Afford yati siyokondwa ndi zochitika za Mkasa Chifukwa cha Nyimbo iyi.

Пікірлер: 224

  • @ThomasSibale-dx6bg
    @ThomasSibale-dx6bg2 күн бұрын

    Mumakwana amphungu Joseph I like your songs

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2xАй бұрын

    Big up Nkasa umaimba zoona zokhazokha zounikira anthu❤❤❤❤❤ APM pachiongolero basi wina afune ❤❤❤

  • @patrickzembani4315
    @patrickzembani4315Ай бұрын

    ❤❤❤❤❤❤❤ very powerful mr favourite Mkasa💪💪

  • @user-ri8em6my2e
    @user-ri8em6my2eАй бұрын

    Kung'alura kung'alura basi mkasa wabwera ngati coming ADad My vote 🔥🔥

  • @geofreydzinyemba6107
    @geofreydzinyemba6107Ай бұрын

    Good song Mr nkasa keep it

  • @GiftFredoh
    @GiftFredohАй бұрын

    Ndakwela yomweyo ankasa mumakwana inuyo ❤❤❤

  • @OjessAndisoni

    @OjessAndisoni

    26 күн бұрын

    Mumakwana.ambuye nkasa

  • @SirpromiseMatabwa
    @SirpromiseMatabwa15 күн бұрын

    🎉🎉🎉 respect mkasa

  • @chrismezalumo5698
    @chrismezalumo56986 күн бұрын

    Mr Nkasa deserve a degree of honor Dr Nkasa on his musical journey which which sheds a light to those who are in the darkness

  • @Thewarrior7093
    @Thewarrior70938 күн бұрын

    What a beautiful song it is. Agalu a mcp munya muona

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fkАй бұрын

    Big up Nkasa kuswakuswa, chilungamo kuyenda ngati madzi 🔥🔥🔥🔥

  • @BittonRashid
    @BittonRashid4 күн бұрын

    Kuyankhula mudayamba kale Mr mkasa ndife osanva achina tione zina koma zoonazi tizaona nazo mkamwa mwankango mcp izipita abale anga kuba kwanyanya.

  • @warrenmwambazi8342
    @warrenmwambazi834213 күн бұрын

    Nice tune 😊

  • @user-fr9ss6lc2t
    @user-fr9ss6lc2t27 күн бұрын

    Nyimbo yabwino heavy. Munthu ukachemelera chinthu chabwno zimachita kukoma chonchi

  • @agreementphiri5416
    @agreementphiri5416Ай бұрын

    This guy is good always. Don’t be jealous of him please. Nkasa,💪💪

  • @lucianojames7555
    @lucianojames7555Ай бұрын

    Inuyo ndi akatundu Ulemu Wanu Mr mkasa keep it up wina aphulika ndithu 😂😂

  • @user-qg4it7my9n
    @user-qg4it7my9nАй бұрын

    i love this song watching from cape town

  • @user-pd4ru7sg2s
    @user-pd4ru7sg2s14 күн бұрын

    Dolo kmb namiyambi sopano m'bwalo. God give you a long live

  • @LacksonChikho-ow5kw
    @LacksonChikho-ow5kwАй бұрын

    Big up mr nkasa

  • @AmandaConstance-fx8cr
    @AmandaConstance-fx8crАй бұрын

    Amen 🙏 🙏 🙏 Nice song

  • @BhekiMavundla-po2bq
    @BhekiMavundla-po2bqАй бұрын

    Mkasa eish! ndikatundu omanga ndimawaya/mashini,mfundo pamaimbidwe ake palibenso,uyu ndi dolo woganiza bhoo heavy kkk ❤❤❤

  • @user-fx4pp2xt7g
    @user-fx4pp2xt7gАй бұрын

    Nice song Dpp my vote 🗳

  • @HannaAsima-t4f
    @HannaAsima-t4f15 күн бұрын

    Wow 😍 that's great advice

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480Ай бұрын

    Koma mkasa machine 😂😂

  • @chakakachaka-man
    @chakakachaka-man26 күн бұрын

    More fire 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @abdullalajabu5871
    @abdullalajabu5871Ай бұрын

    inuyo ndi big basi mbambande akuti olo kuyifusa mizimu ikanakana kuti tambala wakuda asabweleso 💪💪💪😅😅😅

  • @fredsemu7136
    @fredsemu7136Ай бұрын

    This is prophetic song

  • @MustafaHenderson
    @MustafaHenderson25 күн бұрын

    Mkasa keep it up singing trye

  • @vitumbikokamanga5869
    @vitumbikokamanga5869Ай бұрын

    Nkasa ndi machine ❤❤❤❤

  • @user-ik5sz8hc6f
    @user-ik5sz8hc6f8 күн бұрын

    Sangakondweletse onse.Ndibwino amuleke chifukwa nayenso mpomwe akupezela mchere wake

  • @johnbakali27
    @johnbakali278 күн бұрын

    Chipani chantendele on repeat 🎉😂😅❤

  • @TiongeChirwa-kz1ub
    @TiongeChirwa-kz1ubАй бұрын

    DPpppppppppp woyeeee ❤❤❤❤❤❤

  • @jonathanmbewe4246
    @jonathanmbewe4246Ай бұрын

    Nkasa always unpredictable osamukhulupilila

  • @wilisonbornface4282
    @wilisonbornface4282Ай бұрын

    Nice song

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h9 күн бұрын

    Nkansa sawopa naye tili kumbuyo kwako masa we still remember azibale athu anaphedwa ndi mcp zaka zambuyomu sitilora kuti mcp izawinenso 2025 never

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2czАй бұрын

    Nice one ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko9 күн бұрын

    Nyimbo yamphanvu kwambiri moto kuti buuuuuuuuuuuuuu 🔥 🔥

  • @ZekezekeNjala
    @ZekezekeNjalaАй бұрын

    Odana ndi nyimbo iyi usiku amawuluka ndithu nkasa never give up

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd

    @JohnmarkNazombe-hi9xd

    Ай бұрын

    😂😂

  • @JohnKanjete
    @JohnKanjete3 күн бұрын

    Uyu wangonena zabwinozo basi ndipo palibe vuto apaaa😂😂

  • @user-ji4xn6me8d
    @user-ji4xn6me8dАй бұрын

    Amatha uyu siza a Lucius Banda ai

  • @blessingsnyalo-rp9ko

    @blessingsnyalo-rp9ko

    9 күн бұрын

    Ndipo live

  • @gibbohtrust6118
    @gibbohtrust611824 күн бұрын

    Ameneyu sazatheka

  • @user-oz1ts3yi7d
    @user-oz1ts3yi7dАй бұрын

    Nkasa youre number one 🎉🎉

  • @PaulBanda-wm2kq
    @PaulBanda-wm2kqАй бұрын

    Ndine zambian ❤ndimati ndingofunsa AFFORD ndi chanico🙏🙏

  • @chekiamaabdul5083

    @chekiamaabdul5083

    Ай бұрын

    Afford ndi chiwelesye cha achakorwa nivipuwa wanvela ka iwe chifukala

  • @PrinceKachimanga

    @PrinceKachimanga

    Ай бұрын

    they want to.get back in power

  • @petermanMitambo
    @petermanMitambo14 күн бұрын

    Nichikali ichi panyimbo kkkk long live phungu Joseph mkasa

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733Ай бұрын

    Apa ndiye wabwera mkasa umasiya kuti nyimbo ngati izizizi

  • @samdiverson9733
    @samdiverson9733Ай бұрын

    Apm ikulowa Malawi wafikapa sakufuna azitsogoleri a try and error apm only hope for Malawians

  • @MarvellousTech-kz6no

    @MarvellousTech-kz6no

    Ай бұрын

    Uyu ndiye mkasa amene ndimamudziwa ine , na pankhani yoyimba , amathira mbalume, adzaima naye ndindani , !

  • @Okalekale

    @Okalekale

    Ай бұрын

    Anapanga chani uyu?,Bingu yekha,awa ndimanyaka palibe chimene anapanga.Chiyambire cha democracy munthu anapanga zooneka ndi Bingu yekha,zinazi ndimbava zokha-zokha,dziko la Malawi linapita ndi Kamuzu ndi Bingu.Nkasa waona kuti chifukwa anthu akuganiza kuti Chakwera wapha Chilima ndiye kuti DPP idzawinaso wayamba kale kuseteka matako a Peter,opportunist iwe ndale za pa Malawi mwazilowetsa umbuli kwambiri,dzikoli lalowa chintabwalala zoti lingatukukenso ndakayika pokhapokha zipani zonse zitakhala pansi ndikupanga government of national unity.

  • @DennisWachepa
    @DennisWachepaАй бұрын

    Nthawi ya kongelesi eeish. I am speachless

  • @user-sb2mw3xz4j
    @user-sb2mw3xz4jАй бұрын

    Munthu odana ndi chilungamo ndi choncho, Nanga lero si izi chilima ndi anthu kulibe, Nkasa volume 🎉please

  • @AlexMthunziChimpeni
    @AlexMthunziChimpeni23 күн бұрын

    Pa yekha Dpp siyingawine zizachitike za ku south Africa

  • @rashidsabwe1616
    @rashidsabwe16169 күн бұрын

    Mkasa umakwana❤

  • @user-tb9wn1hb3m
    @user-tb9wn1hb3mАй бұрын

    Mkasa umativetsa kukoma ndi nyimbo zako

  • @FrankKalako-tm1bp
    @FrankKalako-tm1bp11 күн бұрын

    Nkasa big up❤❤❤❤

  • @MphimbaMphimba
    @MphimbaMphimbaАй бұрын

    Kkkk koma nkasa mpaka "kuthila madzi pasimenti kut akolope ndimatako" kkkk

  • @IsaacKachimangagamah
    @IsaacKachimangagamahАй бұрын

    Big Man mumatha kukwenza kamba muntengo

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348Ай бұрын

    Koma nkasa ndi nkasadi😂😂😂😂❤

  • @BiquitoniNsandamila
    @BiquitoniNsandamilaАй бұрын

    Nyimbo imeneyi ndi 2018 musayidadwe lero . Nyimbo za nkasa zimapereka ulosi ameneyu ndi phuuuungu jooooseeephhh nnnnkasssssaaaaaa

  • @thomasphiri7799

    @thomasphiri7799

    Ай бұрын

    really 2018?

  • @user-ri2vi2fd5v

    @user-ri2vi2fd5v

    Ай бұрын

    Uzikanamiza banja lako wamva galu iwe, moti tonse pano 2018 tikalephere kuimvera ukamve iwe wekha

  • @AmossAkbar-bt1ks

    @AmossAkbar-bt1ks

    Ай бұрын

    Yes nyimbo iyi anayiyimbadi mu 2018 ndithu musayiware chikumbusa nkhwangwa ndi chisanu

  • @AdsonNamakonje
    @AdsonNamakonjeАй бұрын

    Wamenya kwambili kasa, piter akangoliwa boma galimoto ukwela

  • @isaackaisi8623
    @isaackaisi86235 күн бұрын

    Mkasa ndi machine opangira machine azake

  • @KenuelIyanMarcus
    @KenuelIyanMarcus3 күн бұрын

    Amuna awa

  • @user-kx4og4mv5y
    @user-kx4og4mv5yАй бұрын

    😢😢😢😢 Lero Chilima ndimbiri

  • @AlexHenere-r6l
    @AlexHenere-r6l5 күн бұрын

    Mkasa waimba bwino. Imenei taikonda zikmo

  • @PaulDaka-dc3re
    @PaulDaka-dc3reАй бұрын

    Kuganiza mwakuya Big man paja tisaiwale ndi phungu

  • @CharlesChambo-uz9pf
    @CharlesChambo-uz9pfАй бұрын

    Umakwana Mr Nkasa

  • @RicardoManuelEstivin
    @RicardoManuelEstivin18 күн бұрын

    Nkasa umaitha kwambili ❤

  • @EDSONMAKIYI-mu8ye
    @EDSONMAKIYI-mu8yeАй бұрын

    Powerful

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2lyАй бұрын

    Uyuu akumwa ambuye ntengeni straight kkkk

  • @Gift-gt8em
    @Gift-gt8em6 күн бұрын

    No jealous Nkasa.umatha

  • @PhillipNyaugwe
    @PhillipNyaugweАй бұрын

    Nkasa umachita bwino koma takhalani pachimozi please yehova akusamalire

  • @user-lb6ek3ee6d
    @user-lb6ek3ee6dАй бұрын

    Zina kambu zina leku DPP MORE FIRE i like you Mr Mkasa taziwona tokha Malawi MCP mukozeke kuti tsopo mukukakha zaka 100 muli kunja simudzalowsso boma ayi dzitsiru dzawathu

  • @ChiefJustin-cl8jl
    @ChiefJustin-cl8jlАй бұрын

    Zakumwa za mtundu wanji tikubweletsele mfumu mkasa ❤

  • @OsmanMika
    @OsmanMikaАй бұрын

    Ulemu wanu mr Nkasa kunyimboyi osati manyaka timava aja osapota mcp agaluu

  • @johnmponda9070
    @johnmponda907010 күн бұрын

    This is exactly what was really happening in those days now again but this is really worse

  • @EvraBenes
    @EvraBenesАй бұрын

    Kuma yamikila m,zathu akapanga chabwino nkasa patsogolo

  • @SaleemNicks-fr3zo
    @SaleemNicks-fr3zo5 күн бұрын

    Nkasa timakukondani bwana nyesani ina mcp imve pain

  • @khaleedsaidi6232
    @khaleedsaidi6232Ай бұрын

    Bg up mkasa

  • @user-qq1uj7ct6n
    @user-qq1uj7ct6nАй бұрын

    nkasa amatha. kuvunga mbili yonse ya mcp.. Koma akut vuto amalawi stimachedwa kuiwala 😭😭😭😭😭😭

  • @user-my4gr1pv8h
    @user-my4gr1pv8h27 күн бұрын

    Nde mwati mcp ndima chani😂😂😂😂😂km zoona2

  • @user-sr4fe5bb2w
    @user-sr4fe5bb2wАй бұрын

    Mukamaika zithunzi za a dad anuwo muziika za mmene akuonekera panopa osati zakale kalezi

  • @BhekiLithuli
    @BhekiLithuliАй бұрын

    Mbuyanga taponyani number yanu plz tiponyeko ya cold drink plz

  • @user-im4tc9qi4j
    @user-im4tc9qi4jАй бұрын

    Mesa nyimbo iyi ndiyakalekale?

  • @MustapherDavie-su3nk
    @MustapherDavie-su3nkАй бұрын

    Big up mkasa

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimangaАй бұрын

    nde afford yakwiyanso chani😂😂😂😂😂😂😂munthu asanene chilungamo???

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomoleАй бұрын

    Chilima adaferanji mkasa more 🔥

  • @LacksonChimwalire
    @LacksonChimwalireАй бұрын

    Big up mkasa that's the fact

  • @OssmanAbubaker-sq2xz
    @OssmanAbubaker-sq2xzАй бұрын

    Zoonadi Simukunamana Mr Mkasa ulemu

  • @paultronix-jd8kj
    @paultronix-jd8kjАй бұрын

    Padulidwa mtengo waminga sipathekadi kumera wa papaya eeeish nkasa ka volume kakwezedwe pang'ono

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimangaАй бұрын

    DPP NDI MORE FIRE...RESPECT

  • @JamesStand-oi2px
    @JamesStand-oi2pxАй бұрын

    Number one

  • @StevenKalonga-bp2vt
    @StevenKalonga-bp2vtАй бұрын

    Big man muzetikumbusa pafupipafupi

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xdАй бұрын

    Zoooooona❤❤❤❤!!!!!

  • @GiftBanda-u1g
    @GiftBanda-u1g15 күн бұрын

    Mamuna oziwa kuyimba nkasa

  • @GiftSinalo-ku6zb
    @GiftSinalo-ku6zbАй бұрын

    Eeeeee koma nkasa aaa inu ndi bigy mawu ndilibe mmatha kulinganiza eee

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310Ай бұрын

    Mkasa ndi big uyu amaimba

  • @KhristopherKamphinda
    @KhristopherKamphinda11 күн бұрын

    Kkkkkkkkkkkkk amkasa sadzatha 😂😂

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6erАй бұрын

    Taponya nambala yako ndikupatse ya tea

  • @MalawianCamera

    @MalawianCamera

    Ай бұрын

    😂😂😂😂 Boss

  • @FelixMachika
    @FelixMachikaАй бұрын

    Fact! 👍👍👍👍👍👍

  • @RicardoManuelEstivin
    @RicardoManuelEstivin18 күн бұрын

    Umenyenso inanso yomuza live chakwera kuti siwe mfumu ayi koma zinango lakwika

  • @MasterDombala
    @MasterDombala6 күн бұрын

    Zoona Malu mkasa

  • @GanieAlidih-gu7no
    @GanieAlidih-gu7noАй бұрын

    Umakwana bro

  • @JerryChain-cz8ru
    @JerryChain-cz8ruАй бұрын

    ❤❤

  • @YusufuHaji-gb4kf
    @YusufuHaji-gb4kfАй бұрын

    Wina afune asafune APM akulamula, mkasa ndi katundu Dpp more fire ✅😜😜😜