Anthu omwe anyoza Jetu ... Kut Samantha kuimba

Ойын-сауық

Пікірлер: 128

  • @khonjek125
    @khonjek12515 күн бұрын

    I am a musician,producer and professional sound engineer This woman has changed music in Malawi

  • @daniellomoliwa7394
    @daniellomoliwa7394Ай бұрын

    She's not artist accept that fact.. there's someone behind her but that can't be fact to hate her..we must love what she's doing

  • @PeterNakhutu-tp1ns

    @PeterNakhutu-tp1ns

    Ай бұрын

    Uku nde kulankhula..

  • @AndrewBanda-gk7vo
    @AndrewBanda-gk7voАй бұрын

    Respect what the old woman is doing guys , paka sindingapite ku show kwa jetu Malawi tusungira anthu opondera love each other , pake zinthu zimativuta kuti zizitiyendera

  • @EvanceGift-zr1wy
    @EvanceGift-zr1wyАй бұрын

    Jetu amatha kungoti kumalawi umbuli umatipweka sitimaziwa kupangana support km kunyoza. I love you Grandma jetu i'm watching you from south Africa capetown

  • @ajleonard265
    @ajleonard265Ай бұрын

    Kuli ambiri kuimba saata koma antu amawakondera moraro basi, ena angomukondera chisoni ndikufuna kumunyoza Joy Nathu, but the fact will remain the same and can not change the song, saatha

  • @GeofreyCassim-ip1tk
    @GeofreyCassim-ip1tkАй бұрын

    Mayi wapeza chochita, let's congratulate her , mumafuna kt azikupemphani . Muziwalambila omwewo omwe amakupatsani ndalamawo kt muziwachemerela. At that age but she managed to come up with a song , that's great achievement. This is very sad to hear that people who have many followers discouraging someone coz of the age.What a roll model .Mwakhumudwitsa dziko

  • @user-kr1kg5hy9l
    @user-kr1kg5hy9l2 ай бұрын

    Amatha Jetu,am one of her top fan❤️❤️❤️🔥🔥🔥

  • @user-ie8ed5zm3g

    @user-ie8ed5zm3g

    Ай бұрын

    Amatha kuyimba kwambiri ndipo ndidolo wa azimai kuposaso makape Inu mukumunyozanu nyimbo zanu sitimazira

  • @user-zl1xz9kt5s
    @user-zl1xz9kt5s2 ай бұрын

    Adani okuda nd mitima yomwe a Malawi podcast akumva pain nd Chakwaza Akakhala oyera kungu lokhayu nde amangofuna achina ujeni aja ampatse chibanzi chikankwana azibudikulisa mma social media mu zaziiii Akhalitse Jetu 💪🔥

  • @yungdrashmw4051
    @yungdrashmw40512 ай бұрын

    Amatha kuyimba kwambili ndipo ndichitsazo chabwino kwa anthu wonse wokalamba kuti wokalambaso alindikuthekela kuzitha zinthu chifukwa tonse ndi anthu wolengedwa kuchokela kwa Mlengi wamakolo anthu Over !!!!!🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @innocentmausa6643
    @innocentmausa66432 ай бұрын

    Pass my humbly respect to her Manager for doing good example potiwonetsa ndikutiphuzitsa kuti Agogo ndim'dalitso komanso tinayenera tiwasamale ndikuwathokona pantchito yobeleka makolo athu

  • @innocentmausa6643
    @innocentmausa66432 ай бұрын

    aMalawi timakondwa tikamawona anthu achikulire akutonzedwa kuti ndi mfiti that's Y now tikunyasibwa ndi Jetu but to my side am very grateful to see Jetu being happy,healthy and enjoying lifestyle if U could listen to her when she was saying ine pamoyo Wanga sindiname ndadyapo KFC or Ku Nando's Pano ndikutokoza kubeleka ndikwabwino ,I hope munavapo

  • @georgechimaliro9908
    @georgechimaliro9908Ай бұрын

    She is doing well, let's support her.

  • @MeclinaKamanga-jp7rm
    @MeclinaKamanga-jp7rmАй бұрын

    Amatha Jetu ....asiyeni.asanje a podcast

  • @MadalitsoBaulen
    @MadalitsoBaulenАй бұрын

    We are bangweans and being proud of our talented grand ma Jetu

  • @johnchicoti
    @johnchicotiАй бұрын

    Jesus akuyimba bwino moti apitilize luso lake kuti ngati pali Ena okalamba Aliso ndi luso Lina abwele poyela I love ❤ Jetu anthu awo ndi afiti kwawo usawavele

  • @ChrisChokani
    @ChrisChokaniАй бұрын

    Amene akuti samatha ameneyu chitsilu kwabasi 😂😂

  • @user-tt9qz8jd8c
    @user-tt9qz8jd8cАй бұрын

    She is the best in what she does no need to compare with others she is being Jetu..... she is being her...

  • @patriciap.bandah3385
    @patriciap.bandah33852 ай бұрын

    Anthu inu ndiwomvuta kwabasi, mwini wake anayankhula momveka bwino kuti amasangalala nazo chifukwa sakhalanso akuganiza kuti ndi gogo wamasiye inu ndiye muzichuluka nzeru, kuli oyimba ambirimbiri kunjaku wosatha kuimba koma timakhala tikumvelabe nyimbo zawo ndiye inu yambisani nkhani ina

  • @GanizaniTime

    @GanizaniTime

    Ай бұрын

    Mmmm mzovuta kwaine saimbadi

  • @HappyBirchForest-zy8nq
    @HappyBirchForest-zy8nq2 ай бұрын

    Amalawi munazolowera jealousy panya panu pangani zanu zukukanikani zikanakhala kuti ama jealousy mumalandila ndalama mukanalemera koma mulemera mapwala anu

  • @PrincehrnNgombayela-rq3gi
    @PrincehrnNgombayela-rq3giАй бұрын

    Amalawi tinazolowera kuona agogo mtown mu akupemphetsa ndie jetu pa level yake akuitha let's support her , tikumudikira pa 26 apa kuno ku island kuti azaipatse moto

  • @user-jk8sh7fh2d
    @user-jk8sh7fh2dАй бұрын

    Iiiiiiiii! Amatha jetu ndi gogo wathu ameneyu wa chi malawi, enawo alibe ntima wa chikondi that's why samankonda to me si-kuti ndimazikonda kwenkwen koma zimangondipasa moti ndithakhala kuti kuthekela kwa chuma ndili nako nditha kungonthandiza bsi , posatengela kuti ndimazikonda olo ai why ndi olimbikila kusiyana ndi kumangokhala anapeza zochita jetu bsi let's support her kunyoza si sikungathandize kwa gogoz ngati imenei

  • @wangat2005
    @wangat2005Ай бұрын

    Jetu emweyo kuti waaaaaaaaaaaaa

  • @GharmonizeCondeboy
    @GharmonizeCondeboyАй бұрын

    Salute agogo jetu🎉🎉

  • @pettersen2717
    @pettersen2717Ай бұрын

    Akulu inu a man u.nsanje izakuphani ndithu. Kodi inu ndi agogo anu munachitapo zoterezi kupatula pa ufiti agogo anu aja?

  • @MaureenMugala-yh5pj
    @MaureenMugala-yh5pjАй бұрын

    Yes Jetu nice woman ad she can sing

  • @user-ir2yz5zz5x
    @user-ir2yz5zz5xАй бұрын

    Jetu kusaizi yake amatha kuimba ndpo nyimbo zake timazifira kwambili

  • @RachelPhiri-lm6ev
    @RachelPhiri-lm6evАй бұрын

    vuto amalawi kuphempha salufuna kuvutisa anthu akuchita bwino aliyese akunena za jetu mutu wake kkkkkk mpaseni ulenu

  • @SolomonwaharryLastone
    @SolomonwaharryLastoneАй бұрын

    The Politics Behind This Is Very Barbaric.Some DJs Are Not Happy Seeing Some Pipo Other Than Them Promoting Singers And Artists. This Is Very Barbaric And Must Stop For The Betterment Of The Arts Industry.

  • @Doreen-gp6kq
    @Doreen-gp6kqАй бұрын

    Eya jetu amatha kuyimba pa size yake musiyeni eeeee kambani zina jetu ndi no 1

  • @EmmanuelNedie
    @EmmanuelNedieАй бұрын

    Kodi akamati satha kuimba kodi iwowo ndiomwe anayambisa zoimba .Iwowo ndindani ali ndi mbiri yoyimba

  • @HopesonMatengula
    @HopesonMatengulaАй бұрын

    Jetu amatha akut jetu santha akango nyela basi😅😅 ife akukwan kwabas 🔥

  • @user-pp3zd5zb2h
    @user-pp3zd5zb2hАй бұрын

    Jetu amatha kuyimba l love you jetu❤

  • @YusufuRonad
    @YusufuRonadАй бұрын

    Very nicely

  • @ConeriasPhiri
    @ConeriasPhiriАй бұрын

    Mupaseni sport osati kumubweza buyo pamene akulakwisa mukhozeni

  • @gizzykondwani865
    @gizzykondwani865Ай бұрын

    Jetu akupha sound pa level yake ❤

  • @JailosiKaphuka
    @JailosiKaphuka2 ай бұрын

    Amene Ali ndi mpila ndi amene amamakidwa

  • @user-xe6rf2di4x
    @user-xe6rf2di4xАй бұрын

    😂😂😂😂zantiiiii sanje yopanda nzeru kuda biiiiiii

  • @user-nd9cm3yl7e
    @user-nd9cm3yl7e10 күн бұрын

    Asiyeni ambc ndikudzikondakwaoko athu ambili akusangalalanaye

  • @successm-vt3dx
    @successm-vt3dxАй бұрын

    kaya amatha kasa satha zanu km ife cape town tikufira

  • @LindiweMoloi-wn5qo
    @LindiweMoloi-wn5qo27 күн бұрын

    Guyz agogo aja pachilungomo chake samaziwa kunyumba mungowapopa auzeni chilungamo ,amwenewa akunena zoona sikuti akuwada ayi amalawu tatiyeni tiphunzile kunena zoona,olo mayiko oyandikana nawo akutiseka

  • @yalinhlema
    @yalinhlema2 ай бұрын

    I love Jetu

  • @HafreezihMpalumeinnocent
    @HafreezihMpalumeinnocentАй бұрын

    Jetu ndi 1❤❤❤❤❤

  • @GeorgetteKankhunda-my2sq
    @GeorgetteKankhunda-my2sqАй бұрын

    JetuNo 1❤

  • @StelliaBanda
    @StelliaBandaАй бұрын

    Onyoza getu azipanga zake

  • @nathanvanderberg6558
    @nathanvanderberg65582 ай бұрын

    Anthu muli ndi nsange mpaka eeeee anyamata chitani manyazi live here alone yilipambuyo pa jetu

  • @user-iu5sk1cy7g
    @user-iu5sk1cy7g2 ай бұрын

    Amalawi sanje sipindula wokalamba amene alindikuthekela apange zinthu zoti akhoza kuthandizika pa moyowake kodi amalawi mumafuna wokalamba opephapempha?

  • @TesahBanda-mz2yh
    @TesahBanda-mz2yh2 ай бұрын

    Ine l love jetu

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q2 ай бұрын

    Chokani amalawi oyipa inu amalawi asanje inu musiyeni jetu aziyimba ndipo akuyimbabwino ndithu komaso anyamataake awo akuvinabwino ndithu Vuto amalawi sanje imakuvutandi ndithu iya mbori zanu.ndithu

  • @user-bc2mu2ns5n
    @user-bc2mu2ns5n2 ай бұрын

    Agogowo alimbikiseni pa size yawo amatha amene mumanyoza ndichifukwa chake si ndinu Jetu . Inu ndi inu Jetu ndi Jetu ngati kuwona kuti sakufika mlingo wanu pitilizani kuchokela pamathela Jetupo.

  • @user-yu4np2wq4s
    @user-yu4np2wq4sАй бұрын

    Kuteloko athu Ngati awawa mulungu aziwakhululukila chifukwa ndichiwanda chikwapangisa Kuti ayakhule momunyoza jetu ndichimodzi modzi mmene Alili agogo awo iwoso Ngati alinawo agogo awapangile chochita mulekeni mumuone kumene athele osati zomusisila pas ayiiiiiiiiii ziwanda zaathu inu ofunika tikuyitanilen amulelemba akuphepheleleni amulelemba 🗣️🗣️🗣️ mulikuti pephelelani ziwanda zaathuzoo

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso50622 ай бұрын

    Tiyeni timpatse support Gogo wathuyu, Jetu ndi msangalatsi wathu, kaya kuyankhula kapena kuyimba zonse zili bwino,, Stop compare Jetu ndi Anyamata owimba enawo, Mayi wabwera kudzakhala.

  • @HugoOrthoCamera-ec7vc

    @HugoOrthoCamera-ec7vc

    2 ай бұрын

    Jetu amatha ndidoro

  • @user-fs3wc8ue8b

    @user-fs3wc8ue8b

    Ай бұрын

    Jetu❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @TimothyJere-yb4lz
    @TimothyJere-yb4lzАй бұрын

    Jetuu❤❤❤

  • @FatimaPhirih
    @FatimaPhirihАй бұрын

    Nice woman

  • @user-hl3st3cc4v
    @user-hl3st3cc4v2 ай бұрын

    Mukunyasidwa gogo kumasangalasa anthu koma kukanakhala kuti ndikutchuka kophudzitsa ana ufiti mukamva nazo kukoma

  • @ThokoSalim

    @ThokoSalim

    Ай бұрын

    Eead amafuna azmva zot agogo aja akiphunzitsa ana kutamba ndye iwo ku mtima kwao mbeee zkakoma kumayamikla ine chetee pa mbuyo pa jetu

  • @bmbboymstyles5894
    @bmbboymstyles58942 ай бұрын

    Ine nd JETU....! 🔥🔥🍒❤

  • @edwardedo6798
    @edwardedo6798Ай бұрын

    JETU samatha kuimba ziribe kanthu Bola iye akupanga ndalama and mbiri yake pa Malawi pano iri paliponse, zikumgowapweteka azitsiruwa chifukwa iwowo sakutchuka and they just wanna be famous ponyoza JETU,Iwe ndi ndani? iye ndi JETU, Yomweyo Galu iwe

  • @taniamanenafavouriteneezam8510
    @taniamanenafavouriteneezam8510Ай бұрын

    Jetu she,s the musician by mistake I hope you understand,,,what I saw is,there is someone behind her,she is used to make someone money

  • @user-bp5po7rt8e
    @user-bp5po7rt8e2 ай бұрын

    Mmmm koma akudawo amalankhula uyipa

  • @tadalangozo5167
    @tadalangozo5167Ай бұрын

    Adani okuda ndi mtima omwe,, we love jetu 3 sitopu

  • @user-ck7eb7tb7v

    @user-ck7eb7tb7v

    Ай бұрын

    tiadani tolimbana ndi magogo aluso😀😀

  • @user-fp5qn5ci2v
    @user-fp5qn5ci2vАй бұрын

    Jetu ndiwoimba basi nsanje basi?

  • @doublepmw5497
    @doublepmw5497Ай бұрын

    Jetu ❤❤

  • @user-gd3jx7tr1p
    @user-gd3jx7tr1p2 ай бұрын

    Amatha jetu chabe ndinu anthu ajerous basi

  • @user-ox8cx8xt6b
    @user-ox8cx8xt6bАй бұрын

    Ndipo uyo amati jetu is like a puppet mumuuze pachiphwisi Pake ndipo uyo amati I feel nothing mumuuze pamayake... Agalu anthu oyipa mtima....

  • @JalasiLucasJalasi
    @JalasiLucasJalasiАй бұрын

    Onse oimba chamba chamapiyano sioimba including boyfriend wa bossladie

  • @malawimuahmmed5941
    @malawimuahmmed59412 ай бұрын

    🔥🔥

  • @ThomsonMusowa
    @ThomsonMusowaАй бұрын

    Jetu is one ❤❤❤❤

  • @kelvinngwira3648
    @kelvinngwira3648Ай бұрын

    Sogolo lamuthu Amaliziwa ndi Ambuye.Ngati inu simungapite ku show nde kuti enawo sangapite apita amalawi nsanje basi

  • @user-bb5iy7ry5h
    @user-bb5iy7ry5h2 ай бұрын

    Samatha kuyimba koma ndiwongosangalatsa mtundu wa malawi basi

  • @MasharPablo
    @MasharPabloАй бұрын

    Samatha,vuto amalawi amadana ndi chilungamo basi, iyaaah

  • @CharlesMillion-bt9su
    @CharlesMillion-bt9suАй бұрын

    Jetu amatha

  • @Hlehle719
    @Hlehle719Ай бұрын

    ❤❤❤❤❤

  • @user-rd2td7bg4c
    @user-rd2td7bg4cАй бұрын

    ❤❤❤❤adani okuda

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vnАй бұрын

    Amalawi njiru komanso ufiti

  • @RachelPhiri-lm6ev
    @RachelPhiri-lm6evАй бұрын

    ayi mayiwa mbali yawo akuyesesa ndi mmene tsikhu wawo asiyeni ndimmene akupezera ndalama mmalo mophemphapha

  • @tenexchikumba
    @tenexchikumbaАй бұрын

    Koma mpaka kuzinza nkhalamba? Koma a Malawi, wina nde akut sangasambe😂😂

  • @AndrewChabadwa-xl3ff
    @AndrewChabadwa-xl3ffАй бұрын

    Jetu umakwana iweyo

  • @AbdirahmanWllsonkey385
    @AbdirahmanWllsonkey385Ай бұрын

    Amanta kuyimba jetu chifukwA chake timamusiwa

  • @PatieKates
    @PatieKatesАй бұрын

    Sam malvitha iwe mapwala ako nditu

  • @BaulenPatison
    @BaulenPatisonАй бұрын

    Pasikhu wajetu amatha ameneyo Ena ku Malawi Kuno msikhu wakewo amathawa ngakhale kuyakha 4n

  • @promisendawala60
    @promisendawala60Ай бұрын

    amalawi kungozelera chilichonse ndale agogo ndiwabwino akakhala kuti ndi ambuyanu mukanatani mukumbukire paja inunso kuti mufike pamenepo ndi anthu anakupanga push tidzipuzizira kutukulana tokha tokha, anathu oipa

  • @rhodahjere8747
    @rhodahjere8747Ай бұрын

    Akuimba bwino kwambiri apitilize lunso lake osamukhomelera ayi iiii Amalawinso aaa

  • @jonathansamalani
    @jonathansamalaniАй бұрын

    Komano to be honest amayiwa kuyimba amatha,kumalawi kuno kulinkhalamba zambiri koma ndinkhalamba zingati zingakwanitse kuyimba olo atazipanga managing?

  • @HlupekireMoyo
    @HlupekireMoyoАй бұрын

    Pajatu aliyese akupanga zomusangalatsa nde musiyeni jetu

  • @elevenmtenjemalik5214
    @elevenmtenjemalik52142 ай бұрын

    Nyimbo za gogo yu ine sinamvereko chifukwa sindimazikonda ka palibe cha nzeru chomwe sindimachiona ata

  • @ziyamikanmakowa5981
    @ziyamikanmakowa59812 ай бұрын

    Amatha kuimba ,akunyozao makolo awo angaimbe chomchi

  • @ajleonard265
    @ajleonard265Ай бұрын

    Palibe chanzeru apa

  • @BwanaGD
    @BwanaGDАй бұрын

    Kaduka msanje zagokula bas

  • @rabsonmkandawire858
    @rabsonmkandawire858Ай бұрын

    Jetu alibho heavy achina joy ndi awa a Malawi podcast ma views awo sangapose Jetu 😂😂

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517Ай бұрын

    Adani okuda ngati ntchende lakumamzere

  • @DanMhone-iw6xg
    @DanMhone-iw6xg2 ай бұрын

    Nd dolo kwambili zed jetu

  • @JosephJulias-wd7fl
    @JosephJulias-wd7flАй бұрын

    Ineso amandibowa😩

  • @MadaNamkwenya
    @MadaNamkwenyaАй бұрын

    Zaboza alibho

  • @user-yu4np2wq4s
    @user-yu4np2wq4s2 ай бұрын

    Jetu akuyimba Koma athu jerasi apitilizeeeee

  • @HildahMasebo
    @HildahMaseboАй бұрын

    Aliye ali ndi nthawi yake

  • @HonneyceeMwChibalo-io7zc
    @HonneyceeMwChibalo-io7zcАй бұрын

    zisiluu za anthuu zimenezoooo

  • @TroubleRichard
    @TroubleRichardАй бұрын

    Jetu alibho kwambili

  • @SamuelBlam
    @SamuelBlam2 ай бұрын

    Getu ndi dolo kusiyana ndi gidezi pano kuli piano angamamvele za chigogo ndini anthu nsanje izakuphani

  • @nyirendajohn7443
    @nyirendajohn74432 ай бұрын

    Ndizonadi sikuzuza iyayi Pali ndalama osati ulesi tiyenayo jutu bane ikhoza kukhala Sanje

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj2 ай бұрын

    Makape awa ngakhaleso ndalama zomwe wapeza jetu iwo alibe

  • @user-ou8ng5kb2n
    @user-ou8ng5kb2nАй бұрын

    I think joy is jelous

Келесі