AKUFUNA KUCHOTSA MPANDO WAU VICE PRESIDENT__ MALAWI WANUKHA🙌🙌

Пікірлер: 88

  • @homeremedys3748
    @homeremedys374826 күн бұрын

    Panopa akugwira ntchito za Vice president ndimwana wa president

  • @kondwanimunthali7401
    @kondwanimunthali740125 күн бұрын

    Osati kuthetsa u VP koma kukhale Deputy president nayenso azikhala ndi ntchito zake osati delegated powers

  • @user-is5dl7np9g
    @user-is5dl7np9g25 күн бұрын

    I agree 💯 with this issue very much, VP amangowononga Chuma cha boma for nothing, a very good example is saulos chilima from time of DPP kufikila lero sindinaonepo chomwe anachita chopindulira dziko

  • @user-qm1qb2jp4s
    @user-qm1qb2jp4s22 күн бұрын

    Mpando umenewo wa u vice president ulibe phindu

  • @user-sh6gi5uq3l
    @user-sh6gi5uq3l24 күн бұрын

    I like this chipani chomwe chapeza mipando yambiri pambuyo pa owina kumeneko kuzichola vice president ndiye malamulonso asithe kuti uyu azikhala ndi macondition omuyenereza kusakhidwa komanso kuchosedwa like k in south Africa chipani cha anc

  • @AmusedDimSum-hd5yp
    @AmusedDimSum-hd5yp25 күн бұрын

    wise spoken from Mr chingaipe big up Big man

  • @chipiliromalola6380
    @chipiliromalola638025 күн бұрын

    Good decisions ❤❤❤❤

  • @user-hq6dq7zr1e
    @user-hq6dq7zr1e23 күн бұрын

    Am very agree of that conservation, ulemu wanu zipitilire malawi akhale ndi mphavu,nde kuti president azikhalaso ndi matha ngati pazikhala ma mistake olamula dziko

  • @user-ux3ed3ni1p
    @user-ux3ed3ni1p25 күн бұрын

    Very necessary discussion. We need to change ASAP.

  • @danielmsowoya9107
    @danielmsowoya910725 күн бұрын

    Izi zopanda nzeru izi, basi meeting ndi meeting kukakambirana zimenezi, bwanj osangoyambisa FEDERALISM?

  • @user-on3yu7wt9o

    @user-on3yu7wt9o

    24 күн бұрын

    Inenso i think federal system ija can help

  • @saved1416
    @saved141625 күн бұрын

    I feel this can only work if we agree to review our constitution. The president has all the powers which makes it easy for him or her to abuse the vice president. The only problem is that our political scientists come out when they want to deal with an individual and not to correct things. I hope this is coming out because of milandu ikuthesedwa ija

  • @EmercianahKasiku-en6hl
    @EmercianahKasiku-en6hl23 күн бұрын

    Yosagwira yoti president azichoka komwe mul ma mp ambirimbiri ndizosagwira chifukwa Malawi umakhala ndi mipikisano itatu pa masankho President kasala komaso mp nde vice president amasakhidwa pamodzi ndi president ngati udikilira kut atadwala kapena kumwalira dziko lisalowe chisawawa likhalebe ndi commander in chief koma bola zoti azikhala Deputy president not just president chifukwa vice amapatsidwa ntchito pomwe Deputy president amakhala kale ndi ntchito zoti agwire

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p25 күн бұрын

    Koma president azikocha komwe kuli ma MP chipani chimenecho kuchoke president basi

  • @MwizaChavula
    @MwizaChavula25 күн бұрын

    Ndiye chisasawa mu govt

  • @douglaskamanga7679
    @douglaskamanga767925 күн бұрын

    Anthu amafa nde wina aka mwalira wachiwili wake azitenga position.Koma ngati zipani ndiza family,u vice usiyidwedi.

  • @user-ez8zs1iq9k
    @user-ez8zs1iq9k25 күн бұрын

    yes u vice president uthesedwe ndipo mumalo mwake tizikhala ndi prime Minister ndikuona kuti zitha kumayenda bwino

  • @CharlesPhiri-ds1rk
    @CharlesPhiri-ds1rk8 күн бұрын

    In deep corgitate,, fundo ili bwino kwambir

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc25 күн бұрын

    Mmmm,inu mukudzidzwa,nangati,kuli anthu andale adyela ndiye,ku Malawi kuno.malawi,mpaka pano kulibe olo kukhala azitsogoleli alutha olo vision, chifukwa onse,ali ndi dyela.

  • @JohnFrank-cg1yh
    @JohnFrank-cg1yh25 күн бұрын

    Zoona vice president akufunika azisakhidwa ngat nduna,

  • @charleslimbani8590
    @charleslimbani859023 күн бұрын

    Osati Malawi wanunkha ichi nchichewa cholakwikaaa ......ngati Pali Malo ofuna kuti akonzedwetso mmalawi muno ufulu Otero ulipo.....osamakhazikika pa Malo amozi moxi ngati zinthu sizikuyenda bwino......sinthani zinthu.....

  • @stellakaluluma8241
    @stellakaluluma824124 күн бұрын

    We also say that Head of state and government, my opinion is that the president must be the head of state and vice president be of government. What also Yuba James has said is very sensible and that should be the way to adopt

  • @ChicoBanda-kq7py
    @ChicoBanda-kq7py25 күн бұрын

    Good discussion

  • @MwizaChavula
    @MwizaChavula25 күн бұрын

    Ndiye what if president aka mwalira hu will take the duties of president?

  • @vinceynyone6693

    @vinceynyone6693

    4 күн бұрын

    The army forces wil take all the emergencies

  • @Johnybegood260
    @Johnybegood26025 күн бұрын

    Tsopano a political science nu nthawi yoseyi munali kuti we needed thinkers like you iyi yokha iduse

  • @KnowxySainet

    @KnowxySainet

    25 күн бұрын

    Fodya awa azindikila lit vuto amafuna chilima basi so zakanika

  • @MarthaPhiri-nr7yb
    @MarthaPhiri-nr7yb9 күн бұрын

    Tipange referendum za mpando umenewu. Osangopanga zanu mufunse ife aini ake ovota komanso olipila office imeneyi

  • @user-xq6vp1tx7z
    @user-xq6vp1tx7z20 күн бұрын

    Ndzowona vs asamankhalepho kumeneko diyeku4

  • @MpanjeHardware
    @MpanjeHardware25 күн бұрын

    Nkhani imeneyi ndiyofunika kwambili kuno kuziko lamalawi nyumba yapekezidemti iyenela ithesedwe chifukwa ikungotha ndalama

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu25 күн бұрын

    Zimenezo sizingapangise kuti mzikolino anthu azingosankhana a chipani chimodzi modzi?

  • @user-yk9lx7xd1i
    @user-yk9lx7xd1i25 күн бұрын

    Ndipo mwakambilana nthawi yabwino masankho ali patali chaka chamawa no vice president we will only vote the president

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf25 күн бұрын

    Vice president amayamba kukulira mtima president that's why Vice president Aliyense amafuna naye akhalenso president.Ndichifukwa Chake Vice president Aliyense amayambitsa Chipani Chake Cholinga nayenso akhale president.Ndiyeno office ya U vice president.Komanso president amalephela kumuchotsa Vice wake

  • @AndersonInnocent
    @AndersonInnocent25 күн бұрын

    Vice president kungotafuna misonkho yathu ku Malawi 🇲🇼 kukhale president yekha basi komanso Chakwela atule pansi udindo

  • @robertchitsulo8006
    @robertchitsulo800625 күн бұрын

    Agree with you

  • @MarkoMkundiza
    @MarkoMkundiza24 күн бұрын

    Panopa ncto ya vice president sikuoneka coz akugwila ndimwana wake

  • @mphatsosadiki4983
    @mphatsosadiki498325 күн бұрын

    Best way kuzingokhala Prime Minister...

  • @danielmsowoya9107
    @danielmsowoya910725 күн бұрын

    Ndale chabe izi

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h25 күн бұрын

    Please go on

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w25 күн бұрын

    Fundo apa pakungofunika kuchotsa office ya vice president, office yimenei yikungowononga ndalama.

  • @tawongamhango7335
    @tawongamhango733524 күн бұрын

    We don't need vice president position on ballot paper. I agree

  • @thomluciouss7360
    @thomluciouss736025 күн бұрын

    This is a serious issue what we must do we need to put a right disition so that the president must no have a light disition to chance the vice president becoz its us we choose and vote for them

  • @user-cl5pi4nb1e
    @user-cl5pi4nb1e25 күн бұрын

    Ndizoonadi ithe palibe chanzeru chomwe imapanga ikumangotha ndalama zathu osauka muno mudziko libe ntchito imangoononga ndalama basi ma salary, allowances, utilities, fuels, workers, state rentals and etc

  • @danielmsowoya9107
    @danielmsowoya910725 күн бұрын

    Zaziiii, lero nde mwaona kut office ya Vice President imangoononga ndalama? Pali ma areas ambiri amene ndalama zimangoonongeka like AIP, bwanj tichotse Kaye zimenezi. There a Political smell behind this proposal.

  • @user-pw2dq1yw4b
    @user-pw2dq1yw4b25 күн бұрын

    Ndipo izii zichitike mwansanga tipange system yakuno Ku South Africa nsanga guys komanso parliament ndi imene izikhala ndi mphanvu yapadela.

  • @IbrahimWezely-qd4vj
    @IbrahimWezely-qd4vj25 күн бұрын

    Apa ndiye mbambande

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf668325 күн бұрын

    Udindo umenewu umangotha ndalama za amalawi, atangochotsadi chifukwa phindu lake palibe

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe821425 күн бұрын

    Iziii ndizoona ndinthu mwina anthu anga dza siye dyerali

  • @user-yk9lx7xd1i
    @user-yk9lx7xd1i25 күн бұрын

    I support Mr Auba kumeneko ndiyekunena

  • @HaroonSaidi-jv3ek

    @HaroonSaidi-jv3ek

    24 күн бұрын

    Inenso zomwe wanena mkotakotayo ndagwirizana nazo

  • @douglaskamanga7679
    @douglaskamanga767925 күн бұрын

    Fundo akunena Ayuba James,yingagwire muchipani ngati sicha family koma cha Public.Inu mwini chipani mungamuitane kumufunsa mafunso?Waku chalenjani APM kulibe zopita ku conversation aima ndiyeyo.Akususa ndani?.Mukuona bwa?

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j25 күн бұрын

    Zimangokhala zobvuta kusazichepesa chisanzo MCP kupanda fundo ndikufunikira kumene anthu anakuona kwa achilima chakwera zikanabvuta kukhala aprezident

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri687325 күн бұрын

    Ndimaganizo abwino kuti vice asakhalepo and tizikhala ndi ma prime minister nduna zizichepa. Komaso vice President ngati akhalapo asakhale wachipani china

  • @MarthaPhiri-nr7yb
    @MarthaPhiri-nr7yb9 күн бұрын

    Kapena tinene kuti ifeyo tikhale oyamba kupanga kuti president azichoka chipani chowina,vice from opposition koma vice president akhale ndi duties derived from constitution 😊😊

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j25 күн бұрын

    And vice president amakhonza kukhala ndi maso mpenya kuposa president chifukwa nthawi zambiri vice amakhonza kukhala munthu amene akhonza kuthandiza

  • @user-ub1mw7ce5p
    @user-ub1mw7ce5p25 күн бұрын

    Good decision

  • @mathewssimbi3052
    @mathewssimbi305225 күн бұрын

    Ndipo ndizoona mpando wa Vice President Uthe chifukwa palibe kufunikira kwina kulikose President wolamurayo ndiamene ammakula mphamvu kwambiri choncho Vice kwake mkumangoyembekezera

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r18 күн бұрын

    Zazii vec president akufunika ziko lililose

  • @christopherchikankhen
    @christopherchikankhen26 күн бұрын

    Nkhaniyo Ndiyoona Ndipo Ndaikonda.

  • @fanuelbinde
    @fanuelbinde24 күн бұрын

    Vice presedent asakhaleponso

  • @lucymuhala2176
    @lucymuhala217625 күн бұрын

    The truth is all deputies whether ministry there useless position just worsting taxes pairs money

  • @user-qi8xe7qh1e
    @user-qi8xe7qh1e25 күн бұрын

    Pasakhaleso vp angotiwonongera zithu

  • @alphatosman3137
    @alphatosman313725 күн бұрын

    ine ndimaona ngati ntchito yake ndikudikira akamwalira winayo

  • @MarthaPhiri-nr7yb
    @MarthaPhiri-nr7yb9 күн бұрын

    Kapena tinene kuti ifeyo tikhale oyamba kupanga kuti president azichoka chipani chowina,vice from opposition koma vice president akhale ndi duties derived from constitution

  • @user-yk9lx7xd1i
    @user-yk9lx7xd1i25 күн бұрын

    Tiyeni tibwerere kuzokhoza zomwe zinakhala lamulo laosakhala ndi vice president mu 1965 no need for malawians to have a vice president

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du25 күн бұрын

    Chakwera ndi mbuzi

  • @user-gq1lj6nc8h
    @user-gq1lj6nc8h25 күн бұрын

    Koma iziz aaa ok

  • @WysonMpatama-cv1mc
    @WysonMpatama-cv1mc24 күн бұрын

    Chilimayo amuchotse akuvutitsa amalawi

  • @user-vq9if2ep5q
    @user-vq9if2ep5q25 күн бұрын

    Koma zilipo ku Malawi

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu25 күн бұрын

    africa Ndi dziko liti mu a frica muno limene lilibe vicepresident Ndi dziko liti mu a frika muno kulibe vice president?

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula493725 күн бұрын

    ZOONA

  • @douglaskamanga7679
    @douglaskamanga767925 күн бұрын

    Nkhani yayi kuli ndiyakuti, zipani zambili mu Malawi muno ndiza banja pa chizungu timati family entities. Ndiye mwini wa chipani sangalole kusiila chipani vice president coz, ndekuti chuma chachoka mu banja LA mwini chipani. So nkhani iyi siyofunaso Political Scientist.Office ya vice president ndiyabwino ndithu koma zilinga zizakhala zotani?

  • @user-xg2ks9nw5q
    @user-xg2ks9nw5q25 күн бұрын

    Mukunama🎉 ku south Africa amasanga vice president amasanga ku corvetion ya chipani

  • @WakudaSawerenga-xu9xc

    @WakudaSawerenga-xu9xc

    25 күн бұрын

    Exactly

  • @Chisomo-dh2gq

    @Chisomo-dh2gq

    25 күн бұрын

    Which South Africa 🇿🇦..?

  • @usumanidaudi
    @usumanidaudi25 күн бұрын

    Osachosa chakwera aziba kwambiri

  • @user-jk8sh7fh2d
    @user-jk8sh7fh2d25 күн бұрын

    Ngati nkotheka achosedi , vice amangodya ndalama zaulele . Kunena zoona anthu awa samagwilizana kamba ka nsanje uwelesiki uwelesiki eeh zonse ndizipanga ndekha ndalama zizikhala zanga ndie ndi zovuta so kwa ine 100% ndikugwilizana nawo makosana amenewa ngati zingatheke kutelo . Olo mufufuze ma MP's ndi othandizana nawo aja mmizimu si ndikukhulupilira kuti amagwilizana kwenikweni why nkhani zake ndi zomwezi tikunena apazi , and osatila kwa ma MP's samafunikaso ai. Bwina nkhani yabwino ndi imenei yoti yowachepesela malo amene amalamulira why kupewa kusamvana .

  • @MwizaChavula
    @MwizaChavula25 күн бұрын

    Bad idea

  • @wilsonmmangeni9888
    @wilsonmmangeni988825 күн бұрын

    useless discussion ever. analedzela awa

  • @goliathkujngo3262
    @goliathkujngo326225 күн бұрын

    Komaso ngati vice ali wanzeru ngati mene alili achilima muja ndekuti sangamukonde chifukwa amawona kuti sbwanawo kuposedwa choncho otsatira bwanayo amayamba kumunamiza bwanayo

  • @FosterChilumba

    @FosterChilumba

    25 күн бұрын

    Who told u Chilima ndi wa nzeru?

  • @HaroonSaidi-jv3ek
    @HaroonSaidi-jv3ek24 күн бұрын

    Kodi vice president ndi deputy president kodi Tuttle ya mphamvu ndi iti

  • @alexsumani6823
    @alexsumani682326 күн бұрын

    Olo utatha mpando opanda ntchito anthu ake sakondana 😮😮

  • @user-lc3sw8iz2g

    @user-lc3sw8iz2g

    26 күн бұрын

    Akufuna kubweletsa u prime minister

  • @Felix-os3oq
    @Felix-os3oq25 күн бұрын

    Ma scientists a fake.

  • @FosterChilumba
    @FosterChilumba25 күн бұрын

    Good idea office of vice President is just wasting pples taxpayers money Koma nanga president yo passed on?

  • @JulianaNyerere
    @JulianaNyerere25 күн бұрын

    Km ziliko ku bomako

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula493725 күн бұрын

    Guys nanuso you are piling too much to the already power intoxicated president! Create mmalo mwa "VICE PRESIDENT" to "PRIME MINISTER" like ku ZIM...mpatseni ntchito zake PRIME MINISTER" plus delegation from president pomwe zangakwanitse...koma Prime Minister go in all ministries to ensure ntchito ikugwirika...MULI BUSY PROTECTING PRESIDENCY ....Don't forget ma president ambiri amakhala clueless then with Prime Minister zitha kumayenda