Achinyamata apita kunyumba ya VP Michael Usi kukasiya uthenga

Пікірлер: 126

  • @shayrafernandeslatif9556
    @shayrafernandeslatif955622 күн бұрын

    Madam kaliyati ankhale president wa UTM

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce223 күн бұрын

    Osaopa 💪 Osatopa 💪 Osafooka 💪 SKC FOREVER IN OUR HEARTS 💕 NO! Alliance with MCP ndi chipani ca kupha!

  • @AaronzoAaron

    @AaronzoAaron

    20 күн бұрын

    Aaaaa kokaaaaa

  • @user-oc1uc6gz3w
    @user-oc1uc6gz3w23 күн бұрын

    No alliance with MCP ndiakupha amenewo ng'ona dzimenedzo

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri687323 күн бұрын

    Good achinyamata a utm munthu oipa aziwoneka poyera osati ena amene akubisa anthu oipa kuti aziwoneka abwino. Osaopa osafoka. I

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg23 күн бұрын

    Alliance ithe basi

  • @ChifundoChiwanda-ru3pg
    @ChifundoChiwanda-ru3pg23 күн бұрын

    I agree 100% NO ALLIANCE WITH MCP

  • @omarajibu860
    @omarajibu86023 күн бұрын

    Ndipo mwayitha, wina asowa wopanga naye alliance.

  • @CeniaMayeni

    @CeniaMayeni

    23 күн бұрын

    😂😂😂😂😂😂

  • @marryphili5419
    @marryphili541923 күн бұрын

    Good excellent that is my bro

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire22 күн бұрын

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 achinyamata!!!moto kuti bhu! achinyamata aneneo,wachinyamata ndi wachinyamata ndi kawawa

  • @BaldwinBanda-gd9zo
    @BaldwinBanda-gd9zo23 күн бұрын

    Very good

  • @mishecksipolo7153
    @mishecksipolo715323 күн бұрын

    More fire youth men,big up

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx23 күн бұрын

    That's the spirit guys. Fight for our rights

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v23 күн бұрын

    No alliance with Chikangawa party

  • @user-ww4ei5fb7d

    @user-ww4ei5fb7d

    22 күн бұрын

    😅😅😂

  • @user-ri8em6my2e
    @user-ri8em6my2e22 күн бұрын

    Moto kuti 🔥🔥Osawopa,Osatopa, osafooka

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w23 күн бұрын

    UTM, DPP, AFORD ndi UDF udzakhala mgwirizano wa mphamvu kuchotselatu nyansi zili mu bomazi.

  • @IssacMateyo

    @IssacMateyo

    22 күн бұрын

    Ndiye zopusazo zimenezo akapangeso gwilizo wina apange okha kaya ndiye kumeneko sakanamizaso

  • @user-pv9uk6sc3w

    @user-pv9uk6sc3w

    22 күн бұрын

    @@IssacMateyo no brother, pawokha sangafike 50+1, kungoti all leaders akhale ndi maudindo in government.

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p22 күн бұрын

    Good news for ever🎉

  • @LucianoKapepuza-sy9wx
    @LucianoKapepuza-sy9wx22 күн бұрын

    Ngati usi sakufuna akhale Ku MCP sivuto tizamumangira limozi iyeyoso akuziwa zonsr

  • @kingssalema3364
    @kingssalema336422 күн бұрын

    Yaaaa, Ukunde kuganizaa bhoooo kujaa ukuuuu.

  • @amoschataika7440
    @amoschataika744022 күн бұрын

    Big up Guys

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np22 күн бұрын

    Kuli Yehova kumwamba

  • @Ishmael376
    @Ishmael37622 күн бұрын

    Yes I gree ❤100%

  • @user-ww4ei5fb7d
    @user-ww4ei5fb7d22 күн бұрын

    Kkkkkkk 😂, MCP idaotcha CV pa 10 June

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d23 күн бұрын

    Ndipo asakupusiseni muthetse m, gwilizano umenewo osakonda ndrama anamusasa kale Tate wanu m,pakana. Amupha chokhalila kumeneko ndi chani

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus22 күн бұрын

    Ehhhhe No Alliance Iyyyah Makape a MCP akhale okha

  • @user-ty4pq5ub3q
    @user-ty4pq5ub3q22 күн бұрын

    Zilikotu zilikotu.....halayansi must end sure...aliyense adzadutse yenkha....

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeon23 күн бұрын

    Asaopa osafooka I'm miss chilima

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo419022 күн бұрын

    I like this

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw23 күн бұрын

    Mayi kaliyati ulemu wanu

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du22 күн бұрын

    More fire

  • @thomasbotha9790
    @thomasbotha979023 күн бұрын

    Very good utm

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles234823 күн бұрын

    That's great move😂😂

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo22 күн бұрын

    Anyamata ipatseni moto tatopa ife

  • @IssahAluba
    @IssahAluba22 күн бұрын

    alliance ithe MCP ilibe pabwino

  • @user-kc6tq6hz1b
    @user-kc6tq6hz1b23 күн бұрын

    Good job

  • @user-iv4dj1pi3b
    @user-iv4dj1pi3b22 күн бұрын

    Viva skc ...RIP..

  • @MarkManyowa
    @MarkManyowa22 күн бұрын

    Go deeper

  • @user-re7fo3be2z
    @user-re7fo3be2z22 күн бұрын

    Osawopa

  • @user-it5zv2nz7f
    @user-it5zv2nz7f20 күн бұрын

    Utm moto unandi mwachita bwino mama kaliat😊

  • @SolokingChimzy-yt7dj
    @SolokingChimzy-yt7dj23 күн бұрын

    Kkkkkkkk dziko la pansi

  • @user-vx5kv8dz3d
    @user-vx5kv8dz3d23 күн бұрын

    Achinyamata Saulosi adapita komano presidential immunity ichoke tikwanilise masophenya a SKC referendum basi . Achinyamata dziko lino Palibe angalikoze koma ife. Chakwera adati azachepesa phamvu koma kuti .

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w23 күн бұрын

    Anyamata akunena zoona osapanga mgwirizano ndi MCP .

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp23 күн бұрын

    Mphamvu zokuphatu osati kulamulila dziko

  • @user-bg7ur1gw1q
    @user-bg7ur1gw1q23 күн бұрын

    Yaa ineso ndagwilizana nazo asiyeni agaluwo

  • @PrinceLuckKondowe
    @PrinceLuckKondowe23 күн бұрын

    No alliance with mcp

  • @mathewsnachuma8086
    @mathewsnachuma808623 күн бұрын

    Zayamba bwino

  • @FrankSpison-o7o
    @FrankSpison-o7o19 күн бұрын

    🎉🎉🎉😂 good luck utm

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f20 күн бұрын

    Gwadani guys, no Alliance at all

  • @MerryWayson
    @MerryWayson23 күн бұрын

    Sitirora

  • @TalazanGamah
    @TalazanGamah23 күн бұрын

    We follow u guys no mo alliance

  • @augustMag
    @augustMag23 күн бұрын

    More fire youths

  • @CharlesTambala-zn2bd
    @CharlesTambala-zn2bd23 күн бұрын

    Osaopa... Osafooka osatopa

  • @user-ey6in8is5h
    @user-ey6in8is5h22 күн бұрын

    Ndimayembekeza kuva zimenezo

  • @user-wx7pw8xg6x
    @user-wx7pw8xg6x23 күн бұрын

    Tienaoni amenewo alliance yathapo basi apa

  • @StuartGondwe
    @StuartGondwe19 күн бұрын

    Wabodza uyu kunali ku office ya UTM ku area 10 kulilongwe tsiku lothesa mgwilizano lija osati zomwe akunamazo

  • @allansili-rc9gc
    @allansili-rc9gc23 күн бұрын

    Wow osaopa

  • @AlickMacsando
    @AlickMacsando23 күн бұрын

    Bora pamenepo

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga72323 күн бұрын

    Amalawi ake si amasiku ano

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp23 күн бұрын

    Mphamvu zokuphatu osati kulamulila dziko 0:05

  • @user-wl9vh6rc5z
    @user-wl9vh6rc5z23 күн бұрын

    inthe Alliance.

  • @happymumba2261
    @happymumba226123 күн бұрын

    Zofunikira kuipasa moto osaopa

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon342923 күн бұрын

    Zikathela mapenateee

  • @RachealHarawa-xc9gs
    @RachealHarawa-xc9gs23 күн бұрын

    Za alliance zatha apapa hiyaaa

  • @PiliraniMukhupi
    @PiliraniMukhupi23 күн бұрын

    Uthe kumene

  • @JamesOsman-cz9cw
    @JamesOsman-cz9cw23 күн бұрын

    Kkkkk km kuki kugwadatu

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe821423 күн бұрын

    🔥🔥🔥🙌

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y23 күн бұрын

    Kwavuta

  • @LysonMtalika-tb6fk
    @LysonMtalika-tb6fk23 күн бұрын

    Powerful!!!!

  • @EstherZintambira-sq3yy
    @EstherZintambira-sq3yy23 күн бұрын

    Mcp ndikachaniso

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo22 күн бұрын

    Kapena kumene amakhala Kale kuja mwina kapena

  • @user-gy8yn6qw2k
    @user-gy8yn6qw2k23 күн бұрын

    💪💪💪💪💪

  • @KennedyBanda-ci2wt
    @KennedyBanda-ci2wt23 күн бұрын

    Osaopa ndithu

  • @harrispheleni2205
    @harrispheleni220522 күн бұрын

    Calculated move

  • @HemsonMandolo
    @HemsonMandolo22 күн бұрын

    But be care some are thieves u never know

  • @RodgersPhiri-ju1eo
    @RodgersPhiri-ju1eo19 күн бұрын

    Mwachitabwino muyime panokha ifenso ku DPP sitikukufunani agalu achabechabe inu zoti mubwelela ku DPP sizitheka Mesa mumatitukwana inu chonsecho chilima kupanda DPP bwezi ataziwika kuziko la Malawi mwana oti tinachita kuntola nkumatitembenukila kutiyimila pachulu chifukwa choti kaliyati amamupusisa yendelani yanu tikuoneleni

  • @CeniaMayeni
    @CeniaMayeni23 күн бұрын

    Mbola kkkkkk Mudya ndalama koma movutikila 😂😂😂😂

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp23 күн бұрын

    Mmmm

  • @alickchiumia2616
    @alickchiumia261613 күн бұрын

    Kusowa zochita mumakomomu

  • @user-lg6ym4hz3w
    @user-lg6ym4hz3w22 күн бұрын

    Kkkkkkkk 😂😂😂😂😂😂😂 Amen

  • @BlackSpiderujayo
    @BlackSpiderujayo22 күн бұрын

    Usi Munthu oipa

  • @MoosahChikwakwa
    @MoosahChikwakwa22 күн бұрын

    😂😂😂 kodi guys ndiye kuti simungakomentepo za ubwinoko wa MCP 😂😂😂😂 ndiye kutidi anthu amenewadi ndioipa eti😂😂😂😂 kumanya mundu kutama najo eti😂😂😂 my son give me sima let me simaring myself 😂😂😂😂 ndiye mwati chikatere madolowa akunva bwanji😂😂😂ndikuivunga pa mukuru vote yanga ku ppd😂😂😂 ayi ndalakwisa ku fdu😂😂😂 ayi ndalakwisanso koma ku MTU 😂😂😂 this week mpaseni mpata akalape😂😂😂 chifukwa ijayo ya mchinga ija yandikwana kwabasi.

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn20 күн бұрын

    Munaika nokha MCP m'boma lero MCP yakuchangamutsani and you have nowhere to go

  • @JacksonMoyo-tm8dv
    @JacksonMoyo-tm8dv21 күн бұрын

    Chakwera kulibe chake 2025

  • @Kasiya-gp7fm
    @Kasiya-gp7fm23 күн бұрын

    Wozugurira mitu nde iwetu😅

  • @user-ev6bi7jr7g
    @user-ev6bi7jr7g23 күн бұрын

    Za m'mbuyo mwa alendo zimenezi munayenera kuzichita chaka chatha ena asanaluze myoyo yao

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo22 күн бұрын

    Musamanamepotu apa kunyumba kwa vp angaloweko chotcho kulibe asitkali zazi kkkkkkk

  • @louisbonongwe8537

    @louisbonongwe8537

    19 күн бұрын

    Ur thinking and sight has boundaries i can witiness....unaona zinachitika ku kenya?anthu anakaphwanya ku parliament.....anthu akakwiya bwana mfut ija samainva.

  • @ephraimkadamika
    @ephraimkadamika23 күн бұрын

    No alliance with mcp period

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x23 күн бұрын

    😂😂😂😂

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz23 күн бұрын

    Ngati simukuopa nde mukugwada chani zitsiru za amalawi

  • @inessmsiyambiri8517

    @inessmsiyambiri8517

    23 күн бұрын

    Chitsiru ndi iweyo

  • @hanifahmponda8711
    @hanifahmponda871123 күн бұрын

    Zowona galu modzi tsakukuma kawili kuluma koyamba ndi mistake ya galu koma kukuluma kachiwili ndi mistake yaiwe munthu nde MCP yakuphelani chilima It's ok kuti munayiwala kuti MCP yokupha KOMA PANO MUKALOLATSO KUKALATSO KHASU LA MCP DZIMU WACHILUMA UKUSWANI DZIDI MUKOMANA NDI NYENKWEEEE AKWENI CHENJELANI MCP SICHIPANI CHOPANGA NACHO UBALE MAWONATSO NOKHA manganya uyutu wamitsala mutsamutengele dzelu zaka tiyene nadzo paja muti sutuluka akulowa TIYENI TIDZILOWANO KKKKLL

  • @CHIWSABINYAMBOSE
    @CHIWSABINYAMBOSE18 күн бұрын

    No zithe basi

  • @user-bd5kw8oq1r
    @user-bd5kw8oq1r23 күн бұрын

    Zopanda pake mbuli zokhazokha

  • @KhooMadex

    @KhooMadex

    23 күн бұрын

    Ukati what are you trying to say, anthu sakufuna alliance ndi mcp so akhala bwanji mbuli?

  • @user-bd5kw8oq1r

    @user-bd5kw8oq1r

    23 күн бұрын

    @@KhooMadex ndi malingalilo awo woti chilima amachita kuphedwa ndi omwe ali mmutu mwawo komaso achita kutumidwa ndi ena a mumchipanimo omwe sakufukondwa ndi kusankhidwa kwa a Michael usi ndi ndale izi zimafunika mbuli zizimva mabodza awo ine ayi 😊😊😊

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r23 күн бұрын

    Mcp chipani chakupaa

  • @user-bd5kw8oq1r

    @user-bd5kw8oq1r

    23 күн бұрын

    Ndipo inu 😅 Ngati DPP imaphaso ma lubino,isa njaunju ,chasowa,ndi ena bola yesu basi ndi more Fire yesu ossti andale ayi koma ine ndikavotera MCP mnkhani zopanda umboni sitichita nawo ngozi ya ndege ndimayidziwa ine mkovuta kupulimuka 😅😅😅😅

  • @AbdulKaswiri
    @AbdulKaswiri22 күн бұрын

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @CatherineKumwex
    @CatherineKumwex23 күн бұрын

    😂😂😂

  • @AbdullahaziziAmoswalala
    @AbdullahaziziAmoswalala23 күн бұрын

    ?😂😂😂😂😂

  • @officialturfrican_ent
    @officialturfrican_ent23 күн бұрын

    Sorry i saw white woman, correct me😢

  • @officialturfrican_ent

    @officialturfrican_ent

    23 күн бұрын

    This black dude humbled himself for a reason,,,kumalawi kulibe kape if u oppose kape ndi iweyo nyini yamako

  • @ManifoldPhiri
    @ManifoldPhiri22 күн бұрын

    Anthu akumamkhalabe ndi nthawi ya zimenezi mmalo mokonza mtima wanu kuyanjana ndi mulungu. Kodi simunawelenge bible zochitika mmasiku otsiliza?

  • @stevenoah4578

    @stevenoah4578

    22 күн бұрын

    Komatu ngati inu mwaika comment ndekuti mwatayanso nthawi ndi zomwezi. Simukusiyana ndi winna aliyense. Don't pretend to be spiritual.

  • @ManifoldPhiri

    @ManifoldPhiri

    22 күн бұрын

    @@stevenoah4578 kkkkkkk koma achinyamata akunyanya

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj23 күн бұрын

    Achita kutumidwa Mcp ndi chipani cha mphavu pachokha

  • @ShalifahKasimu

    @ShalifahKasimu

    23 күн бұрын

    Mphavu yake itiso nanuso

  • @innocentmusuli7380

    @innocentmusuli7380

    23 күн бұрын

    Kkkkkk mukutanthawuza kuti a UTM atuma anyamata a UTM ku mtsokhano wa UTM zosekesa kwabasi anthu ena mitu sigwira

  • @SaidiMbawa-st6bj

    @SaidiMbawa-st6bj

    23 күн бұрын

    @@innocentmusuli7380 a Dpp akufuna utm kuti achoke ku gwilizano koma sizitheka chifukwa akulu akulu oziwika bwino sakufuna ndiye munthu ulibe ndalama ungatani ndiposo sokhano walero cholinga chake sichimenecho

  • @SaidiMbawa-st6bj

    @SaidiMbawa-st6bj

    23 күн бұрын

    @@ShalifahKasimu ndichimene chikulamula iwe sukuziwa utm iri ndi mphavu zanji ku mcp

  • @InessMchenga

    @InessMchenga

    23 күн бұрын

    Mphamvu zake zitizo paiwo okha anakawina amene aja za zodza basi

  • @user-qq3ip1od6i
    @user-qq3ip1od6i22 күн бұрын

    Comedian is not patriot to the movement

  • @yowasschitsosa5348
    @yowasschitsosa534823 күн бұрын

    Apupuluma sakuganiza bwino achinyamawa dziko si anthu 50 ndi mamilion

Келесі