I watch there real fights amangokokana ma jacket panalibe olesetsa
@emmammatsa12845 жыл бұрын
Mr Ken Msonda ndiwo akhala akulandira ndalama ku zipani zosiyanasiyana...ndiponso bambo Msonda is very defensive he doesn't know how to respond to the questions...
@argentchilanga79086 жыл бұрын
koma ndiye kkkk
@omarlux94025 жыл бұрын
Ine sonda amandiyasa ndiwadyela kufuna ndalama bas
Choka khumba dyela iwe nsonda wakhala ngati hule mukufuna chiyani mzipani zonse choka!!!!! Ukukana chulungamo iwe
@graciankanyanthama53057 жыл бұрын
😂😂😂😂Msonda no.1
@lastnumber66643 жыл бұрын
Kikkkkkkkkkkk Mr can mumaitha
@harrisonbanda51007 жыл бұрын
Wakumana nazo, amadutsa m'mbali Brian
@mankemisomthombeni46056 жыл бұрын
Brian wadya masikono Ku chipan cha chilima ?? ndichifkw Aku chuluka xeru
@Leonardmposahjnr Жыл бұрын
Koma msonda-yu 😂😂😮
@mankemisomthombeni46056 жыл бұрын
Koma Na APA guys kkkkkkk msonda wayankha poganizira mawa guys km brayn akanaimika manja mn
@user-qp2zu1ye7y9 ай бұрын
Problems kindly don't oppress the reporter please
@bashirfaida13736 жыл бұрын
Koma Brian apa unakumananazo apa yachiwiri kansayila
@samuelkusah78016 жыл бұрын
KKKKKK chitsiru Brain kkkkkk waperelatu koma kkkkk
@fahadwalipeya865613 күн бұрын
Asonda oshota aaa
@martinmulenga58502 жыл бұрын
😂😂😂lemme laugh & sleep
@emmammatsa12845 жыл бұрын
A Brian muzinyozedwa kwabasi ndi anthu opanda nzeru, l would advice if you meet such kind to adjourne the interview constructively 😂munthuyu akuoneka kuti mawaya ena sakuyenda bwino mmutu mwake...mpakana kuti mwadya masikono a Brian...shaaaaa!!!
Kodi tikupindulanji panopa tingopeza njira zokonzera mavutowa basi
@damsonqassim97446 жыл бұрын
Kkkk Msonda sazatheka
@orphanmdyali82822 жыл бұрын
Koma ntchito zinazi! Eee! Nzofunika kulimba mtima komanso kupirira!
@matolabokelo69045 ай бұрын
😂 koma msonda ndi fire 😂😂
@omarlux94025 жыл бұрын
Iwe ungathandize ndani zakuba chisilu
@user-to5of3ks3g8 ай бұрын
Mdala ameneyu alimbe zeru
@oscarsolola-sj7dk Жыл бұрын
This interview 😂
@jossamjulius22975 жыл бұрын
Ati eti Brian amayima kutchalichi kutsogolo nkumalalikila, aaaah ine ndiye mpaka nnditadzuka nkutuluka, ndiponso mpingowo ndiusiila pomwepo. Ngatidi Brian malalikila za mulungu, ayi ndithu chikayiko chilipo ngati mulungu wake ali yemwe tikumudziwayi, kapena mwina mulungu wa Chakwera.
@johnmark336
Жыл бұрын
🤣 🤣 🤣
@dodosiahmadu97425 жыл бұрын
brian sadadyeso bazi koma inuyo msonda ndimene ddp yakupasa chigumu kapena kuti wakupasa chikonda moti iiiiimuthu otengeka udzafela moyenda
@Chifundo-ph1gsАй бұрын
Asonda nd katundu
@jossamjulius22975 жыл бұрын
Ayi ayi ayi Penapake Brian amaonjeza. Kodi DPP inamulakwila chiyani? Ndiye kuti munthu akaphatikizana ndi DPP baasi akhale mdani wake ati ndithu Brian chepetsani uchitsiru wanu. kkkkkkkk koma apapa ndiye akumana nazo. ina ndi ija ya Kunsaila kukuthirani nonse moto ndi chitsiru chinzako Kasakula kkkkkk, wayalikadi Brian.
@user-pc7hj7hs5v2 күн бұрын
Koma Brian ndaseka 😂😂😂😂 ndy mudyera kuti nanga Mesa mumadyela mu ndale
Пікірлер: 141
I've watched so many interviews from B B he is very professional and intelligent
Many thanks should to u Mr Brian Banda for a great job ur doing, ur speaking behalf of fellow Malawians
I can't stop listening to this program, i laugh one wayyyyyyyy🤣🤣🤣🤣🤣
@johnmark336
Жыл бұрын
Me tooo🤣🤣🤣
@LukeshadrickShadrick
7 ай бұрын
Also me am very laughing more
🤣 🤣 🤣 🤣 Who is with me in 2023?
Kikikii akuti even buluzi amakhala ndi ambition yofuna kukhala ng'ona. Interview iyiyi 🙌
Who is here still 😂😂😂
Brian Banda the great i always follow you BB my man
It doesnt get old... 2023, 30 august... A nsonda tikuziwana ngati munthu oshota..
ndikudabwa nanu a Brian, mwadya maskino kwandani😄😄😄
KeNsonda umatha kumuphwetsa Brian
Haha Ken Msonda. I owe you 1 . Umatha👍😂
That was fire for fire
Never gets old😂😂💣
Am here again
😄😄😄😄ndikudabwa nanu a Brian, mwadya maskino kwandani😄😄😄
Masiku sakoma onse Brian 😀
Mr msonda man of answer 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
Ken Msonda Ndiwamzeru kwambiri
Brian wadya masikono angat lero kkkkkk waziona Brian
Thank you Brian for your patient when you're on duty ,, Msonda is Useless
Adara bambo brayan🔥🔥🔥
Brayn katifusile kwa nsogoleli wanu chakwela kut chiloweleni mb'oma, musamalimbane ndi amisalawo wakalamba mwasala pang'ono kufa ameneyo
Best politician 😂😂😂
Brian Banda
kkķkkkkkkķ wakumana nazo Brian msonda koma guys inu eish ndale ku Malawi
nsonda ayayayayayaa
Kkk msonda ndi fire Kwa fire❤!!!
msonda dyera ameneyu
Brian banda ndi machine
Achina Msonda.!!! Mashini!! Brian wachepa akayambirenso
@mercythom5868
8 ай бұрын
Ndipo kwambiri
Amen Nsonda..kkkkl
Msonda ndi dolo🤣🤣🤣
Palibe yankho ngakhale limodzi limene ntolanlhani wathuyu anawafunsa a sonda,ayankha...ansonda sanayankhe chilichonse....ansonda adzitenga ngatii odziwa koma tikamvvetsera bwinobwinoo....ansonda ...angonyozapo ntolankhaniyu apa....
Answer the reporters not asking him, his job is to ask
Hahaha this interview was too personal. 🤣🤣🤣🤣
@johnmark336
3 жыл бұрын
Too mch personal oooooh!!!!!!
malawis finest Brian Banda😂❤
Brian iweyo umatha, msonda has lost his temper komano u r trying to keep calm.
Kkk inu mdazolowera kuyankhula koma kumeneko mlimba " fire to fire"
A Brian leave awawa akuoneka kuti adya zambiri kiki kiiki ndi mamuvu awo.Time will come the truth shall prevail, not too far
kkkkkkkkk msonda ndimunthudi wandale amaziwa kuyankha mwandale
Asonda lakula ndidyera.aiwala zomwe ananena pambuyo
I watch there real fights amangokokana ma jacket panalibe olesetsa
Mr Ken Msonda ndiwo akhala akulandira ndalama ku zipani zosiyanasiyana...ndiponso bambo Msonda is very defensive he doesn't know how to respond to the questions...
koma ndiye kkkk
Ine sonda amandiyasa ndiwadyela kufuna ndalama bas
Ansondaaa mapazi awo
Interview iyi ikufunika ina
msonda muthu wachilungamo sayenda yenda amayima PAMODZI woooonama inu msonda
kkkkk Nsonda amakwana
Uyutu akuti ma files ose ada chita delete
@clifton1952
5 жыл бұрын
Kikikiki
umayesa dxida brian banda
Apa nde a Brian adanyika amafusa mbwelera🤣🤣🤣🤣
kuyamkha kuona pa mawa kkkķkk
💪💪💪🔥💯🤣🤣
Choka khumba dyela iwe nsonda wakhala ngati hule mukufuna chiyani mzipani zonse choka!!!!! Ukukana chulungamo iwe
😂😂😂😂Msonda no.1
Kikkkkkkkkkkk Mr can mumaitha
Wakumana nazo, amadutsa m'mbali Brian
Brian wadya masikono Ku chipan cha chilima ?? ndichifkw Aku chuluka xeru
Koma msonda-yu 😂😂😮
Koma Na APA guys kkkkkkk msonda wayankha poganizira mawa guys km brayn akanaimika manja mn
Problems kindly don't oppress the reporter please
Koma Brian apa unakumananazo apa yachiwiri kansayila
KKKKKK chitsiru Brain kkkkkk waperelatu koma kkkkk
Asonda oshota aaa
😂😂😂lemme laugh & sleep
A Brian muzinyozedwa kwabasi ndi anthu opanda nzeru, l would advice if you meet such kind to adjourne the interview constructively 😂munthuyu akuoneka kuti mawaya ena sakuyenda bwino mmutu mwake...mpakana kuti mwadya masikono a Brian...shaaaaa!!!
Msonda kukanika kuyankha mafunso momwe amayenela kuyankha nchifukwa chake tomato mnthu akakula azivomeleza nkumasiyila achinyamata ndale ichi ndichisilu chamnthu chimsonda
Koma asonda mpatali
Hahaaa ati ansonda timakudziwani ndinu oshota hahahaha
@mankemisomthombeni4605
6 жыл бұрын
Thokozani Tebulo kkkkkkkk
😂😂😂😂🖐️🖐️🖐️🖐️ iii BB
politicians there Crux
This msonda has no respect, shame on him
Komatu mafunzowa palibe funzo lolakwikatu apa. Koma a ken msonda anali ndi mawu kukhosi
kkkkkk koma
Bwana brian banda inuo matha😂😂😂
Msonda ndale zakuvutani
Zakumanatu apa
Aa mutu wanu Amsonda siukugwira bwino tchito zikungooneseratu kt ndale utazitenga uipa umayambanazo misala ,Brian akukufunsani mafunso inu zimene mukayakha zinanso zosagwirizana ndi funsolo kodi mwatopananzo ndale kulibwino kungosira ena chifukwa zimene mukuchitazi muzichititsa manyazi ana anu
tiyeni timange dziko zinazi tichedwa nazo
panabeba apa. tidzikhala tikubwerezabe zimenezi
eish politicians
@eversonnhlovu183
6 жыл бұрын
Eee koma akuyankha
😂😂😂😂😂 Brian sakuwaziwa achina msonda 😂😂😂😂 ndege ndinakwera pompano ndinapita ku china
Kkkkkk
Brain anafusa mafutso mbola msonda umakwana hahahhahahahha
Kodi tikupindulanji panopa tingopeza njira zokonzera mavutowa basi
Kkkk Msonda sazatheka
Koma ntchito zinazi! Eee! Nzofunika kulimba mtima komanso kupirira!
😂 koma msonda ndi fire 😂😂
Iwe ungathandize ndani zakuba chisilu
Mdala ameneyu alimbe zeru
This interview 😂
Ati eti Brian amayima kutchalichi kutsogolo nkumalalikila, aaaah ine ndiye mpaka nnditadzuka nkutuluka, ndiponso mpingowo ndiusiila pomwepo. Ngatidi Brian malalikila za mulungu, ayi ndithu chikayiko chilipo ngati mulungu wake ali yemwe tikumudziwayi, kapena mwina mulungu wa Chakwera.
@johnmark336
Жыл бұрын
🤣 🤣 🤣
brian sadadyeso bazi koma inuyo msonda ndimene ddp yakupasa chigumu kapena kuti wakupasa chikonda moti iiiiimuthu otengeka udzafela moyenda
Asonda nd katundu
Ayi ayi ayi Penapake Brian amaonjeza. Kodi DPP inamulakwila chiyani? Ndiye kuti munthu akaphatikizana ndi DPP baasi akhale mdani wake ati ndithu Brian chepetsani uchitsiru wanu. kkkkkkkk koma apapa ndiye akumana nazo. ina ndi ija ya Kunsaila kukuthirani nonse moto ndi chitsiru chinzako Kasakula kkkkkk, wayalikadi Brian.
Koma Brian ndaseka 😂😂😂😂 ndy mudyera kuti nanga Mesa mumadyela mu ndale
Kkkķkk musonda magogo musiyeni
Koma mdonda
Koma na iyi yokha nde kkkkkkkk
@chipilirotchapo55
5 жыл бұрын
Kkkk akumana nazo banda
@vinnie1nyirenda755
9 ай бұрын
Ndikuziwani ngati munthu oshota