Bakili MULUZI TV 30 June 2024

Ойын-сауық

Пікірлер: 45

  • @Jafaliwathombo
    @Jafaliwathombo2 күн бұрын

    Umatha nkulu, keep it up for giving us update chilungamo chiziwika

  • @johnmiselo2230
    @johnmiselo22302 күн бұрын

    Keep it up 💪👍💪👍💪💪 we. Love your channel 😊

  • @FrancisKazembe-og4vh
    @FrancisKazembe-og4vhКүн бұрын

    Watching from uganda

  • @victorchidothi-gd8bu
    @victorchidothi-gd8bu2 күн бұрын

    Indeed history is the best teacher, best TV ever. Big up boss

  • @user-vo9ie2gv7o
    @user-vo9ie2gv7o2 күн бұрын

    Ichi ndi chilungamo cheni cheni, tikufuna chilungamo komamso mayankho pamafumso ambiri omwe a Malawi tili nawo pa ngozi imeneyo apo biiii MCP I kupitiliza ntchito zake zokupha

  • @andrewjohnsiwinda7050
    @andrewjohnsiwinda705011 сағат бұрын

    Go up bro mumatiimilila

  • @user-um6yo6nc3e
    @user-um6yo6nc3e2 күн бұрын

    Chakwela ndi M"kulu wa z i Gawenga za MCP

  • @user-vo9ie2gv7o
    @user-vo9ie2gv7o2 күн бұрын

    Ndinene ndi inu amene mukudana ndi chilungamo kuchokera pa chanel ichi, kuli bwino mukhale chete ino sinthawi ya chipani chimodzi ayi

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h2 күн бұрын

    ❤❤❤ keep it up brother

  • @user-et5nz4vz2v
    @user-et5nz4vz2vКүн бұрын

    Best TV ever

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg2 күн бұрын

    MCP ndiyakupha ndp agalu amenewa aziwon

  • @rashidadan2533
    @rashidadan25332 күн бұрын

    Inshort , MCP is a terrorist government , apapa wina aliyense akudziwa ndipo avomeleze , Komanso chosangalasa ndichoti chakwela ndi ndunazake azabweza pavute olo pasavute

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283Күн бұрын

    Ndege yagwa koma Chilima ali ndi mabala a zikwanje.

  • @user-st6bt5vv9c
    @user-st6bt5vv9c2 күн бұрын

    Kukuyu tafotokoza bwanji popeza agwira ntchito chakuphachi

  • @user-lc3sw8iz2g
    @user-lc3sw8iz2g2 күн бұрын

    Boma ili likachoka TIMVA ZENI ZENI.

  • @MorganBanda-oc2jx
    @MorganBanda-oc2jx20 сағат бұрын

    listening and watching....😊

  • @ayamijackson1443
    @ayamijackson14432 күн бұрын

    I salute youm

  • @user-ji3in4cp3m
    @user-ji3in4cp3m2 күн бұрын

    Mcp ndiyoipa hvy 😭😭

  • @user-ir8dd8lm1c
    @user-ir8dd8lm1c2 күн бұрын

    Eeeeeesh this world 🌎😢

  • @KazembeSemion
    @KazembeSemion2 күн бұрын

    Chilungamo

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8oКүн бұрын

    Wa bakili uyu ndi chitsiru

  • @andrewjohnsiwinda7050

    @andrewjohnsiwinda7050

    11 сағат бұрын

    Opusa ndiweyo

  • @DixonKanjoka
    @DixonKanjokaКүн бұрын

    4 r😊

  • @Littlefair7
    @Littlefair72 күн бұрын

    Koma channel yanuyi bwanji imatumiza ma video a ma channel ena? Izitu youtube imaletsa, musamazitenge chimalawi zinthu, this is a global community, you need to stop this tendency.

  • @JamesIngeni-ku3qj

    @JamesIngeni-ku3qj

    2 күн бұрын

    Who is complaining and who are to complain are you spoke person for you tube

  • @SameKaposa

    @SameKaposa

    Күн бұрын

    Kagwere uko iwe wa mcp

  • @Littlefair7

    @Littlefair7

    Күн бұрын

    ​@@SameKaposa Bulutu, unabadwira mu chipani cha ndale? Mbuzi. Mutu ngati bondo.

  • @yamikanichirwa9787

    @yamikanichirwa9787

    Күн бұрын

    😂😂😂😂😂

  • @Littlefair7

    @Littlefair7

    Күн бұрын

    @yamikanichirwa9787 Club Junta 🤣🤣 vuto lake aliyense akufuna kukhala ndi channel koma alibe ma plan.

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m2 күн бұрын

    anthu awa asiyeni asanene chilungamo Koma thawi idzabwela

  • @PetroMatias
    @PetroMatias2 күн бұрын

    Veleveli sipomani

  • @ShentrycChinoko
    @ShentrycChinoko2 күн бұрын

    Kwachela mabodza usikuwose umaganiza mabodza basi eeee azibambo ngati azimayi

  • @peterchikwakwa8476

    @peterchikwakwa8476

    2 күн бұрын

    Ngati amalankhula zabodza then don't follow him

  • @peterchikwakwa8476

    @peterchikwakwa8476

    2 күн бұрын

    Pali ma channel ambiri pa U-TUBE pano umati kutsekura kuwona wekha kuti aaaaa izizi ai

  • @peterchikwakwa8476

    @peterchikwakwa8476

    2 күн бұрын

    Zimangotengera interest Yako mmene ilili

  • @InnocentMlowoka-ew4lo

    @InnocentMlowoka-ew4lo

    2 күн бұрын

    Our lecture in history is here, ngati zakubowani siyani kuvetsela, this is not 1970s myaluka athu akupha inu, ziwe lang'ona, anthu oipa.

  • @Ishmael376

    @Ishmael376

    2 күн бұрын

    Tell them​@@InnocentMlowoka-ew4lo

  • @earltamimo8660
    @earltamimo86602 күн бұрын

    Satanyahu

  • @ShentrycChinoko
    @ShentrycChinoko2 күн бұрын

    Kod akulu inuyo uthenga wanu umalimbikitsa zotani kudziko mobodza sangakupindulileni abambo

  • @petertaulo8014

    @petertaulo8014

    2 күн бұрын

    Opusa iwe mchewa ofunika kuti usukusule maso ako

  • @richardbanda9997

    @richardbanda9997

    Күн бұрын

    Pangani kafukufuku ngati akunama mutiuze zoonazo inuyo. Mukufuna zoti aMalawi asadziwe chilungamo?

  • @rashidadan2533
    @rashidadan25332 күн бұрын

    Inshort , MCP is a terrorist government , apapa wina aliyense akudziwa ndipo avomeleze , Komanso chosangalasa ndichoti chakwela ndi ndunazake azabweza pavute olo pasavute

  • @harrispheleni2205

    @harrispheleni2205

    2 күн бұрын

    Uja anati too much turbulence? Inu nde odziwa?

Келесі