A Ntanyiwa Mubweletse Umboni Pasanathe 72 Hrs - Agape Khombe
On Nyasa VoiceBox, Agape Khombe responds to allegations that he is a drug dealer and is implicated in the death of Ralph Kasambara in Lilongwe. He also warns Comrade Ntanyiwa of Limpopo FM, who made the allegations, about legal action if he does not provide evidence to support his claims.
Ku Nyasa VoiceBox, Agape Khombe akutsutsa phekesela yoti ndi wogulitsa mankhwala ndipo akukhudzidwa ndi imfa ya Ralph Kasambara ku Lilongwe. Iye akuchenjezanso Comrade Ntanyiwa wa ku Limpopo FM, yemwe wanena izi, za milandu ngati sapereka umboni wotsimikizira zomwe akunenazo.
#malawi
Пікірлер: 273
Mtanyiwa amanenatu zoona,paja anatumiza audio kut ndege yagwa ndipo anthu afelatu onse koma inu mumkalesa lero ndizabodzaso? Mulekeni mtanyiwa we love mtanyiwa❤
@KellyHart-pi4hd
13 күн бұрын
Ayi asamuleke awayaluse Ntanyiwa ndakharapo naye gulu limodzi akafuna kutulutsa Nkhani amakhara wasunga maumboni onse ndiye awayike pambarambanda
Ok we are waiting for the serious action you mentioned, this is how we know you people,but nothing is hidden on earth.
Utsi sufuka popanda moto bwana!!
Mtanyiwa is the best like Bakili Muluzi TV ❤❤❤❤
@user-ky4ce9gb6j
12 күн бұрын
Ndipo kwambiri tu mmm
72h ikatha bwera udzaone ngati udzazikonde galu mbuzi manu kumusi ..biry malata ali ndi ntchito yanji wamisala ngati ameneyo galu wachabechebe
This is mcp. Chilima still living we need true story about Chilima that's 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼home land
Mukfuna mumuphenso ntanyiwa.sabwera
Iiiii ndalama ndi yoopsa kwambiri,dziko lathu la Malawi chipwirikiti pwirikiti kufuna ndalama. Ana anjoka inu
Agape Khombe ndi mfiti kapena kuti nthakati oyipa kwambiri.
Mwagwidwa basi inu
Ubwino wake muli ku Boma nde mkona kuyankhula motha mawu unagwilira anamutsekera natuluka nde olo utapha munthu sukuopadi.. Bola unakangokhala. Osayankha..
Uyamba iweyo kufa bro unapangiranji I we ,oipa iwe kwambiri anaazako ndiamasiye pano chifukwa chaiwe umusiye wa Limpopo apitirize kuurura zomwe mumpanga agaru inu
Iweyo ndi galu ndipo ndiwe m'modzi mwa anthu akuphawo ndipo ukunama sungawowopseze mbuzi ya munthu😢😢😢
Munthawi inoyo muzikana koma pachoka nzimu wamunthu chilungamo chizaziwika tizanweza mopweteka zangoyamba
Mtanyiwa the best
USAOPSEZE ANTHU KUTI TISIYE KUKAKAMBA CHILUNGAMO BIG
Khombe ndi Chigawenga.
Ntanyiwa adali oyamba kunena kt ndege yapezeka ndipo onse afa mudatsutsa a aaaa a kupha inu
Onjeza kwambili moto Ntanyiwa ayamba kubwera okha pammbalambanda atchulana onseeeee🔥🔥🔥
@user-si7po9sd5i
13 күн бұрын
Kkkkkkkkkkkkkkkkk
@alfredjosen8207
12 күн бұрын
😂😂😂😂😂
Chilungamo chotani popeza here in Malawi we have corrupt judicial system
Wakupha naye azafa pomwe wakhalapo ndi pamanda usanyadire Thanks
Nkhanga ziona ❤❤❤❤mntanyiwa on limpopo fm
Thanyiwa koma sanama please mumati mwabisala koma muli pantente
Choka!! Wokonda ndalama iwe.
Iwe usanene zambili tangobwera anyamata azakuthudzule ndi Chipolopolo
Ndinu achifwamba agape khombe
Pot amalamulowo munagula
Koma ngati mukuziwa kathu mlungu azakuyalusani komaso no matter what koma muziwe zoti mlungu akukuonani nonse
Amazitenga kwanu ku Malawi 🇲🇼 koko unachita kutumidwa ulibe umunthu iwe choka apa za zii
He sounds so defensive like a guilty man kkkkk #TeamNtanyiwa
Opusa iwe u cant intimated mr Ntanyiwa bro
@CharlesmakveliNyirenda
12 күн бұрын
Kkkkk zoona bro
He talks truth
Anthu okupha inu.. what serious action you're talking about kwa ntanyiwa?
Wavomelezatu kuti ndiwe wakupha 😢😢
Ine I believe Antanyiwa as there is no smoke without fire.
Ok
It's seems like true because of response
😢unapha ndiwe osewa angakhale abodxa
Apolisi ake ati anafufuzawo panyo pako sopano pote unamata mmawindo uja machende ako
Muyaluka agalu ojiya
He confess what he is
Zaziiii
Mtanyiwa kweza volume
God knows the truth
Inuyo mukunena zimenezo ,poti mukudziwa kuti anapanga delete cc tv yonse
Utsi ukachuluka ku uwuna wa mbewa, mbewazo zimasaka malo otulukira ndipo zimatuluka zokha
Ndiye iweyo ukukana galu iwe
Eeeeh moto wabukatu apa 😢
Tikudikirani debeni muno basi borani mubwere ndimakwacha ambiri
kodi chidzungu ukuyakhulacho
Agape Khombe ndi mfiti and no doubt atha kupanga izi. Kupemphera kwachani apaaa. Bwenzani ndrama munadyera mnzanu zija
Ati ngozi, ngozi ya man made yo yoti wanzeru aliyese akuona.
Ea ali ndi umboni tu
Aaaa sukaaa ndichizungu chosamveka ndi sound yabwino, bwanji kuopseza do you think anthu angakuope asatana inu tsek
Billy Kaunda anaimba oyenda ndilupanga azafa ndilupanga ?
Akugwilani
Tive zoonad chomwe chapha anthu awa
Musapase 72yo tazingo onesa azizanu sapangaizi
Mumabisala mmbatata lero dziko lamva😢😢😢
Honestly saying mtanyiwa sakunama anthu Inu ndinu akupha 😢,,mkulimba mtima coz mkuziwa that u do it under secret nde mumatamikano not knowing that they are people like mtanyiwa
Osasiya kuulutsa umanena zoona usawaope akuphaamenewa
Mukuopa mulandu mudikire kaye utsi tsufuka popanda moto. ..munanyanya kuyera maso kunya ndalama zamangazi ku mcp munyera matumvi....tiye nazo tanyiwa ipatse moto azingokwera ma bp onkha. ..agalu afiti awa opephera chakwera muthu opanda chibwano ndi anyani ake.
Zaziii
Ndiye utani akupha inu
The MCP will never cover this up
Ntanyiwa sakubwela kuno mumugwila mumuphe ndipo siwamisala ziko loseli watchula inuyo bwanji mukuziwana
Mukufuna mtanyiwa mumudyenso akabwela , mwatchukatu ndikumwamba komwe , Olo angelo ayamba kukuthawani a MCP.
Mmmmm mwayamba kale kunjenjemelatu kkkk tchimo liZuza ochitanu
Akulu kambani za issue yanu zinazo muchedwa,,
Kutsutsaku kuperekabe mafunso
Mwatambisisa mu Lilongwe mo
Ndaletu nzoopsya, ukalowa umakhala wasainira mabvuto
Inu mukudzibvuta chani akuwalephera boma mukakwanitse inu 😂😂😂😂
@ebenezerkamanga6016
13 күн бұрын
Kkkk ndipo ase awa ndi mbuzi
@ThokohKalonga
13 күн бұрын
@@ebenezerkamanga6016 apenga awa kkk
Ku Malawi kulibe police,army ,court yachilungamo .Mulungu ekha akudziwa chilungamo chimene chaapha a Ralph ndi onse omwe anakwera ndege aja Not zomwe alengeza a boma zija
Palibe chinsisi
Ntanyiwa adali oyamba kulengeza kuti ndege yagwa onse afa uyu sanama
Yikuti 72hrs yantha bwera kuno mbuzi iwe umawona ngeti 72hrs ndikutari bwera
Ndiye ngati anatengedwa ndi transport inu mukuganiza zoti transport amenewo amadziwa komwe anthuwo amakhala, afiti okupha mukufunanso mumuphe Ntanyiwawo afiti inu ngozi yake yochita kulengayo
Koma nde #nglish ya Chichewa esh... Mot kumapetoko angoziwululatu
Very simple Comrade Ntanyiwa says ask the owner of the Lodge to provide the Camera's footage ku ma hours omwe zinachitika izi if you are failed to then you are not clean. Just prove yourself
Palibe kuopsezana aise,,,, ntanyiwa ipatse motooo malawi ndiwathu palibe kupepetsa boma linatenga ma radio onse ndinu nokha our last hope
Kunyankhula kwanu kungosonyeza kuti ndinu a MCP anthu akupha.
Bwera adzakutumbule wayaluka chitsilu.
Nanga komatu mmmmmhu Mulungu kumwambako akuwona maso Ake akuyang'ana pansi pano Mulungu alibe kumubisira kanthu zonse iye amdziyika poyera
Akuyakha wosadandaula
Ntanyiwa ndi wamusala,munthu opanda zeru,if anything amene amamuuza nkhaniwo nawoso mitu yawo ndiyoduka, Raph basi kungomuponyera basi iyeyo kumwa zoona? Iyeyo chinyama,kapena galu? Zoona
72hs yachuluka witness we found after one minutes mbuzi iwe
Ooh right,you have never taken a strong drugs as such,but fake drugs mesa!!! Ndie mukanaila zchan baba.
Anthu akudkila kuika malilo ndy Kut inuyo ngakhale mukuyankhulazo mulibe mzelu anzanu akulila inu mukufuna umbon kusonyeza Kut malilo mulibe nawo ñtchito mulungu akuoneni aliyense adzafa
Mwakwiyatu muziwika ili nd dziko 😮
Ubwino wake chilungamo chichokela kukhomo kwako. Tsiku la chilungamo likazakwana malamulo anuwo zasatha kukuombolani. Palibe chomwe muzachite ndipo muzayaluka chaka chake nchino ndi cha mawamawali
Mmmmmm Mcp singasinde, crocodile 🐊 ndi crocodile 🐊
AGAPE musathe mau Antanyiwatu ali ndi ma Audio anu bwinotu mukutha mawu muyalukatu zakuwawanitu mphakana kumuwopyezanso ndi za imfa? Anthu a MCP inu oyipa kwambiri nchito yanu kukhetsa mwazi basi
Warning of a guilty person. Ma threat zomwezi?
Kod iweyo ungavomele zoti udapanga?Mesa ukuwopa kumangidwa,kuwawona anthu kupusa?
Padziko lapatsi palibe bwenz lokonda,umati ukuchita chinthu in secret koma wina momo amazemba mkukuuza for example ena amati ndege yasowa while people were died koma mthanyiwa anabwera mkutiuza ndipo ndimomo
Mtanyiwa usasiye kunena musamuphe akuntchulanibe mukangomupha muona agaluinu palibe 72 hrs machendako
Iwe gape nawonso akuthila msembe anthu a MCP kuti ganyu unapanga okupha athu kt siku lina usazawulule usamale MCP ikupha ngati mene amuphela chilima
ichi mchakuphadi aaaaah
Mumamusewelesa maneneyi pambuyo pake azizapepesa pa court, ameneyu akalowe kuti Anthu ena atengelepo phunziro