI MPHANVU ZAKO".

  • @mellipherjohn7158
    @mellipherjohn7158Ай бұрын

    akuba avutatu mmmm

  • @Vickb-sz6dk
    @Vickb-sz6dkАй бұрын

    😢😢😢😢😢😢

  • @ChristinaNyirenda-zb1if
    @ChristinaNyirenda-zb1ifАй бұрын

    Mmmm kma abale mulungu alowelelepo

  • @MuhaShaibu

    @MuhaShaibu

    Ай бұрын

    Amankhala anthu akundende awa ma prisoners ...akaidi

  • @danielsulani8689
    @danielsulani8689Ай бұрын

    😢😢

  • @user-xq2mv7jl5m
    @user-xq2mv7jl5mАй бұрын

    Mavuto 😢😢😢😢😢

  • @user-bb5iy7ry5h
    @user-bb5iy7ry5hАй бұрын

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @fannyzimba149
    @fannyzimba149Ай бұрын

    Kuchita kudziwikilatu kuti wakuba uyu mmmm zokamba zake mmmm Mulungu akuyendereni muyaluke komwe muliko

  • @philipoga2401
    @philipoga2401Ай бұрын

    amalawi kupusa anthu ali kundende kale milako ichoka kuti ali ku chichili phulizoni

  • @user-ol1hf7ru1v
    @user-ol1hf7ru1vАй бұрын

    Mulungu amukatha munthu ameneyo ndithu mmmm😢😢😢😢

  • @unarinematshomo2841
    @unarinematshomo2841Ай бұрын

    Mauwo ngati nyapala, koma kumalawi eeeee mbola zokhazokha.

  • @emiliaumali8360

    @emiliaumali8360

    Ай бұрын

    Ndi emweyo😅😅😅

  • @unarinematshomo2841

    @unarinematshomo2841

    Ай бұрын

    @@emiliaumali8360 kkkkk koma iwe usanditseketse.

Келесі