No video

A Opposition Simukudziwa Mmene A Malawi Amakukondelani - Bon Kalindo

On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo reminds opposition parties and their leaders that they are Malawi's hope in the upcoming 2025 election. However, he urges them to stop acting out of fear and instead start working for Malawians now, in preparation for the election.
Ku Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo akumbutsa zipani zotsutsa ndi atsogoleri awo kuti iwo ndi chiyembekezo cha Malawi pachisankho chomwe chikubwera cha 2025. Koma wawapempha kuti asiye kuchita zinthu chifukwa cha mantha, m’malo mwake ayambe kugwira ntchito kwa Amalawi pokonzekera chisankho.
#malawi

Пікірлер: 19

  • @user-mh7cc8up4i
    @user-mh7cc8up4iАй бұрын

    Chofunika nkuvomeleza kuti achewa ndiambili koma sikuti wosewo ndiachipani cha MCP komaso zawoneselatu kuti MCP ndiyasakho amalawi tichenjele tipemphele mowonantima kuti afitiwa kuzawachele akutamba athu oyipa chipani chakumpha chamagazi olo muzabele koma mulungu ndi mulungu I love you bon kalindo mulungu azikusungilani moyo wabwino ❤

  • @GiftPhiri-tt7nn
    @GiftPhiri-tt7nnАй бұрын

    Boooooniiiiiiii kalindoooooooo😅❤

  • @ivychithyoka1551
    @ivychithyoka1551Ай бұрын

    Etini DPP,UDF,AFFORD,UTM,,,tamverani!!!!!!

  • @marryphili5419
    @marryphili5419Ай бұрын

    Akuwopa kuphedwa ndi chakwera pajatu chakwera ndi fiti

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xmАй бұрын

    I support The DCs mwana woooopsa kwambiri akhalise Malawi

  • @ChikondiChauma-ib9pg
    @ChikondiChauma-ib9pgАй бұрын

    The DC khaniyi nde ndiyoona opposition yakahala chete kwambiri

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bsАй бұрын

    Kozani ulendo akalindo takawankhureni a DPP, UDF komaso UTM

  • @ChristopherChakometsa
    @ChristopherChakometsaАй бұрын

    Tatopa nao anthu akuba awa

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9dАй бұрын

    Abale kod achakwera analid abusa kapena anali yudac??????

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1qАй бұрын

    Ndipo nde zoonadi utsutsa sakuwoneka boma lingapanga mmene angapangile vuto zipani zotsutsa sizikuwoneka

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429Ай бұрын

    Zoona DC opposition yachetama kwambili

  • @sayidimisessa
    @sayidimisessaАй бұрын

    Ndimasatira from here south Africa 🇿🇦

  • @user-xe5lb4uf3n
    @user-xe5lb4uf3nАй бұрын

    Zoona zake otsutsa boma agonadi akuperekaa mpata kwa adani (Manyaka kkkkkk

  • @FunnyBasketball-er3vc
    @FunnyBasketball-er3vcАй бұрын

    Self proclaimed President 😂😂😂

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyoАй бұрын

    Simukunama a opposition sakuchitapo kanthu

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6yАй бұрын

    Good Messnge my Bon Kalindo

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9dАй бұрын

    Chakwera anabwera kuzampha ndi kuononga

  • @user-pl8kw3dc9d
    @user-pl8kw3dc9dАй бұрын

    Thanks the DC

  • @MarkinaJohn
    @MarkinaJohnАй бұрын

    The DC