ANG'ALULA MOSAIPA LERO PA 10 July 2024

Пікірлер: 31

  • @TisopeChagala
    @TisopeChagala17 күн бұрын

    Chawezi asazabwerenso

  • @lysonmhone5425
    @lysonmhone542517 күн бұрын

    Kuswa kuswa Kufotokoza mmene ziliri pa ground Mavuto anayala mphasa dzikoli 90% ndi anthu osauka

  • @kennedybanda
    @kennedybanda17 күн бұрын

    Mosatayitsana nthawi vision 2063 ndibodza lamkunkhuniza ndithu. Malawi wachulukitsa usatana.

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon342917 күн бұрын

    Yes chawezi asazabweleso apangisa kuti ine ndisamavele program iyi

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI17 күн бұрын

    Chakwela wamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon375617 күн бұрын

    Atsongoleri anthu onse ationongera Mother Malawi......Very sad Nation😢😢😢

  • @HamzaShaff-vo3ci
    @HamzaShaff-vo3ci17 күн бұрын

    Ngat mukufuna kt tizikupangan for4 mumuchose chawez

  • @user-dp7bc7yy6s
    @user-dp7bc7yy6s17 күн бұрын

    Program imenei lelo ikumveka bwino kwambiri. Tikupempha chonde Chawezi uja asamapezeke kumibawako ameneuja ndiwa Mcp

  • @ChembeWaimba
    @ChembeWaimba17 күн бұрын

    Kuyankhura it's simple kungonena mavuto sungatchule mavuto amene tadusamo, wabodza iwe kagwere uko, ine ndiye sunganinamize chilungamo ndikuchidziwa, cadet program muziwonera nokha.

  • @user-lp2sd7lt8b
    @user-lp2sd7lt8b17 күн бұрын

    Kabambe anali m'boma kale bwanji sanapange zimene akunenazi

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o17 күн бұрын

    Akalindo aja kungomangidwa ma million akumalowa ku ACC kwawo, ife kutimanga basitu tikafela konko

  • @hopembendela
    @hopembendela17 күн бұрын

    Malawi we have weak politics if the politicians stop stealing the money malawi will be a better country again

  • @JasonMailos
    @JasonMailos17 күн бұрын

    😭😭😭 Malawi wanga

  • @user-cy9zp4fb2m
    @user-cy9zp4fb2m17 күн бұрын

    Yes vutodi ndy atsogoleli😢

  • @FrancoKaunga-rq2ki
    @FrancoKaunga-rq2ki17 күн бұрын

    Malawi is not a country it's a farm for politicians!

  • @user-qz3ol8mj2c
    @user-qz3ol8mj2c17 күн бұрын

    Very good analysis the question is , what have you done at your level to help the situation apart from making this good analysis?

  • @fredgabrielnyangulu
    @fredgabrielnyangulu17 күн бұрын

    Vuto lathu ife a Malawi vision yeni yeni tilibe chomwe timakhala nacho ndi kusintha zipani basi ndipo akabwera zomwe amadziwa ndi kuba . Chomwe chimandinvetsa chisoni munthu walembedwa ntchito ndi amphawi Ndalama zomwe akulandira ndi misonkho ya a Malawi more over amalandira ndalama zambiri ndie ndimadabwa kuti akamapita ku misonkhano ati akufuna allowance za chani ndalama zomwe timawalipira ndi zomwe amayenera kuti azigwiritsa ntchito ndipo ma Civol servant ndi omwe amawononga misonkho yathu chifukwa munthu akulandira ma million koma akuti misonkhano chili chonse cha ndalama za amphawi

  • @ChisomoMandawala
    @ChisomoMandawala17 күн бұрын

    Tiyenawoni ma comrade

  • @user-xx4jb9se3z
    @user-xx4jb9se3z17 күн бұрын

    Ai dzana 60 .chomwe tapanga bro kuba kupha ndi maulendo opita ku junja pa passport kulibe kkkkk

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w17 күн бұрын

    A Victor mumalongosola bwino, vuto lakula kwambiri zaka 4 zapitazi chifukwa cha Utsogoleri wa Chakwera, sakudziwa chilichonse.

  • @goodwilljeza8419
    @goodwilljeza841917 күн бұрын

    Man subwoofer

  • @rexnyalugwe4910
    @rexnyalugwe491016 күн бұрын

    Queen Elizabeth hospital mwati unamangidwa liti?

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i17 күн бұрын

    Zakhala bwino kuti munthu oipa uja chawezi Banda palibepo

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y17 күн бұрын

    Chakwela wapha Chilima

  • @retirementtoafrica
    @retirementtoafrica17 күн бұрын

    60 partys shaaah?

  • @eliaskhofielias8152
    @eliaskhofielias815217 күн бұрын

    Kadziko kamalawika mwati kadziko or kamunda?kadziko komvesa chisoni kwambili ndiye kanakakhala kadziko kakakulu akanapanga nako bwanji ngat tikukalephera kukatukula pano?muli nsanje kwambili mujadziko kamalawi,chikondi mulibe.kadziko komvesa chisoni kakang'ono koma zochitika Eeeeh 👹👹👹.tianthu takenso timaoneka ngat tozindikila koma ziro ku 10.mumakhala ngat muli anthu anzeru koma heeee!!zero ku 10.tanzania and zambia ndikaiona kuisilira ngat ndikakhaleko ndisamuke kumalawi.nzimai akuchita kuitukula Tanzania kuona ma bridge amakono.sitima zapantunda koma kumalawi vuto kumangoyang'anana basi kuipidwa ndikuphana popanda kanthu.andale athu malo mopitisa chitukuko amalimbana ndimunthu.malo momanga misewu or ti mabridge tamitsinje tomwetu kulephera ngat boma kukonza ma bridge a standard.malawi mulibe mitsinje yaikulu ikulu yoti mutha kukhala ma bridge akulu akulu.maiko anzathu akupanga zimabilidge zazitali 20 to 50 kilometer koma ife ka bridge ka 1 kilimeter matatalazi kut kamangidwe.azitsogoleli athu ndalama amakhalangati ndizawo akuchosa thumba mwawo osati zathu.look pano misewu yambili ingoikidwa pa central region tinganene zoti zitukuko zambili zangodzadzana pakati komanso ti madevelopment akuphangilato tosekesa kwambili.ndikumanyadila tikupanga chitukuko zopusa basi.tamayendani maiko ena.bvutonso losankha azitsogoleri okut sanayendewa ndizimenezi timakangowa votera azikapeza mabusiness awo.akamadzasiya zitalemera ife kutisiya manja lende iwo ndibanja lawo atalemera.

  • @retirementtoafrica
    @retirementtoafrica17 күн бұрын

    Tsopano malamulo amati musanachotse logo yaeni ake anapanga video yi khaya ndi times, zodiak olo mibawa kuti musadzabvutane nawo.

  • @DawoodIssah-mp1yi
    @DawoodIssah-mp1yi17 күн бұрын

    Ufulu wotilamulira Osati Wozilamulira, Akulamula dziko la Malawi ndi ndani? Akulamula ndi America ndi Britain Osamanena kuti ufulu wozilamulira Almost more than 90% ya boma or dziko la Malawi zikuchokera Or kuuzidwa ndi ma west.

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg17 күн бұрын

    😂😂😂 60 years for nothing shame malawi

  • @wakisawinga2744
    @wakisawinga274417 күн бұрын

    Very sad nation 😭😔

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p17 күн бұрын

    Where are SKC reforms? Why is Malawi being held back?