BAKILI MULUZI TV 2 JULY 2024

Ойын-сауық

Пікірлер: 339

  • @IbrahndemangaIbrahndemanga
    @IbrahndemangaIbrahndemanga5 күн бұрын

    Best of the best bakili muluzi tv

  • @muhmmadsarwer9527
    @muhmmadsarwer95275 күн бұрын

    Anthu Andale ndiabodza koma awawa eeeeeee awonjeza kwambiri

  • @user-xr3ty6qq5o
    @user-xr3ty6qq5o5 күн бұрын

    Ine n'saname Chakwera amandinyasa

  • @user-ww4ei5fb7d

    @user-ww4ei5fb7d

    3 күн бұрын

    Kkkķķ😅

  • @user-ww9rj2wx8d
    @user-ww9rj2wx8d5 күн бұрын

    Chakwela ndi mfiti kwabasi

  • @DelamoBalacho
    @DelamoBalacho5 күн бұрын

    Best tv bakili muluzi

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda58915 күн бұрын

    Akutivutisadi ng'azi ameneyu 🐬🐊🐊🐊🐬

  • @JeanKambala-gm1zr
    @JeanKambala-gm1zr5 күн бұрын

    Akwanilitsa bwanji kupanga zonsezo ndalama akupatsa anthu akunja kumalemba anthu aganyu Kuti azimpha anthu ndalama zake zomphela anthu

  • @VinsentMwapabwe
    @VinsentMwapabwe5 күн бұрын

    Yes mwamuza zona ZIKOMO kwambili potiziwisa chikhalidwe chake

  • @user-ec4jo9cu4d
    @user-ec4jo9cu4d5 күн бұрын

    😂😂😂😂😂ati kagowero kkk km naseka bwanji

  • @FrancisKazembe-og4vh
    @FrancisKazembe-og4vh5 күн бұрын

    Watching from Zimbabwe

  • @raytavares2256
    @raytavares22565 күн бұрын

    Ifee nga ngaa nga nga pambuyo pa ngwazi yamuyaya Dr LAZURUS CHAKWERA wathu wokendedwa 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤

  • @ChristopherMakamo-ky4pq

    @ChristopherMakamo-ky4pq

    5 күн бұрын

    Galu wachabechabe iwe

  • @harrisbanda5891

    @harrisbanda5891

    5 күн бұрын

    Chokani apaa mwana wang'ona iwee, mwapha chilima asatana inuu 👹👺👿☻ , kunali ng'azi ina mdzaka zammbuyozo mumkaitchulanso kuti ngwazi, , lero alikuti?

  • @ZenusKabwili
    @ZenusKabwili5 күн бұрын

    Aaaaa koma kunena zowona kutengela mmene analonjezela zambiri szinatheke 😢

  • @user-qq1uj7ct6n
    @user-qq1uj7ct6n5 күн бұрын

    Kunkuyu umve zimene ndikunenazi,, iweyo ndi amene akumuuza zabodza chakwera wakoyo. Achakwera mumve Mau angawa,, kunkuyu akukunamizan ndi mfundo zake zopeperazi. Chifukwa iyeyu akukulimbikisan kukuuzan zabodza zomwe amalawi Eni ake sakukondwera. Muzafa ifa yowawa.

  • @Concerned320
    @Concerned3205 күн бұрын

    Best TV ever..may God continue protecting you Bakili Muluzi TV

  • @user-ep6ro8uk6e
    @user-ep6ro8uk6e5 күн бұрын

    😅😅😅😅koma anthu.inu musandisekese akut akaziwo mimba nguuu ngat mbuzi yakhuta mphale yokuba

  • @user-zr5oc3rg2c
    @user-zr5oc3rg2c5 күн бұрын

    Kkkkkkkkkkkk koma brother mumatha Inu mudzangokhala president ndinuyo chaka chikubwerachi

  • @SymonNamalomba-sh3fu
    @SymonNamalomba-sh3fu5 күн бұрын

    Olo chimodzi palibe chomwe wapanga iye, 30minutes olo itakhara non stop sizingatheke ayi ,

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x5 күн бұрын

    Boss mwaiwalatu chitukuko China chomwe MCP yapanga kupha Ralph ndi Chilima

  • @user-fd1tu6ku1r
    @user-fd1tu6ku1r5 күн бұрын

    Mr Kamwendonjira okudya Matako agaluwa sangawine Chisankho in the Next Polls

  • @Aisha-db6ds
    @Aisha-db6ds5 күн бұрын

    Kunkuyu mapwala ake ndithu

  • @MosesPhiri-l6e
    @MosesPhiri-l6e5 күн бұрын

    Let me correct you in Mzimba sugar ndi k 2495 in big mart shop ya fair price Chakwera dziko lamukanik passport anasiy kupang ndet only in lilongwe zoona zak achinyamat ntcht njee Achoke I will support that

  • @user-qx3dd7xt9c
    @user-qx3dd7xt9c5 күн бұрын

    😂😂😂 bon voyage kkk da gama emweyo wa gowelo

  • @BishopMaxwell
    @BishopMaxwell5 күн бұрын

    Afune asafune 2025 azaluza akumkuyu akumpusitsa kape wawoyo

  • @user-hm9nc7lz6e

    @user-hm9nc7lz6e

    4 күн бұрын

    Onse ndi amagazi mmanja kumkuyu sakudziwa comwe akuyakhula

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf5 күн бұрын

    kumkuyu ma chende abambo ake chakwera ndi mcp ndizigawenga za kupha anamupha chilima mcp ndi chipani chazigawenga zitsiru zokha zokha

  • @WittinessBeza-cp5kf

    @WittinessBeza-cp5kf

    5 күн бұрын

    Chakwela mumuone khope yakeyo chigawenga cheni cheni akakhaka mkaka ngati wagwa kotamba

  • @georgechikonje4904
    @georgechikonje49045 күн бұрын

    Best TV station in Malawi so far.

  • @user-mi3fw1zg8b
    @user-mi3fw1zg8b5 күн бұрын

    Ali Maso rwaa! Ngati Nazikambe kkkkkkk koma Manganya😂😂😂

  • @vinceynyone6693
    @vinceynyone66935 күн бұрын

    Ndaonadi nkhope yamfitidi

  • @Moses51
    @Moses515 күн бұрын

    Best TV in Malawi keep

  • @DanMwatchipitsa
    @DanMwatchipitsa5 күн бұрын

    Chitumbili chingwile pangali mbwaa in 2025😂

  • @JjhdshkKfdsahk
    @JjhdshkKfdsahk5 күн бұрын

    I trust bakili muluzi TV always because is talking true

  • @user-pi8mz3bx9n
    @user-pi8mz3bx9n5 күн бұрын

    We really appreciate for this channel

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda58915 күн бұрын

    Koma ada awa amatha kwambiri, kuwelenga mwachifase ndimodekha

  • @user-vb1iq5un5p
    @user-vb1iq5un5p5 күн бұрын

    Koma pa udindo wa upulezidenti uja umafunika kukhala okhwima nzeru.😂😂😂akt amakajambulitsa zithunzi ku china akazawo Ali pompo ..

  • @rashidlamos3403
    @rashidlamos34035 күн бұрын

    Thanks brother for news

  • @GreenMwachande
    @GreenMwachande5 күн бұрын

    Kkkkk akuti umange gowero Garu iwe

  • @oneriaChiwaula
    @oneriaChiwaula4 күн бұрын

    I like this TV keep the fire burning dude

  • @user-hq6dq7zr1e
    @user-hq6dq7zr1e3 күн бұрын

    Zomwe wakwanitsa ndi kupha ndikumanga osalakwa

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda58915 күн бұрын

    Chilichonse chamoyo chikàmaphedwa sichilephela kuphupha chikamafa , umu ndimomwe chikuphuphila chipani cha magazi cha mcp killing party

  • @ORTONPHIRI-i1z
    @ORTONPHIRI-i1z5 күн бұрын

    Chakwera chomwe wa kwanitsa ndi Mabokosi AMALIRO osati chitukuko Chitsiru cha munthu .

  • @Kelvin-hj5qv
    @Kelvin-hj5qv5 күн бұрын

    Kkkk 😂😂 khaniyo ndiyowona amange gowelo bs zachamba bs

  • @user-cj2bo4lf7c
    @user-cj2bo4lf7c5 күн бұрын

    Chakwera waononga dziko la Malawi .angongwetsa kwacha mosanganizira anthu osauka

  • @omarjustin5518
    @omarjustin55185 күн бұрын

    Chakwera Kodi sigaru ameneyu

  • @stainmujiwa3617
    @stainmujiwa36175 күн бұрын

    Kkkk ati kamuyenda njila anadya matako agalu.nde ndi nkazake ngt otupa mutu uja😂

  • @kubengovender6996
    @kubengovender69965 күн бұрын

    Keep it up brother man!!

  • @BlessingMbule-m4d
    @BlessingMbule-m4d3 күн бұрын

    Iwe ndi one❤

  • @user-mw8dq4is6k
    @user-mw8dq4is6k5 күн бұрын

    😂😂.😂 Chilichonse chakwera ndichakwera adatelo APM

  • @fxmw

    @fxmw

    4 күн бұрын

    😅

  • @TimothyNkhutembaChirwa
    @TimothyNkhutembaChirwa5 күн бұрын

    Kumukuyu alibe ku immigration anthu akuvutika kwambiri komaso kuba passport amati yikhala k50,000,pano ndi k500,000

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk5 күн бұрын

    Powerful long live bakili muluzi TV

  • @AubreySymon
    @AubreySymon5 күн бұрын

    Ndiana sakuziwa kathu auze mwina aiwala. 😅😅😅

  • @user-dx4zu1wv4q
    @user-dx4zu1wv4q5 күн бұрын

    ❤❤❤timakunyadila man kwambiri tione ku lsrael ndi ku Russia zikuti bwanji kumeneku

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw5 күн бұрын

    Bakili mulizi❤❤❤❤

  • @shafiemalobvu
    @shafiemalobvu5 күн бұрын

    tafufuzani za ku Burkina Faso kuli president wazeru kwambili mutibweletse mbili yake bg man

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv

    @AbdulmajeedJbanda-oz3jv

    4 күн бұрын

    Yes plz

  • @JamesChiphwanya-tb3tq
    @JamesChiphwanya-tb3tq5 күн бұрын

    Abwana president chakwela Ali ngati chidole kapena kuti katuni ena amagomungwila ntchito zaumunthu uyu mulibemo ndipo ndi khutukumve chakwela wa mwazi uyu

  • @user-dh1oi8mb4v
    @user-dh1oi8mb4v4 күн бұрын

    Akunamizana akuti awina ndipo sawina anthu ameneyo ndipo azafa ndi mtima ndithuu my vote for Dpp hoyee

  • @nationsmpweti8088
    @nationsmpweti80885 күн бұрын

    Abwana bwanji mzakhale president zikuwoneka kut muli ndi nzeru zoti mngasinthire znthu

  • @LastenWesele-wq8jh
    @LastenWesele-wq8jh5 күн бұрын

    Video iyi ndiyakale tinayiwonela kale

  • @thomluckson4557
    @thomluckson45575 күн бұрын

    In fact chakwera nd mbuzi

  • @user-is5dl7np9g
    @user-is5dl7np9g5 күн бұрын

    Zoonad MCP singawineyi, thanks bro for informing us

  • @PhillipMtonga-g7o
    @PhillipMtonga-g7o4 күн бұрын

    Yakwia ndi mizimu

  • @BrightPhiri-bt6ev
    @BrightPhiri-bt6ev5 күн бұрын

    Ine ndikanakhala peter ndikanangozitaya kuti apume kutukwanidwa.mwina iweyo nkuzakhala minister galu iwe.

  • @JuliusAndrea-iq6xc
    @JuliusAndrea-iq6xc3 күн бұрын

    Kkkkk chitukuko chake ndi kuba 😅😂😂

  • @JacksonMoyo-tm8dv
    @JacksonMoyo-tm8dv5 күн бұрын

    Inu ndinu heroe bwana ,MCP isazabwelere muboma kufikila titafa chifukwa muwaru,gadama,solobala ,chilima,chisiza anaphedwa ndi MCP komanso amatenje

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire5 күн бұрын

    Akadzi Ake kamimba ngu Ngati mbudzi yakhuta mphare yakuba 🤣🤣🤣

  • @RhodneyBwa3
    @RhodneyBwa35 күн бұрын

    Kunkuyu ndi mfiti otheratu

  • @rashidadan2533
    @rashidadan25335 күн бұрын

    Kumkuyu ndi Mr nonsense

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire5 күн бұрын

    Komanso Mzuzu airport Ngati airport ya witchcraft kkkkkk

  • @TerryNac
    @TerryNac5 күн бұрын

    Good good continue

  • @thomasbodo4099
    @thomasbodo40995 күн бұрын

    President uyu ndi pa nja penipeni munthu osadziwa chimene akuchita ndi munthu wanji

  • @AbdulmajeedJbanda-oz3jv

    @AbdulmajeedJbanda-oz3jv

    4 күн бұрын

    Sindikudziwanso Kuti ndiophunziladi uyuuu Kunachita kuyiwala zomwe alankhula dzulo zimayenda Koma mkalasi munthu ameneyu

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji16085 күн бұрын

    🎉🎉🎉🎉

  • @GoodwellRaphael
    @GoodwellRaphael5 күн бұрын

    Akapume atisautsa mokwana agalu amenewa

  • @user-tu8yx2on1r
    @user-tu8yx2on1r5 күн бұрын

    Following 😊

  • @user-hk1kj9bk7b
    @user-hk1kj9bk7b5 күн бұрын

    Kkkkk khani ndiyomanga gowero ,

  • @amoschataika7440
    @amoschataika74405 күн бұрын

    Kkkkk Anyamata tilipo ife timanga ka Gowero Bro 😂😂😂😂

  • @msatisi.reangfordphiri
    @msatisi.reangfordphiri5 күн бұрын

    Kkk koma ndaseka yandibaya yomanga kagowero ku ku airport

  • @user-nm1jj5qv8i
    @user-nm1jj5qv8i5 күн бұрын

    Welcome bwana for today again Amen ❤

  • @user-wd9yd1bg9n
    @user-wd9yd1bg9n3 күн бұрын

    Ķķkkk chitukuko chake ndi kuba😅😅

  • @sharlifcassim6591
    @sharlifcassim65913 күн бұрын

    Tamulimbikiseni nkhani yomanga gowelo Ku airport komwekoyo😂😂😂

  • @PatrickTchuma
    @PatrickTchuma5 күн бұрын

    Dziko la Malawi silidzasithaso ngt atsogoleli anthu sadzasintha

  • @VeronicaYohane
    @VeronicaYohane5 күн бұрын

    Amangilen pofikiladi abusawo nkhosa zikudandaula busa amanthawa😄😃😄😃😄😃

  • @MercykanchureJohnson
    @MercykanchureJohnson5 күн бұрын

    Tikhara kuti tikungotukwana bas pa social media sizitithandiza Ife tingopanga zoti Mulungu atione ndikutivera chisoni basi Tizizivera chisoni kuti Mulungu atikhululukire

  • @RasheedMaster-md2vz
    @RasheedMaster-md2vz5 күн бұрын

    Apanga post not bakili muluzi page yake ai nokha simukuona inuyo

  • @MacdonaldChimwaza-bn9cu
    @MacdonaldChimwaza-bn9cu5 күн бұрын

    Video ya kalekale iyii

  • @AngellachifundoMwale
    @AngellachifundoMwale5 күн бұрын

    He has forgotten about the boolet train your just reminding him now poor Malawi that used to be a milky and honey country shame on us 😂😂😂😂

  • @ishmaelmkuluma2013
    @ishmaelmkuluma20135 күн бұрын

    Iwe aise video iyi ndiyakale wamva galuso iwe eti uzingoponya ma videos akale kale

  • @user-kw7wr4kq9w
    @user-kw7wr4kq9w5 күн бұрын

    Malawi politicians are all poor minded because all of them are just after money after these ones other Gandangazi are coming ooh my beautiful country 😢😢😢

  • @RhulaniMukasi
    @RhulaniMukasi5 күн бұрын

    Enainutu mukutukwanira ameneyu mukuziwa kut 2025 muyaluka amanena chilungamo maka mphava za MCP zimadananaye ndipo anamachende achakwera ndiguluranu tikumana 2025 minyeromwanu nonse😊

  • @KhamillMathuso
    @KhamillMathuso5 күн бұрын

    Maka feteleza yo iiiih🙌

  • @user-xe5lb4uf3n
    @user-xe5lb4uf3n4 күн бұрын

    Zoonadi amange Gowero ku Airport komweko.

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y4 күн бұрын

    Bakili TV number one ❤

  • @user-xe1so5xj2w
    @user-xe1so5xj2w4 күн бұрын

    Chakwera tatopa nayo bolani afe basi anthufe tatopa naye kwambiri

  • @abe9104
    @abe91045 күн бұрын

    l,m watching from .am angry with Britain .mcp never win

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h5 күн бұрын

    Tiyeni nazo big ❤❤❤yu

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu53945 күн бұрын

    Kkķkkk koma iwe akuthyola kholingo chakwela ndi satana

  • @lovenessmuthiya3513
    @lovenessmuthiya35135 күн бұрын

    Best TV ever

  • @ChriKezi
    @ChriKezi4 күн бұрын

    Mcp izalila maliro onyamula wina azathawa malawi akufuna

  • @danielmuriya8675
    @danielmuriya86755 күн бұрын

    Mosses ndi mmodzi mwa afiti mmalawi muno.

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa5 күн бұрын

    Kagowelo kkkkk

  • @user-es4jt6ds8m
    @user-es4jt6ds8m5 күн бұрын

    Chakwera zimene wakwanitsa kupha chilima basi palibepo chimene akupanga komaso nanga asikali Aja Amati azapanga ma video ya momwe chilima alikuti anthu Aja chonde asawaphesotu

  • @MichealDPhiri
    @MichealDPhiri4 күн бұрын

    😅😅😅 at bola Vasco da gama 😅😅

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili5 күн бұрын

    Apm my vote

Келесі